Thyolo, Mulanje finally split from Malawi

Malawi tea.

After heightened land disputes in Thyolo and Mulanje districts, the two districts have finally seceded from mainland Malawi, a pressure group behind the move has announced.

Vincent Wandale
has made the announcement : Wandale

Leader of the People’s Land Organisation (PLO) – the pressure group behind the calls – Vincent Wandale made the announcement while speaking to Channel Africa’s flagship Zochitika Mu Africa- Chinyanja Service program on Monday night.

According to Wandale, PLO is currently formulating a constitution, looking for a Supreme Court Judge and other important statues which will recognize the two district as a state.

PLO has been calling on the Malawi government to rule that all the companies which own estates in the districts got them illegally and that tea estates which are not being used should be shared to people who do not have land for cultivation.

However, government has been silent on the matter since last year.

But according to Wandale, it is not wrong for someone to make calls for secession and the two districts have borrowed a leaf from Kosovo which seceded from Serbia in February 2008 as the Republic of Kosovo.

”You see what, we are our country here in Mulanje and Thyolo because the Malawi government has failed to meet our needs. We feel that since now we are a country, we should be able to solve the matters of land disputes with the tea estate owners our own way. Most of the land the tea estates own was taken illegally and we know the truth. At the moment, we are just looking for a Supreme Court Judge and other statues to meet the state requirements,” he said.

On whether PLO is afraid or not, Wandale was quick to say that there is no crime in seceding from a mainland nation and that Kosovo set a precedent which they are now following.

What this means

If Wandale’s remarks are anything to go by, it means that Thyolo and Mulanje are a nation on their own and not part of the Malawi government.  The two districts sit in Lhomwe Southern region area.

They will now have their own flag, Coat of Arms, Anthem, Capital City, Leadership (Prime Minister or President) and Legislature among others.

But what does the Malawi government say

The Malawi Government says it is leaving no stone unturned in trying to end Thyolo and Mulanje land wrangles between the locals and tea estate owners, but if what Wandale says is anything to go by, then the Malawi government is quite late.

 Where it goes wrong

The PLO has however received condemnation by chiefs from the two districts though the group claims the traditional leaders have been bribed not to support the calls.

Vocal Senior Chief Ngolongoliwa Thyolo maintains that the chiefs do not support the calls for the peace and unity of Malawi and not for the said attachment to the government.

“We are the custodians of the people but all of us do not know him and his conduct request police to investigate and arrest him so that he properly explains his bizarre actions,” said Ngolongoliwa.

A matter of precedent

Despite borrowing a leaf from Kosovo, the grouping has also been motivated by pressure from the Northern Region part of Malawi where leaders there had wanted the region to secede from Malawi on claims that all administrations have been ignoring the region in terms of development as well as in picking people for top government positions.

The two districts according to PLO will be known as “African Traditionalist Republic of the United States of Thyolo and Mulanje (MUST).”

 

 

 

Advertisement

2,038 Comments

 1. Izi akupanga Alimwe sizabwino especiary uyu Pitala munthalika achinkhala kuti izi akupanga ndi Atumbuka kumpoto kwadziko lathu laMalawi bwenI pano anthu atamangidwa kalekale bt bkz akupanga II ndi aalomwe I think achita kutumidwa ndi pitala yemweyo in oder kulanda mafamu mmanja mwaazungu
  I’m Bosco Banda Miliwa
  Mwana amene samamuopa even Pitala munthalika

 2. Zitsiluza anthu kuganiza mofoka basi iwe osagwila tchitomolimbika kudali boma mbuzi zaanthu mukufuna mumuphenso monga munaphela ujayi fuck sence khaniiliyose mukhudze boma basi mwalephela kugawana malile boma fuck

 3. Zitsiluza anthu kuganiza mofoka basi iwe osagwila tchitomolimbika kudali boma mbuzi zaanthu mukufuna mumuphenso monga munaphela ujayi fuck sence khaniiliyose mukhudze boma basi mwalephela kugawana malile boma fuck

 4. Chamba chimenecho akauzane ,ine ndi akwathu onse m’boma la Thyolo ndife a Malawi. Zopusa tatopa nazotu ife ,iyah,agalu eti?Inu mbuzi mukufuna kutionjezera mavuto njalayi simukuiona?Akuyambisa ndani zopusazo?Galu,mkhundakudwe,mkhupakupa,mundichimwisa inu. Ku Thyolo tasiya ana apatchire muwasamala ?

 5. Chamba chimenecho akauzane ,ine ndi akwathu onse m’boma la Thyolo ndife a Malawi. Zopusa tatopa nazotu ife ,iyah,agalu eti?Inu mbuzi mukufuna kutionjezera mavuto njalayi simukuiona?Akuyambisa ndani zopusazo?Galu,mkhundakudwe,mkhupakupa,mundichimwisa inu. Ku Thyolo tasiya ana apatchire muwasamala ?

 6. Chamba chimenecho akauzane ,ine ndi akwathu onse m’boma la Thyolo ndife a Malawi. Zopusa tatopa nazotu ife ,iyah,agalu eti?Inu mbuzi mukufuna kutionjezera mavuto njalayi simukuiona?Akuyambisa ndani zopusazo?Galu,mkhundakudwe,mkhupakupa,mundichimwisa inu. Ku Thyolo tasiya ana apatchire muwasamala ?

 7. Wandale is true tea ndiwa azungu but mindayo njathu so why we r suffering example kuchikhwawa kuli ilovo azungu amathandiza alimiwa wth 120 000 pa chaka and amawapataa fetereza matumba 11 ndi mbewu zoti azale nor only dat adagawa half ya mindayo kupereka kwa alimiwo kuti azitha kulimanso chimanga thats is why zikuyendako ku ck even alimi ali ndi ma share mukampan ya ilovo why nt us from thyolo and mulanje. Achoke azunguwo even tea akudulanso

 8. Wandale is true tea ndiwa azungu but mindayo njathu so why we r suffering example kuchikhwawa kuli ilovo azungu amathandiza alimiwa wth 120 000 pa chaka and amawapataa fetereza matumba 11 ndi mbewu zoti azale nor only dat adagawa half ya mindayo kupereka kwa alimiwo kuti azitha kulimanso chimanga thats is why zikuyendako ku ck even alimi ali ndi ma share mukampan ya ilovo why nt us from thyolo and mulanje. Achoke azunguwo even tea akudulanso

 9. iwe wanena za bushili ukulakwitsa ndipo sizikugwilizana olo pang,ono.chilichonse kumangoti bushilichifukwa chani?bushili ndiwa kumeneko?kodi mumamutola chifukwa chani? mudzafa ndiumphawi pangani za mulathyolo zo osati za bushili mumusiye apume naye.kambani nkhani mmene nkhani ilili osati zomutchula bushili chifukwa sizikugwilizana.

 10. iwe wanena za bushili ukulakwitsa ndipo sizikugwilizana olo pang,ono.chilichonse kumangoti bushilichifukwa chani?bushili ndiwa kumeneko?kodi mumamutola chifukwa chani? mudzafa ndiumphawi pangani za mulathyolo zo osati za bushili mumusiye apume naye.kambani nkhani mmene nkhani ilili osati zomutchula bushili chifukwa sizikugwilizana.

 11. iwe wanena za bushili ukulakwitsa ndipo sizikugwilizana olo pang,ono.chilichonse kumangoti bushilichifukwa chani?bushili ndiwa kumeneko?kodi mumamutola chifukwa chani? mudzafa ndiumphawi pangani za mulathyolo zo osati za bushili mumusiye apume naye.kambani nkhani mmene nkhani ilili osati zomutchula bushili chifukwa sizikugwilizana.

 12. iwe wanena za bushili ukulakwitsa ndipo sizikugwilizana olo pang,ono.chilichonse kumangoti bushilichifukwa chani?bushili ndiwa kumeneko?kodi mumamutola chifukwa chani? mudzafa ndiumphawi pangani za mulathyolo zo osati za bushili mumusiye apume naye.kambani nkhani mmene nkhani ilili osati zomutchula bushili chifukwa sizikugwilizana.

 13. iwe wanena za bushili ukulakwitsa ndipo sizikugwilizana olo pang,ono.chilichonse kumangoti bushilichifukwa chani?bushili ndiwa kumeneko?kodi mumamutola chifukwa chani? mudzafa ndiumphawi pangani za mulathyolo zo osati za bushili mumusiye apume naye.kambani nkhani mmene nkhani ilili osati zomutchula bushili chifukwa sizikugwilizana.

 14. Chomwe mungaziwe alomwe inu mukuyenera mukhale ndima passport ngat mukufuna kupita dziko la Blantyre komaso mumuuze president wanu Kaliati kut alomwe nose muzuyenda mosamala tizikugwirani deportee

 15. Chomwe mungaziwe alomwe inu mukuyenera mukhale ndima passport ngat mukufuna kupita dziko la Blantyre komaso mumuuze president wanu Kaliati kut alomwe nose muzuyenda mosamala tizikugwirani deportee

 16. Chomwe mungaziwe alomwe inu mukuyenera mukhale ndima passport ngat mukufuna kupita dziko la Blantyre komaso mumuuze president wanu Kaliati kut alomwe nose muzuyenda mosamala tizikugwirani deportee

 17. Chomwe mungaziwe alomwe inu mukuyenera mukhale ndima passport ngat mukufuna kupita dziko la Blantyre komaso mumuuze president wanu Kaliati kut alomwe nose muzuyenda mosamala tizikugwirani deportee

 18. Chomwe mungaziwe alomwe inu mukuyenera mukhale ndima passport ngat mukufuna kupita dziko la Blantyre komaso mumuuze president wanu Kaliati kut alomwe nose muzuyenda mosamala tizikugwirani deportee

 19. Kkkk Blantyre nso akhale dziko tili nd chayamba, chibisa, dalameya, Immigration, Reserv bank, tilinso nd chichiri shoping mall, stadium nd mseu wa m’mwamba pa clock tower….tiwapempha ma guyz mu NDILANDEMU atipangile ma ID.

 20. Kkkk Blantyre nso akhale dziko tili nd chayamba, chibisa, dalameya, Immigration, Reserv bank, tilinso nd chichiri shoping mall, stadium nd mseu wa m’mwamba pa clock tower….tiwapempha ma guyz mu NDILANDEMU atipangile ma ID.

 21. Kkkk Blantyre nso akhale dziko tili nd chayamba, chibisa, dalameya, Immigration, Reserv bank, tilinso nd chichiri shoping mall, stadium nd mseu wa m’mwamba pa clock tower….tiwapempha ma guyz mu NDILANDEMU atipangile ma ID.

 22. Kkkk Blantyre nso akhale dziko tili nd chayamba, chibisa, dalameya, Immigration, Reserv bank, tilinso nd chichiri shoping mall, stadium nd mseu wa m’mwamba pa clock tower….tiwapempha ma guyz mu NDILANDEMU atipangile ma ID.

 23. Kkkk Blantyre nso akhale dziko tili nd chayamba, chibisa, dalameya, Immigration, Reserv bank, tilinso nd chichiri shoping mall, stadium nd mseu wa m’mwamba pa clock tower….tiwapempha ma guyz mu NDILANDEMU atipangile ma ID.

 24. I think they have to follow right procedures bt though likhale palokha kodi ngat dziko ali ndi zoziyeneleza zobweretsa chuma mzikomo ?maganizowa siabwino akungoyenela asatelo koma avane ndiboma. poti akuti afuna akambilane

 25. Enanu musanene za mwano apa mumadalira nthochi ndi tea zochokera Ku Thyolo ndi Mulanje mukunyodzako timadalirana enanu nenani zonse mumapanga kwanuko palibe kwa njala ngati kumeneko madzi samati asefukira liti,njala yosatha mpaka munathawako kukakhala Ku Bt LlsMzudzu

 26. Maganizo Anga Ndioti Gululi Lachita Bwino Kutero Kamba Koti Zikuonetsa Kuti Boma Silikuwathandiza Pothetsa Mikangano Yawoyo. Apapa Gululi Likufuna Kulikakamiza Boma Kuti Lithane Ndi Vutoli Mwansangansanga. Zilibwino Chifukwa Izi Zikuchokera Ku Maboma Omwe President Peter Anachokera. Funso Nali, Akankhala Kuti Apanga Izi Ndi Atumbuka Boma Likanawasiya Monga Akuchitiramu Anthu Aku Thyolo Ndi Mulanje? Sakanawamanga Amenewa? Kutsogoloku Mudzamvanso Kuti Chigwa Cha Mtsinje Wa Shire Chikufuna Chikhale Dziko Loima Palokha. Izizi Zikumachitika Kamba Koti President Peter Akuoneka Kuti Akumasowa Mzeru Zakuya Zotsogolera Dziko La Malawi.

 27. Khaniyi ndiyofuna kuyinvetsetsa anthu aku Mj ndi TO zoti mungapange dziko lanu ilo ndi bodza.komanso vuto lili apa silinabwere ndi boma ili ayi.thawi imene azungu anapatsidwa malo oti azilima tea mwina mkutheka kuti tinali chiwelengero chochepa adayiwala kuti chidzakwera komanso inu #Awandale munali kuti

 28. Anyamatawo ndithu akulondola asiyeni apange dziko lawo sivutonso limenelo ngakhale malawiyo siyinali malawi koma kamudzu anayesetsa kulipanga dziko so let them do I’m proud of them

 29. kkkkkk osangowasiya bwanji ife tingotumiza nuclear kuwaphulisa bwanji…….kadziko kawoko ndikalanda coz tiwauza Malawi mwathu muno asayerekeze kulowa azilowa Ndi passport apo bii tikunyenyakkkkkk lol……………..z

 30. Amene akuyambitsa zimenezo ine ndikuti ndi boma la Dpp. Kuchokera 1964 -1994 komatso kuchokera 1994-2013 sindinamveko zinthu zonga izi.kodi Dr Banda,Dr Muluzi, Dr Bingu ndi Dr j Banda zoterezi never happan.why 2016 happen

 31. Do you mean we will be ruled by PRESIDENT of abroad. Tionera kuti apurezidenti akhala mbali iti. He would please own district or not.

 32. Kodi atumbuka anali olakwa ?aa
  Koma ngati sanali olakwa analeselanji ?
  Sono alomwewa akupanga zadzelu kupotsa zomwe amkaganiza atumbuka ? Malawai okoma wapita kuti
  Masiku otsiliza aliyese akufuna kulamulila akuona kulephela kwa dzake

 33. Kodi atumbuka anali olakwa ?aa
  Koma ngati sanali olakwa analeselanji ?
  Sono alomwewa akupanga zadzelu kupotsa zomwe amkaganiza atumbuka ? Malawai okoma wapita kuti
  Masiku otsiliza aliyese akufuna kulamulila akuona kulephela kwa dzake

 34. Kod mwasowa chitachita kumalawiko ,m’malo mothetsa njala mukupanga dziko lina for what?.chamba tikusuta ndi ife zikukubandan inu, chafukwa chan ,ndiyetu munyamule tyolo n mulanje mukapange ziko lanulo kutali kwambiri.Nawexo pitala muthalika osauza anthu zochita bwanji imeney ndi nzeru?ma mulanjeans n ma thyoloans muchenjele timenya nunu nkhondo chaka chino……

 35. Kod mwasowa chitachita kumalawiko ,m’malo mothetsa njala mukupanga dziko lina for what?.chamba tikusuta ndi ife zikukubandan inu, chafukwa chan ,ndiyetu munyamule tyolo n mulanje mukapange ziko lanulo kutali kwambiri.Nawexo pitala muthalika osauza anthu zochita bwanji imeney ndi nzeru?ma mulanjeans n ma thyoloans muchenjele timenya nunu nkhondo chaka chino……

 36. Kkkkk mtsogoleri wa gulu limeneli ndi wa nyaupe, akungofuna pochukira. Kwatsala nkupenga basi apite kaye ku mental ameneyo.

 37. Kkkkk mtsogoleri wa gulu limeneli ndi wa nyaupe, akungofuna pochukira. Kwatsala nkupenga basi apite kaye ku mental ameneyo.

 38. Yes ndimaganizo abwino kwa anthu amene sakuwona ubiwino wa bona kuti ndi chani.Komabe ndimaganizo abwino chifukwa dziko la Malawi palibe chomwe chikucitikakpo

 39. Yes ndimaganizo abwino kwa anthu amene sakuwona ubiwino wa bona kuti ndi chani.Komabe ndimaganizo abwino chifukwa dziko la Malawi palibe chomwe chikucitikakpo

 40. Anthuwa sakulakwa akufuna malo amakolo awo asamachite kusowa polima ngati iwowo ndialendo mdelalo, azunguwo ndi achikudawo mulendo ndindani pamenepa? Chilungamo chioneke akufuna malo amakolo awo.

 41. Anthuwa sakulakwa akufuna malo amakolo awo asamachite kusowa polima ngati iwowo ndialendo mdelalo, azunguwo ndi achikudawo mulendo ndindani pamenepa? Chilungamo chioneke akufuna malo amakolo awo.

 42. Anthuwa sakulakwa akufuna malo amakolo awo asamachite kusowa polima ngati iwowo ndialendo mdelalo, azunguwo ndi achikudawo mulendo ndindani pamenepa? Chilungamo chioneke akufuna malo amakolo awo.

 43. Anthuwa sakulakwa akufuna malo amakolo awo asamachite kusowa polima ngati iwowo ndialendo mdelalo, azunguwo ndi achikudawo mulendo ndindani pamenepa? Chilungamo chioneke akufuna malo amakolo awo.

 44. Akunena zoona come and witness your selves people have no land for cultivation komanso pokhala , anawapatsa malo mphiri la thyolo kuti azimangamo nyumba, that is un justifiable

 45. Akunena zoona come and witness your selves people have no land for cultivation komanso pokhala , anawapatsa malo mphiri la thyolo kuti azimangamo nyumba, that is un justifiable

 46. Akunena zoona come and witness your selves people have no land for cultivation komanso pokhala , anawapatsa malo mphiri la thyolo kuti azimangamo nyumba, that is un justifiable

 47. nonse mukulowetsa ndale pa nkhaniyi ndinu mbuli zothela2, kaya mwa2midwa ndi chakwera wanuyo munya muona, malogwa aminyu, munyepe mwanapwa. nde tipanga (south malawi muone/ south korea) tikhal ndi nation team ya2, tizikuchinyani muone iyaaaaa.

 48. nonse mukulowetsa ndale pa nkhaniyi ndinu mbuli zothela2, kaya mwa2midwa ndi chakwera wanuyo munya muona, malogwa aminyu, munyepe mwanapwa. nde tipanga (south malawi muone/ south korea) tikhal ndi nation team ya2, tizikuchinyani muone iyaaaaa.

 49. nonse mukulowetsa ndale pa nkhaniyi ndinu mbuli zothela2, kaya mwa2midwa ndi chakwera wanuyo munya muona, malogwa aminyu, munyepe mwanapwa. nde tipanga (south malawi muone/ south korea) tikhal ndi nation team ya2, tizikuchinyani muone iyaaaaa.

 50. mukati thyolo n mulanje not in malawi, where are they?? mozambique or zimbabwe….they are in malawi just as limbe is in blantyre but considered separately…mwatani kod!!!

 51. mukati thyolo n mulanje not in malawi, where are they?? mozambique or zimbabwe….they are in malawi just as limbe is in blantyre but considered separately…mwatani kod!!!

 52. mukati thyolo n mulanje not in malawi, where are they?? mozambique or zimbabwe….they are in malawi just as limbe is in blantyre but considered separately…mwatani kod!!!

 53. mlomwe ndiochuluka nzeru samalani.inu osadabwa olo kumpira alomwe sapezeka akutchuka ndi mpira why?amafuna akautenga mpira asapasire anzake mpaka akachinye yekha ndiye becarefull.

 54. mlomwe ndiochuluka nzeru samalani.inu osadabwa olo kumpira alomwe sapezeka akutchuka ndi mpira why?amafuna akautenga mpira asapasire anzake mpaka akachinye yekha ndiye becarefull.

 55. mlomwe ndiochuluka nzeru samalani.inu osadabwa olo kumpira alomwe sapezeka akutchuka ndi mpira why?amafuna akautenga mpira asapasire anzake mpaka akachinye yekha ndiye becarefull.

 56. ku meneko ndiye kubwera kwa bwino.dziko likamayenda mokondera kuti zisinthe zimayamba choncho. tiyeni nazo. kukanakhala kumpoto kapena pakati bwezi polis yamanga anthuwa kuti akuukira koma ayi kuli ziii. tengani maboma amenewo migodi ndi tea. muchita bwino mbendera mu mpatse kamlepo kaluwa akuthandizeni kupanga. yeee.

 57. ku meneko ndiye kubwera kwa bwino.dziko likamayenda mokondera kuti zisinthe zimayamba choncho. tiyeni nazo. kukanakhala kumpoto kapena pakati bwezi polis yamanga anthuwa kuti akuukira koma ayi kuli ziii. tengani maboma amenewo migodi ndi tea. muchita bwino mbendera mu mpatse kamlepo kaluwa akuthandizeni kupanga. yeee.

 58. ku meneko ndiye kubwera kwa bwino.dziko likamayenda mokondera kuti zisinthe zimayamba choncho. tiyeni nazo. kukanakhala kumpoto kapena pakati bwezi polis yamanga anthuwa kuti akuukira koma ayi kuli ziii. tengani maboma amenewo migodi ndi tea. muchita bwino mbendera mu mpatse kamlepo kaluwa akuthandizeni kupanga. yeee.

 59. Panopa zikutathauza, kuti tikamapita kumulanje ndi kuthyolo tizikhalat ndipassport.zopusa basi ngati mwakhuta maungu osakagona bwanji

 60. Giv me any concrete evidence beyond this i can believe otherwise i dnt c any sense what i see its no sense period, may i beg ur permission to sit down ?

 61. Giv me any concrete evidence beyond this i can believe otherwise i dnt c any sense what i see its no sense period, may i beg ur permission to sit down ?

 62. Komaso nzeru za mu tea nde kaya basi. Bola inu president muli naye kale koma nde kaya ife ndalama tikazitenga kuti zopangira chisankho. Tione fans kukana kwawo kkkkkk

 63. Komaso nzeru za mu tea nde kaya basi. Bola inu president muli naye kale koma nde kaya ife ndalama tikazitenga kuti zopangira chisankho. Tione fans kukana kwawo kkkkkk

 64. Kusamvetsetsa ndili bvuto la amalawi amafuna kulankhula pazinthu zomwe sanazimvetsetse kuti ndi chain,mufunse mumve kuti Anthu aku Mulanje ndi Thyolo akulilila chiyani musanatukwane.

 65. Kusamvetsetsa ndili bvuto la amalawi amafuna kulankhula pazinthu zomwe sanazimvetsetse kuti ndi chain,mufunse mumve kuti Anthu aku Mulanje ndi Thyolo akulilila chiyani musanatukwane.

 66. even if mulanje n thyolo can be a country does it mean they have solved the matter? n if the govt says akambilana nawo agululi does it mean that ths group has much power than govt? angokhala pasi wit the hlp 4m thdd gvt n solve the matter,

 67. Pamenepo ine ndikuti akupanga bwino kamba kakuti Azungu kuno sikwawo akhala bwanji ndi malo akulu kopasa eni thaka? tisamangoti malawi ndife aphawi uku zinthu zikuonongeka.chitsanzo anthu akukasungu ndimadela ena ozungulila anathamangitsa azungu a #genorel #farming ndiye akumulanjenso achoke basi.

 68. Pamenepo ine ndikuti akupanga bwino kamba kakuti Azungu kuno sikwawo akhala bwanji ndi malo akulu kopasa eni thaka? tisamangoti malawi ndife aphawi uku zinthu zikuonongeka.chitsanzo anthu akukasungu ndimadela ena ozungulila anathamangitsa azungu a #genorel #farming ndiye akumulanjenso achoke basi.

 69. Tisapusitsidwepo ape. Likanati likhale gulu chabe bwenzi anthuwa ali mndende pano, ena mwa iwo atasowa kumene. Kodi Peter Mutharika siwakuTyolo? Ndiye gululi sakulidziwa bwino? Apa zikuwonekerathu kuti a president athu is behind this move

 70. Tisapusitsidwepo ape. Likanati likhale gulu chabe bwenzi anthuwa ali mndende pano, ena mwa iwo atasowa kumene. Kodi Peter Mutharika siwakuTyolo? Ndiye gululi sakulidziwa bwino? Apa zikuwonekerathu kuti a president athu is behind this move

 71. Comment loading……? Ya loader kma alomwe ximuzatheka tawapaxeni mulanje ndi thyolo inu kma tikatengeko magesi ndi madzi anthu ma filling station kungonenapo zochepa zomwe anapaxidwa ndi boma lamalawi then aike maboarder awo ndikuyamba kuma owoda zithu ziko lakunja kwao la malawi ngati sugar ndi zina zamafactory xangakwanixe inu anthu oxapita kuxool amenewa apaxeni timaboma tawoto akula atha aziona

 72. Comment loading……? Ya loader kma alomwe ximuzatheka tawapaxeni mulanje ndi thyolo inu kma tikatengeko magesi ndi madzi anthu ma filling station kungonenapo zochepa zomwe anapaxidwa ndi boma lamalawi then aike maboarder awo ndikuyamba kuma owoda zithu ziko lakunja kwao la malawi ngati sugar ndi zina zamafactory xangakwanixe inu anthu oxapita kuxool amenewa apaxeni timaboma tawoto akula atha aziona

 73. Ithink national anthem yakumeneko ikhala ya hip hop kkkk Capital city Ndata farm shame to my Malawi…Afuna akyime uPresident kwawo ku United States of Thyolo 2019 vice president Winiko….pa flag pazakhala makasu.

 74. Ithink national anthem yakumeneko ikhala ya hip hop kkkk Capital city Ndata farm shame to my Malawi…Afuna akyime uPresident kwawo ku United States of Thyolo 2019 vice president Winiko….pa flag pazakhala makasu.

 75. wandale is paranoyer, stupid and foolish man thus why he is doing all that nonsense .to hell with that…galu iwe

 76. Kkkkkkkk zachamba baxi,nde chilankhulo azilankhula chiti,ndalama azigwiritsa iti?kma dziko la Malawi sikutha uku lero timve zasatanik achina,Bushri ai ,ameneyo ndmunthu wa Mulungu,,,kulaniwa basi

 77. Kkkkkkkk zachamba baxi,nde chilankhulo azilankhula chiti,ndalama azigwiritsa iti?kma dziko la Malawi sikutha uku lero timve zasatanik achina,Bushri ai ,ameneyo ndmunthu wa Mulungu,,,kulaniwa basi

 78. Nagama WaGama Kettie Tabitha Shallon Ziyaya Chibwanah Chikumbutso Yewsuf Margret B Kakwela Leonard Gombachika Narcia Lorianne Luse Ida Tewesa Daniel Mzati Mwai Kumwenda Mwabi Netballer Gift Chinsakasa Gertrude Madinga Love Msuku Kalulu Eckless

 79. Ayi Wakula Ndiumbuli Kodi Akapanga Dziko Lawo Akuganiza Kuti Mavuto Awo Atha Komatu Asachite Zinthu Zongofuna Kuchuka Komanso Aganizire Kuti Ndi Boma Lomwero Limene Analivotera Okha

 80. Ayi Wakula Ndiumbuli Kodi Akapanga Dziko Lawo Akuganiza Kuti Mavuto Awo Atha Komatu Asachite Zinthu Zongofuna Kuchuka Komanso Aganizire Kuti Ndi Boma Lomwero Limene Analivotera Okha

 81. Ayi Wakula Ndiumbuli Kodi Akapanga Dziko Lawo Akuganiza Kuti Mavuto Awo Atha Komatu Asachite Zinthu Zongofuna Kuchuka Komanso Aganizire Kuti Ndi Boma Lomwero Limene Analivotera Okha

 82. Chithandizo adzachipeza kuti ngati dziko? Azigalira madonnarz omwewa ofokawa ? Ngati tate wafuko lino anayenera kukhazikitsa bata ngati iyeyo akungoyang’ana akutanthauza chani?

 83. Kkkkkk Nzosekesa Anthuwa Akumapanga Maganizo Awo Ngati Asogoleli Osati Anthu Eni Ai, Komanso Ngati Akufuna Maudindo Njila Zake Sizimenezi Ai. Mulanje Ndi Thyolo Sangakhale Oyima Pa Okha Ai Pali Zambili Zofunika Kuti Ayime Pawokha.

 84. Chodabwitsa mchoti a President amachokeranso Ku Thyolo,iwowa nde akuti bwanji? Dziwani kuti utsi siungafuke popanda Moto. We got military bwanji aku mulanje ndi Thyolo sakuopa nkhondo cz they are labels.

 85. Chodabwitsa mchoti a President amachokeranso Ku Thyolo,iwowa nde akuti bwanji? Dziwani kuti utsi siungafuke popanda Moto. We got military bwanji aku mulanje ndi Thyolo sakuopa nkhondo cz they are labels.

 86. Chodabwitsa mchoti a President amachokeranso Ku Thyolo,iwowa nde akuti bwanji? Dziwani kuti utsi siungafuke popanda Moto. We got military bwanji aku mulanje ndi Thyolo sakuopa nkhondo cz they are labels.

 87. Chodabwitsa mchoti a President amachokeranso Ku Thyolo,iwowa nde akuti bwanji? Dziwani kuti utsi siungafuke popanda Moto. We got military bwanji aku mulanje ndi Thyolo sakuopa nkhondo cz they are labels.

 88. Aliyense kaya ndi msogoleri wadziko yemwe kwawo ndi ku Thyole he/ she must be deported with immediate effect.

  So that we can see, How best we can restructure our country Malawi without Thyolo and Mulanje citizens.

  Either our country needs Re-Elections of State president.

 89. Aliyense kaya ndi msogoleri wadziko yemwe kwawo ndi ku Thyole he/ she must be deported with immediate effect.

  So that we can see, How best we can restructure our country Malawi without Thyolo and Mulanje citizens.

  Either our country needs Re-Elections of State president.

 90. Aliyense kaya ndi msogoleri wadziko yemwe kwawo ndi ku Thyole he/ she must be deported with immediate effect.

  So that we can see, How best we can restructure our country Malawi without Thyolo and Mulanje citizens.

  Either our country needs Re-Elections of State president.

 91. Aliyense kaya ndi msogoleri wadziko yemwe kwawo ndi ku Thyole he/ she must be deported with immediate effect.

  So that we can see, How best we can restructure our country Malawi without Thyolo and Mulanje citizens.

  Either our country needs Re-Elections of State president.

 92. Nothing wrong to do so if the government is doin nothin brother coz even south africa thr is a country for africans only so keep it up and c wht will happen in future

 93. Nothing wrong to do so if the government is doin nothin brother coz even south africa thr is a country for africans only so keep it up and c wht will happen in future

 94. Ok then malawi alibe presdent as of nw sichoncho pakuti ankolowo ngaku thyolo .oooohh ndichifukwa chake siku lija anati ziko lamalawi ndilafodya ndipo zafodya mkupangazo pitirizani pakuti zimabweresa ndalama lero izi zaululika

 95. Ok then malawi alibe presdent as of nw sichoncho pakuti ankolowo ngaku thyolo .oooohh ndichifukwa chake siku lija anati ziko lamalawi ndilafodya ndipo zafodya mkupangazo pitirizani pakuti zimabweresa ndalama lero izi zaululika

 96. Leave the white man alone to continue growing tea in mulanje and thyolo coz they are providing jobs to the people of these two districts and they are paying tax to the government also.Peter Mutharika must not do what these people demanding him to do coz they gonna make him stupid very soon.However, Malawi is a small country how can it be devided into many denominations?.How stupid are the lomwe people?.Do they have a living spirit or dead one?.Do they want to make all Malawians stupid in the eyes of the wolrd?.With an immediate effect,this MUST STOP!!!!!.

 97. My psychic readings focus on positive thinking & positive change. It may assist in bringing clarity to a confusing situation, help you prepare for the future in a more focused way and may empower you with positive potential. If you are seeking spiritual guidance with your relationship, marriage, love, family, career, money, health matters, or life’s daily issues, my insightful accurate psychic reading will help you answer the questions that weigh heavily on your mind. I would love to assist you with making the best decisions for your Future. No matter where you live I can help you.Call +27738951830 MUNIL SALEH, I do Whats-App, Face book/munilsaleh, Phone and personal readings.

 98. [READ MY STORY. ON HOW I GOT MY HIV CURED].
  Truthfully, i was tested HIV + positive for the past 8 years. I keep on managing the drugs i usually purchase from the health care agency to keep me healthy and strengthen, i tried all i can to make this disease leave me alone, but unfortunately, it keep on eating up my life. So last Two Months i came in contact with a lively article on the internet on how this Powerful Herb Healer get her well and healed. So as a patient i knew this will took my life one day, and i need to live with other friends and relatives too. So i copied out the Dr Collins the herbal healer’s contact and I contacted him immediately, in a little while he mail me back that i was welcome to his Herbal Home whereby all what i seek for are granted. I was please at that time. And i continue with him, he took some few details from me and told me that he shall get back to me as soon as he is through with my work. I was very happy as heard that from him, as i was just coming from my friends house, Dr Collins called me to go for checkup in the hospital and see his marvelous work that it is now HIV negative, i was very glad to hear that from him, so quickly rush down to the nearest hospital to found out, only to hear from my hospital doctor called Browning Lewis that i am now HIV NEGATIVE. I jump up at him with the a test note, he ask me how does it happen and i reside to him all i went through with Dr Collins. I am now glad, so i am a gentle type of person that need to share this testimonies to everyone who seek for healing, because once you get calm and quiet, so the disease get to finish your life off. So i will advice you contact him today for your healing at the above details: Email ID: [email protected] or you can also add him up on whataspp +2349036950737. CONTACT HIM NOW TO SAVE YOUR LIFE AND DOCTOR ALSO CURE ALL KIND OF DISEASE AND SICKNESS: [email protected] AS HE IS SO POWERFUL AND HELPFUL TO ALL THAT HAVE THIS SICKNESS.

 99. kubeleka kwambiri ngati makoswe lero ndizo malo avuta paja mumati muziswana kwambiri kuti muzitilamulira ,kuswana ngati ajoni white kaya,trison ija ndiimeneyi awatione ngati angamangidwe kapena poti mngakumudzi,komaso kadzikoko azilamula ndindani?

 100. Kakakakakakakaka! . so who said ds . they mean ds two district they will bi part ov Mozambique or just Thyolomulanje country..kkkkkkkkkkkk!

 101. The problem is these have consulted the help from government but the government did not help them so because of angry the have made that decision if the government acted on the issue it could been another case….all in all the decision is bad but our president should be aware of peoples problems and do something otherwise leaders are not helpful in the country……..

 102. Malawi 24 please post issues after you have really proved the situation not because you want to fill the blank pages.Thyolo is aMalawian district & so is Mulanje.

 103. Malawi 24 please post issues after you have really proved the situation not because you want to fill the blank pages.Thyolo is aMalawian district & so is Mulanje.

 104. Uku ndikutsowa nzeru bwanji osapita kunyumba yamalamulo konko mwaunyinji kukamuza peter ngati atakane kulilamulo loti ngati amene akuyendetsa dziko inu anthu sakukuthandidzani kumanani ngati anthu amene munamuyika pamupando namuchosa nkusankha winanso koma ukufuna kutelo ndiye sikusova mavuto koma kupepula dziko komanso kuzionetsa umbuli

 105. Uku ndikutsowa nzeru bwanji osapita kunyumba yamalamulo konko mwaunyinji kukamuza peter ngati atakane kulilamulo loti ngati amene akuyendetsa dziko inu anthu sakukuthandidzani kumanani ngati anthu amene munamuyika pamupando namuchosa nkusankha winanso koma ukufuna kutelo ndiye sikusova mavuto koma kupepula dziko komanso kuzionetsa umbuli

 106. Kuukira kumeneko, ndiye poti HE ndi wa kumeneko amutenge kwinaku tisankhenso wathu. Akanakhala a zigawo zinazi pano police itawatsekera kalex2

 107. Kuukira kumeneko, ndiye poti HE ndi wa kumeneko amutenge kwinaku tisankhenso wathu. Akanakhala a zigawo zinazi pano police itawatsekera kalex2

 108. Akukhuta ndikuona akulimbana ndi nkhani zopanda pakezo akanakhala ena bwenzi akulimbana ndi njala yi osati nkhani xopusa mulanje ingakhale dziko umbuli chani kusowa zochita etiii

 109. Akukhuta ndikuona akulimbana ndi nkhani zopanda pakezo akanakhala ena bwenzi akulimbana ndi njala yi osati nkhani xopusa mulanje ingakhale dziko umbuli chani kusowa zochita etiii

 110. Lawless Mtonja Degryt Cowmbeeh, Kamwendo Steve, Aaron Kalanje, Tionge Chigwenembe, Wa Kassm Firstbon Innocent Ndakhala ndikukuuzan nthawi yaitali kuti ine siwakumalawi inu makani,,,ine ndiwakunja

 111. Lawless Mtonja Degryt Cowmbeeh, Kamwendo Steve, Aaron Kalanje, Tionge Chigwenembe, Wa Kassm Firstbon Innocent Ndakhala ndikukuuzan nthawi yaitali kuti ine siwakumalawi inu makani,,,ine ndiwakunja

 112. Now land belong to native black in The Native Royal Supreme Governing Coucil presided over by Native Superior Majesties Charismatic Eldets and their pple.Tea Estate Owners be payind rents to these native authority.Rental arrears be calculated since they were established.

  pub by GLOBAL ORIGINAL HERITAGE MINISTRIES
  by Traditionalist BishopBishop G Mlalazi.

 113. Now land belong to native black in The Native Royal Supreme Governing Coucil presided over by Native Superior Majesties Charismatic Eldets and their pple.Tea Estate Owners be payind rents to these native authority.Rental arrears be calculated since they were established.

  pub by GLOBAL ORIGINAL HERITAGE MINISTRIES
  by Traditionalist BishopBishop G Mlalazi.

 114. The Move Is An Unprecedented Pamenepa Ndekt Ndalowa Politics..Thoz Pple Claiming The Independence Of Thiz Districts Are Ignorant Dey Dn’t Know How It Takes For That To Happen And Sizichitika M.Ne Zililimu……..Peter Wake Uti Amene Angalore Zimenez Kt Ztheke…..Let’s Pray Hard……

 115. The Move Is An Unprecedented Pamenepa Ndekt Ndalowa Politics..Thoz Pple Claiming The Independence Of Thiz Districts Are Ignorant Dey Dn’t Know How It Takes For That To Happen And Sizichitika M.Ne Zililimu……..Peter Wake Uti Amene Angalore Zimenez Kt Ztheke…..Let’s Pray Hard……

 116. Kuyambila nthawi ya Kamuzu nthawi ya Bakili kunali ku Malawi pano anene kuti si ku malawi zitheka bwanji, anthuwa asatiphimbe m,maso ife ayi ndizopangana akufuna Peter akazachoka m,boma akakhazikitse kadziko kake tisapusitsike a malawi anthuwa akudziwa chomwe akuchita ndipo ndizopangana

 117. Kuyambila nthawi ya Kamuzu nthawi ya Bakili kunali ku Malawi pano anene kuti si ku malawi zitheka bwanji, anthuwa asatiphimbe m,maso ife ayi ndizopangana akufuna Peter akazachoka m,boma akakhazikitse kadziko kake tisapusitsike a malawi anthuwa akudziwa chomwe akuchita ndipo ndizopangana

 118. Peter munthalika tumiza asilikali ako kumeneko imeneyo akuyiyambayo ndi boko malawi ofunika kusamala dziko lako asakulande wamva.

 119. ndizopusa kwambiri zomwe akupanga iwo angalowese ndalama zingati kuboma la malawi.anthuwo azipatula okha kuti si amalawi alibwino koma atisiyire thyolo ndi mlanjeyo anthu amenewo mitu yawo siyenda bwino

 120. First take all those behind this to a doctor something somewhere is wrong secondly deport him and his family back to mulanje or Thyolo akapeze Kaye viza passport and a working permit for him to be here jkkkkk

 121. Mwachita bwino Chifukwa Mulanje ndi Thyolo anthu m’mabelekana kwambiri ndinu amene mukupangitsa kuti chiwerengelo cha dziko lino chikwele kwambiri. half ya chiwerengero cha dziko lino anthu ake ndi a ku Thyolo ndi mulanje, ndiye m’mene mwaimila panokhamu population yathu pano yafika 8.5million. mwachita bwino mudzionere nokha ndi kuberekana ngati nkhumba kwanuko!

 122. Ngatimwachokamlawi mwachitabwino mutengenyangwitazanu ndi presdent wanuwamkulupakamwayo petar muzipitakwanuku moqambiq palibekudula maliledzikomudalipeza bolamwavomela kutimwakanikakulamulila bwezelani ufumukwaenidziko( ochewa)

 123. Ndizosatheka kuti maboma awiliwa akhala oziyimila paokha, zuto lomwe ndikuliwonapo ine ndilakuti; Boma lomwe likulamula panoli lili ndivuto losathandiza anthu mwachangu, m’alo mwake anthu akumataya chikhulupililo mwa iwo, ngati pali wina yemwe ali ali m’boma likutilamulali pano, akafotokozele azinzakewo kuti Amalawi ambili akuwadandawula chifukwa cholekelela anthu awo akuvutika

 124. Something wrong upstairs.Anthu opanda kwawo amatero .sakhazikika kafunseni anzanu akuzimbabwe.Dziko lomwe it was called abread basket.now in shambles even in one year simungathe ku salira ka one hector.kakumbeni mbewa muzigulitsa kwa vumbweko You will be able to put madeya on ur table find something possitive to tell dont destroy learn to build.cry the beloved lomwe and khokholaz wake up amanganja.

 125. Amalawi titsegukeno maso chomwetu akufuna Awandalewo ndi ndalama akudziwa kuti pokha boma langoti akambilana nawo ndichi Banzi chimenecho ndinawamva ineyo mafumu onse amaboma awiliwa akuyankhapo pankhani imeneyi ndipo adakanitsitsa kuti sangalore kupanga zimenezi tisanamizane apa Amalawi chomwe akufuna a Vicent Wandalewa ndi Banzi.

 126. Those are WEAK declarations! Weak indeed! Where there is problem,we find out solution. That is not solution. It is emotional reaction. Reacting out of emotions cannot solve the problem

 127. Ok ku lowershire kukhalanso dziko posachedwapa pulezdent mbuya chakuamba,komanso boma ndlokondera tinamva atumbuka akufuna dziko kumpoto koma boma lidasokosa kwanyoza ndkudzudzula dr joyce banda kut nd omwe amayambisa koma apa boma langot duu olo kudzudzula aliense kod zimenez coz iwo nd alomwe.tizitero mmalaw muno.

 128. musasankheso presdent tikupatsani peter yemweyu vice kaliyati ma mp muli nawo kale achina winiko manganya ndi azinzawo musatitopese iyaaaaa likhala dziko lambuli zambiritu coz alomwe sukulu alibe nayo ntchito

 129. Mwanena kuti akulimbirana malire, ndiye akakhala paokha mikangano yawo izatha?. Already anthu amenewo ali divided ndiye i don’t think akakhala independent azagwirizana. Together we stand divided we fall. No development, poor leadership.

 130. Wins amafunsa kuti kodi uyo ali pa chithunziyo ndiye president wao? Eee atha kukhala. Watani? Inu simumationa? Ndi handsome ameneyo kkkkk . Koma izi ndiye zopepera zopepera 100%. Chi big fish chingoyangana chiri tiye nazoni anyamata. Kufuna Chani? Anthu avutike? Za chamba basi

 131. Atengenso peter wawoyi akuwalimbitsa mtima izi anakalakhula mzomera gwira kuti northern tatulukamo malawi bwenzi bwampini mutharika atatuma apolice nd anyamata azikwanje kuzakhapa mzomera koma poti nd mulakho eeeh ikakhaladi pa uta silasika

 132. This part of madness how can mulanje n thyolo became a country by its on what do they have to become a Republic more over if u chase the white people u will be like Zimbabwe. Course tea is only the source of income we have

 133. This part of madness how can mulanje n thyolo became a country by its on what do they have to become a Republic more over if u chase the white people u will be like Zimbabwe. Course tea is only the source of income we have

 134. vuto ndi nsogoleri wadziko iye wagulisa maboma awiri wa koma sakufuna kuonekera kuno kumalawi azungu sikwao akhala bwanji ndi mphanvu zogawa ziko nao anthu andziko muno angoyang’anira zimenezi amalawi tulo

 135. vuto ndi nsogoleri wadziko iye wagulisa maboma awiri wa koma sakufuna kuonekera kuno kumalawi azungu sikwao akhala bwanji ndi mphanvu zogawa ziko nao anthu andziko muno angoyang’anira zimenezi amalawi tulo

 136. Mubwere Ku Ekwenden Muzawone Zomwe Azungu Omwe Mugabe Anawathamangitsa Ku Zimbabwe Achita Kuno. Atsegula Ma Hectres A Makademia Pano Ntchito Yili Mkati. Malo Oti Amangozalapo Ma Blue Gumo Pano Zosangalatsa. A Thyolo Ndi Mulanje Cool Down. Palibe Chomwe Mungachite Bola Akanakhala Mpoto Chifukwa Kuli Mgodi , Northern Collidor , Ulimi, Etc. Ndiyesa Muli Ndi Peter Kumeneko?

 137. Mubwere Ku Ekwenden Muzawone Zomwe Azungu Omwe Mugabe Anawathamangitsa Ku Zimbabwe Achita Kuno. Atsegula Ma Hectres A Makademia Pano Ntchito Yili Mkati. Malo Oti Amangozalapo Ma Blue Gumo Pano Zosangalatsa. A Thyolo Ndi Mulanje Cool Down. Palibe Chomwe Mungachite Bola Akanakhala Mpoto Chifukwa Kuli Mgodi , Northern Collidor , Ulimi, Etc. Ndiyesa Muli Ndi Peter Kumeneko?

 138. Sanalakwitse koma kuti apanga mothamanga.Anthu aku Mangochi nawo anayamba zimenezi miyezi iwiri yapitayi koma akuyamba ndi Constitution ndi zina kaye,kenako adzalengeza kutuluka kwawo Malawi nkukhala the Peoples Republic of Mangochi.

 139. Sanalakwitse koma kuti apanga mothamanga.Anthu aku Mangochi nawo anayamba zimenezi miyezi iwiri yapitayi koma akuyamba ndi Constitution ndi zina kaye,kenako adzalengeza kutuluka kwawo Malawi nkukhala the Peoples Republic of Mangochi.

 140. Kwa amene mudachoka m’ziko muno nde kuti mudaona kuti malawi wanunkha,ngati ngati simukuvomeleza nde kuti ife timasuke,,,,keep quite!!! 2. Maboma awiriwa TY and MJ ndimaboma anthaka yabwino and blessed,,,atakhala kuti eni nthaka akulima ,,,no njala,more economic income., let me ask u, do you giv 1st grade use of the land to de whites than de owner(real malawians)? What are they benefiting out of it? Nde azivutikabe mpaka liti? 3. Mutharika siwaku-Thyolo,trust me, adakakhala wa kumeneko nkhani iyi adakathandizapo kale. Avomeleze ,,,United states of Thyolo and Mulanje bax. Ife tiwathamangisa azunguwo , malowo tidzilima bax… Note: have passport if u want to visit ,United states of Thyolo and Mulanje.

 141. Kwa amene mudachoka m’ziko muno nde kuti mudaona kuti malawi wanunkha,ngati ngati simukuvomeleza nde kuti ife timasuke,,,,keep quite!!! 2. Maboma awiriwa TY and MJ ndimaboma anthaka yabwino and blessed,,,atakhala kuti eni nthaka akulima ,,,no njala,more economic income., let me ask u, do you giv 1st grade use of the land to de whites than de owner(real malawians)? What are they benefiting out of it? Nde azivutikabe mpaka liti? 3. Mutharika siwaku-Thyolo,trust me, adakakhala wa kumeneko nkhani iyi adakathandizapo kale. Avomeleze ,,,United states of Thyolo and Mulanje bax. Ife tiwathamangisa azunguwo , malowo tidzilima bax… Note: have passport if u want to visit ,United states of Thyolo and Mulanje.

 142. Uku ndikuukira boma(treason)osangowamanga oyambitsawo bwanji?Koma akanakhala Kabwila ndi Chakwantha za pa whatsapp eti?This is part of insecurity.Tidzalanditsa dziko ndithu!

 143. Uku ndikuukira boma(treason)osangowamanga oyambitsawo bwanji?Koma akanakhala Kabwila ndi Chakwantha za pa whatsapp eti?This is part of insecurity.Tidzalanditsa dziko ndithu!

 144. Pamenepa tinenepo mosapsatira.Titati tipite ku thyolo nd mulanje tikadabwa ndipo tikazifunsa kuti, kodi anthu amakhala kuti?Anhu oawe sianthu obwela apanikizidawa kwambiri malo onse ofewa azungu anatenga.Mr president kwaonso ndikomweko koma ndima district omvesa cison.Ine maganizo anga ndioti ngat boma silithandizapo apange zimenezo athana ndiimeneyi ayambenso ija yanseu wa thyolo to nsanje chifukwa ngati kuli malo othandizanso ndimaboma awiriwa.

 145. Pamenepa tinenepo mosapsatira.Titati tipite ku thyolo nd mulanje tikadabwa ndipo tikazifunsa kuti, kodi anthu amakhala kuti?Anhu oawe sianthu obwela apanikizidawa kwambiri malo onse ofewa azungu anatenga.Mr president kwaonso ndikomweko koma ndima district omvesa cison.Ine maganizo anga ndioti ngat boma silithandizapo apange zimenezo athana ndiimeneyi ayambenso ija yanseu wa thyolo to nsanje chifukwa ngati kuli malo othandizanso ndimaboma awiriwa.

 146. This is irritating of demeaning the so called Wandale and his fellas have exergalated,as a matter of fact they are all nicomples, who voted for them? Badadash!!

 147. This is irritating of demeaning the so called Wandale and his fellas have exergalated,as a matter of fact they are all nicomples, who voted for them? Badadash!!

 148. kkkkkkk akhuta eti? nde dziko lawolo dzina lake likhala chani? penapake sukulu ndiyofunika guys. iwowo akanangopempha chithandizo bas osat kulimbikira mtunda opanda madzi

 149. masiku omaliza basi ntundu ndi ntundu udzaukirana ana adzakhala osavepa akuwabala apa thyolo ndi mulanje sakuvera Malawi ngati kholo lawo osadandaula koma dziwani kuti ndi nthawi

 150. Maboma awiri akhale dziko kkk malawi chamba chafikapo ndithu dziko la serbia linapatukalo nd mayiko olemera nanga mulanje ndi Thyolo kuli chani

 151. Azungu omwe anatenga minda anali akhristu kodi chikhristu kumeneko chithaso? Livinstone mpongozi wache ndiye anali patsogolo

 152. Kkkkkk Malawi akulamulira (President) ndi Mlomwe, anthu aku Mulanje ndi Thyolo ndi a Lomweso, athana okha. Akadakhala olamulira ndi Mtumbuka kapena Mchewa tikadanena kuti anthu sakumufuna,koma apapo akudziwana okha. Thumba latambe, Tambeyo amamasula yekha. Zisiyeni zikulire limodzi, zidzaoneka pokolora. Ku suta tea, its more harzadus than chamba, mind u. On the other hand, this is treason, apanga declare bwanji maboma awo kukhala dziko palokha? M’malo moti muwakwidzinge mungoonerera koma ena akanena zakusowa kwa chimanga m’ma admarc kenako mpaka ku cell, the same shud happen to the ring leaders of this new nation they have declared.

 153. kkkk ngati boma lingawalole..inenso ndikuuyamba wakwathu ku ntcheu ndikaimile u president..isaa nanga ngati akumukana abale ake nde kulibuanji ife hahahahaha tangoelekezani kulolo muone

 154. sindidziwa kusiyana kwa a lomwe ndi atumbuka kudzikonda too much, kungotenga akasinja akagwile ntchito malo amenewa

 155. A2 aukirapo dziko lino tzfukwa take tochepa nkuwaonetsa mbona wona/kiyama koma Wandale #rebelion yake ndichilendo even file yotere mu Archieve mulibe koma chodabwitsa boma likumusisita ngati mphaka…..

 156. Poti alengeza kale kuti ndi dziko sindikukaika, alinso ndizida zankhondo, gulu lankhondo ndinso la apolisi; ndiye ife sitikambirana nawo amenewa, wakhungu amati ndikugenda amakhala ataponda mwala. Ife tisankha wathu president alipoyu akufunika deportation.

 157. tawauzeni a wandale atigaile chamba akusutacho kuno ku mangangochi mwina ifeso tingamaone kukula kwa bomali kuti tipange dziko lathu…!!!!

 158. Lhomwe Peoples Republic = LPR President APM Vice WINIKO NYO Speaker AKWENI PBK Cabinet very lean but vibrant to be sworn in at NDATA STADIUM ON SUNDAY. Chief justice MPWARAHA sc to preside the ceremony at noon. Alhomwe ooyyee WOYHEEEE 😎

 159. Vuto Ndirot Boma Likumasiya Amwenye Azungu Ndimachina Kt Azizuza Amalawi, Kuli Azungu Ku Kusika Wafodya Akungogura Mmene Angafunire Koma Uyu Bitara Akungot Ndikamba Nawo Koma No Change Ndzowawa.

 160. Zitsanzo zomwe atengera za Kosovozo ndi zausiru. Alipo wabisala kumbuyo kwake yemwe afuna kuyambitsa nkhondo ku Malawi. Mudzandivomereza kutsogolo kuno. Dziko lina lililonse kuli azungu olanda malo, munamvapo kuti mdela la dzikolo lagalukila dziko?
  Ku Zimbabwe anangowalanda mindayo, lero akuilepheranso, komanso akuwapatsa chipepeso azungu olandidwa mindao. Kuli chiyani ku Thyolo? Vuto ndi loti alomwe amaberekana kwambiri. Ndiye akuona ngati kulanda minda ndi kupanga zogalukira kuwathandiza. Ndi nzeru zopusa chabe.

 161. Could u pliz stop playing silly jokes wth Malawi, be serious display a sense of patriotism to ur country. Does all need someone to civic educate you? really?

 162. Mumene akuwonekela uyu alipachithunziyu angakhale president mnthi maso atalefuka kale ndi chamba agalu awa mzifunsana msanatengele nkhani pabwalo

 163. kagulu aka ndi ka anthu otsuta kanundu okha okha nzowona maboma awiri kugwilizana kukha dziko? ngati dzinthu dzikuvuta mzikolathu la Malawi timaboma tiwilit titizapange chani, msayipitse mbiri ya malawi anthu openga inu naloso bomali poti ma president anthu akusankha ngati zilizaufumu dzowona dziko kulamulidwa ndima brothers okha okha president akana khala kuti sakuchokela ku thyolo bwezi zitsiruzi atazimanga kale

 164. ndi nkhani yayitali kungoti anthu ambili ku Malawi kuno ndi mbuli “Malo a mulanje ndi tholo ali manja mwa adzungu omwe anawatenga pa rent ndiye kuli ngongole ya mamiliyoni yoti anzungu apere kwa mwini malo ndiye ngati munthu wakanika kupereka rent amachotsedwa pa malo PITILIZANI NDINU ANTHU ANZERU***