Nomads send strong warning to Bullets

Advertisement
Mighty Wanderers.
Mighty Wanderers.
Nomads Japanese midfielder Genki Nakamura races with a Max player.

Mighty Be Forward Wanderers have today sent a strong warning to Nyasa Big Bullets ahead of next week’s Chifundo Cup after beating Max Bullets 1-0 at Kamuzu Stadium on Sunday afternoon.

Rafique Mussa scored the only goal of the match in the dying minutes of the second half to set Wanderers ready for next weekend’s Chifundo Cup which will be played on 9th of April, 2016.

Jabulani Linje and Peter Wadabwa came closer on several occasions but they all lacked the scoring composure in front of the Max Bullets goal in the first half until the last whistle of the first half.

In the opening minutes of the second half on loan Mighty Wanderers strikers Precious Msosa put Max Bullets ahead but his goal was disallowed by the referee for an offside . Mighty wanderers mentor introduced Mussa, Jimmy Zakazaka into the Nomads squad as he was looking for the Nomads goal. Both Wanderers and Max Bullets played entertaining football in the second half as they were all looking for an opening goal of the match but they all failed to find the back of the net.

As the game was looking to be settling for a draw, the nomads found a freekick outside the box after Genki Nakamula was fouled and Patrick Gunde stepped up for the challenge. Gunde fired his shot inside the Bullets 18 yard box and it met the strong head of Mussa who headed it in to make it 1-0 in favour of the Nomads and the game ended 1 nil.

Advertisement

275 Comments

 1. Kodi iwe nebe ukuganiza zoti ukadusa pa bb akamuna muiwale tipita tikathana nanu ndinu ana muli ndi chani mesa mukufuna kungothesa sogoro lake la jafa bs nayexo jafa opuxa zedi noma ndi team yopita aaaaaaa osazifusa bwa chaka chino league titenga palibe tikumuona mmasomu.

 2. koma penapake a noma muzikhala serious zomenya zake zimenezija nkumagundika kuti mukupeleka strong warning? ana aja mwawzbela chigoli and ref anali mbali yanu do u think ya bullets zikakhalanso chonchija?

 3. Koma inu anoma bwanji mukulimbana ndi National Team? Ngakhale mantha mulibe? Aaaaa tadikirani inu panado mupatsidwa ndipo matenda anu ayankhula zopusawo muchira. NBB,,,,, moto uwo waotcha nyerere zonse zatheratu psiti kkkkkkkkkkkkkkkk

 4. Paja pano tilibe negative points neba uziona watengelathu tuzikho tako. MANOMA woyeeeeee!!!!!!!!

 5. kupusa kwaonekera k team y nm k chgol kamdz tmnso yakdvisn nd drow imney nyns nakamla aaa bola matchn musa manyenje ndmtnda ina

 6. Iwenso olemba mulilimozi nanga mpaka strong warning yake kunena imeneyo asee.inu ndiakazi athu ana ngati amwene mpaka 1 zero paja alum a much into ran I ndimadefender

 7. Supporter weni weni wa Norma nkhaniyi yamukulisa mutu kkkkkkkkkk nkhani yochititsa manyazi iyi Norma ililadi season ino ndithu

 8. Umbuli wake umenewu nchifukwa ndinasuthako ku Malawi kkkkkkk 1-0 ikakhale strong warning zoona eti???? Team yakenso Max Bullets hahahahaha neba uziona zonyadila zake.

 9. pa mateam onse amu super league ndiye kuti noma imaopa bullets eti?kochi wanu akudandaula kuti simunasewere bwino’koma inu phokoso basi.kkkkk koma nyerereeee nzeru palibe.mukonzekenso kupereka six points ku bullets ngati last season

 10. Ayi ! Mukunama ANOMA Mateamwa Angofanana Maina Oti Bullets But Mind U Inayi Ndi BIG BULLETS.

 11. Tikugwebani kumene, mukuopa chani? season mudziwanso ana opanda khalidwe inu kuzolowera ndudu et musamenye wa pakamwa ayi tkumane nxt wk, kulankhula kwambiri inu mwawina ma friendly angati? zamkutu eti,,,,!!

 12. nyerere ndi mphale ngati zulo amazunzika ndi ana amax bullets

 13. kupanga chibwana noma ziwavuta kwambiri game ya zulo sizinali bwino lef kukwera ndi frndly yomwe kkkkk kaya tiziwona ife timafuna kuti mupange timu ya bwino kuti ligi ikome zoti wina tizizamusiya 18points gap ukuziwa kale za bullets koma neba

 14. Ineso Game ndayionela Noma imasewera za mbola zenizeni inangochita mwayi kachigoli kamodzi ndiye kumatisokosa chonchi tiwakhawulitsa pa 9 pano

 15. Koma chisoni abale inu!!!!!!…..max bullets….kkkkkk….u just know …..big bullets..

 16. Nyerere matama pa buledi!!!!!!!!why Nakamura is not scoring
  Wait for the pples team sartuday the scoring machine chiukepo

 17. Nyerere matama abale, kungokoka kapisi ka buledi kumalimbana ndi munthu kuti ankokele kuuna kkkk samalani mukulimbana ndi chitimu osati team ai!!!

 18. Nanga mukuwopa chani yet chandeyo wll not be there utsi wadzadza kubongo eti ndempaka nkhani ya chande ikungowira mmutu mbuzi za ndudu fc umbuli thats why muli mavenda wogulitsa mamemory card anyimbo kale

 19. outof 14 chances scoring 1goal ndenkumati chenjezo to bullets mwasowa zochita eti,ana aphuu muziona za kusimongoliya pa 9.

 20. kuchinya max bulets mpaka dziko lonse kudziwa hehede,ziliko kulinga utatosako,mutivuta zedi,wk yatha zoona ku lepherana ndi ana a ngokwe foot ball club.hei what ashame.

  1. kod amenewatu aziona chaka chino inu mumalephera kusunga kope imozi yokha ya chande kut mawa muzakhale ndiumboni muoneka nazotu mbuli izi. osat ndinu mbulitu kkkkkkkk pepani

  2. kod amenewatu aziona chaka chino inu mumalephera kusunga kope imozi yokha ya chande kut mawa muzakhale ndiumboni muoneka nazotu mbuli izi. osat ndinu mbulitu kkkkkkkk pepani

  3. kod amenewatu aziona chaka chino inu mumalephera kusunga kope imozi yokha ya chande kut mawa muzakhale ndiumboni muoneka nazotu mbuli izi. osat ndinu mbulitu kkkkkkkk pepani

 21. Sizachilendo KWA ife a noma kutichinya mpira wapakamwa koma ubwino wake tikabwera pa ground ndipomwe amadziwa kuti Bullets ndi chi team

 22. How can I explain this testimony to the public about a great man who help me out in serious illness I have HIV AID for good 3year and I was almost going to the end of my life due to the way my skin look like all I have in my mind is let me just give up because life is not interesting to me any longer but I just pray for God every day to accept my soul when ever I’m gone lucky to me my kids brother run to me that he found a doctor in the internet who can cure HIV online he help me out on everything, the doctor ask for my details, so he can prepare the herbal medicine for me from his temple after all he ask is done one week later I started getting more stronger my blood start flow normally for 4 to 5 days I start getting Wight before 6 days my body start developing my skin start coming up after 8 days which he told me that i will be completely healed, I went for HIV test and I was tested negative I’m so happy that I can say I’m not a HIV patient if you have HIV/AID or any sickness he can still help you in getting your ex-back to you please contact him via his email: [email protected], or whatsapp him on +2348143143878.

 23. kkkkkkk Wakwiya naye Adminyu padakalipano ndi Mfiti kkkkk its true ihave head it, akuwopadi Ati awonesedwe kaye Contract Ya J Chande apo biii!! akuwopa sasewela nawo. Maaaamaaaaa!!! koma Manoma Na Season ino ithesesa team inayake baasii sindikukayika.

 24. palibe chifukwa chomaopyezera BB inu ngati mukuona kuti muli bwino limbikilani mutenge nzikho nzonse. koma chimene muganziwe pakamwa nsipamamenya mpila nzonse nzimathera pa Graund. ngati mwamenya max b. nsumunamenye BB. ndiye tiyenazoni zioneka tikakumana

 25. 1 yokha bas ndananso ngat amenewo mpaka kuima pachulu kkk koma neba ndmanyaz omwe ulbe lets mt next wk tdzakuonetsen a head (fodya) pantchto yawo

 26. vuto la masaporta abullets amazitenga ngat madolo koma ndimakape enieni,team yomwe inakamenya ma game awiri osachinyako olo chigoli chimozi mesa inali bullets yomwei hedeee matama bas za ziiii manyazi bwa

 27. Kkkkkk Beating Max Bullets By A Single Goal Z A Strong Warning To Big Team Like NBB, Dont Talk Much About That Game, Let Us Wait Until 09 April Then From That Time You will Know That Here In Malawi There Z no Any Best Team Rather Than NBB

 28. Ine ndikuganiza kut walembayo nd wa noma, komaxo anaxowa zolemba ndithu!!! Max Bulletx nd kachani? komaso ka chigoli kamodziko et!!

 29. Kkkkk neba mpira wake umene uja ! Ukanama uli kutali uona weekend ikubwerai kulephera kukhala ndi uniform yosiyananso neba!

 30. kkkkkkk strong warning for beating a team from division?hahaha khala serious Neba ka 1-0 komweka kma phokoso the whole world.Shame

 31. Tidikire pa ground nde muzalembenso izi weekend. Kod masponser enawa bwanji? To say the fact,the blue and white jersey imawakhala manoma.imaopysa noma poongoiona mmaso koma iyi yonga chipan cha amayiyi aaaa sili bho.

 32. Tidikire pa ground nde muzalembenso izi weekend. Kod masponser enawa bwanji? To say the fact,the blue and white jersey imawakhala manoma.imaopysa noma poongoiona mmaso koma iyi yonga chipan cha amayiyi aaaa sili bho.

 33. Neba..kkk..strong warning?..hahaha…si boxing2 iyi…this is dadada-kudoda…Kung Fu Agent Nakamura akukuphunzisani malodza..mukuzilakwila2 inu…NBB sipabawo2..9th April..1wk is lyk a page..plz lets go 2d nxt page..kkk..strong warning my foot!

 34. Neba..kkk..strong warning?..hahaha…si boxing2 iyi…this is dadada-kudoda…Kung Fu Agent Nakamura akukuphunzisani malodza..mukuzilakwila2 inu…NBB sipabawo2..9th April..1wk is lyk a page..plz lets go 2d nxt page..kkk..strong warning my foot!

 35. Kkkkkkkkkkkkk,koma neba wasowa chonena eti?kumenya max bullets wayesa ungamenyenso nyasa?ukuchita kupanga matukutuku ndi ka 1 komweko?ife timamenya matimu akunja monga dainamos.

 36. Kkkkkkkkkkkkk,koma neba wasowa chonena eti?kumenya max bullets wayesa ungamenyenso nyasa?ukuchita kupanga matukutuku ndi ka 1 komweko?ife timamenya matimu akunja monga dainamos.

 37. That’s really bull shit, after I read strong warning I thought its something about players or something illegal. But then beating max bullets is that really enough to scare others? Comeon!

 38. That’s really bull shit, after I read strong warning I thought its something about players or something illegal. But then beating max bullets is that really enough to scare others? Comeon!

 39. Kkkkkkkkkkkkk,koma neba wasowa chonena eti?kumenya max bullets wayesa ungamenyenso nyasa?ukuchita kupanga matukutuku ndi ka 1 komweko?ife timamenya matimu akunja monga dainamos.

 40. Kkkkkkkkkkkkk,koma neba wasowa chonena eti?kumenya max bullets wayesa ungamenyenso nyasa?ukuchita kupanga matukutuku ndi ka 1 komweko?ife timamenya matimu akunja monga dainamos.

 41. kkK ya no wonder why u r afool, wining game over max bullets z it suprise? is jst ateam coming from division. noma u r realy ateam full of fools starting from offiscial, playerz, suppoterz and u r team witch doctor kkkkk. c, bullets manage 2 beat abig team from mzimbabwe bt we didn’t say anything, but u fools 2much talktive kkkkkk

 42. kkK ya no wonder why u r afool, wining game over max bullets z it suprise? is jst ateam coming from division. noma u r realy ateam full of fools starting from offiscial, playerz, suppoterz and u r team witch doctor kkkkk. c, bullets manage 2 beat abig team from mzimbabwe bt we didn’t say anything, but u fools 2much talktive kkkkkk

  1. Shame!! poor perfomance 4 dat game u talking about, Lucky enough owner goal 4 the vistors so umati akananenapo chaanii!!?? kkkkk Manyazi mulibe?.

  2. Mbuli za manoma, max ndi team yoti mpaka muzimva nao sugar? just imagene ma frnds mukat mwawina nd 1 eg mxanama club 1, max 1, thondwe united 1, wizard 1. jali rangers 1 tangoganizan mamvuz thoo! kumathela 1. nden bullets magame amene amenya ndi amene inuo mwamenya can you compare your self?? Mxiew!

  3. someone call himserf acarter u r northing but ashirt of doggy pussy, fuck u men kkkk if u wann mes wth me then inbox me, hw u feel? ilk it

  4. Guys kodi mpirawu mumapindula nawo chani mPaka kutukwanana? Usapota omweu? Samalani mpira ungathe kukhala fano lanu!!

  5. zampira zilingati zandale.Masapota kutukwanizana uku maplayer eni akugawana madzi okumwa pa ground. Zaziiiiiiii.Usapota omwewu mpaka kumunena mzako afool.Iwe nde ndani? umapindulako chani kuusapata?kupusa kwamanga linga mmitima mwa anthu ambiri eti.

 43. ine game ndaionera noma siimamenya Bwino oti ref ndi amene anaikwera kwambiri.akozekutsogolo Kwao.pakati palibwino ndi rafiq miss ndi machine koma nakamula paja siwabwino

 44. ine game ndaionera noma siimamenya Bwino oti ref ndi amene anaikwera kwambiri.akozekutsogolo Kwao.pakati palibwino ndi rafiq miss ndi machine koma nakamula paja siwabwino

 45. Mpira ku malawi,strong wat?simunasiyebe kumenya mpira wa pa kamwa.azanu omwe mwawapasa wng amamenyera mpira pa graund ndi miyendo osat pa kamwa ay.

 46. Mpira ku malawi,strong wat?simunasiyebe kumenya mpira wa pa kamwa.azanu omwe mwawapasa wng amamenyera mpira pa graund ndi miyendo osat pa kamwa ay.

 47. Neba mtima mmalo next week yo ubatizo ulipo, ukuyeneradi kubatizidwa kuti machimo akowo akhululukidwe mwina ziyambe kukuyendera. NBB mo fayaaaaa

 48. Neba mtima mmalo next week yo ubatizo ulipo, ukuyeneradi kubatizidwa kuti machimo akowo akhululukidwe mwina ziyambe kukuyendera. NBB mo fayaaaaa

 49. Neba matama bac kkk point of collection u hav beaten Max Bullets Not Nyasa Bullets, Kmaxo Cigol Cimoz Sicopangra Matama Kkk Et Mpaka Warning Hahaha Kma Musandsekese

 50. Neba matama bac kkk point of collection u hav beaten Max Bullets Not Nyasa Bullets, Kmaxo Cigol Cimoz Sicopangra Matama Kkk Et Mpaka Warning Hahaha Kma Musandsekese

  1. Just imagine, 1-nil ya dying minutes after ref kukwera nde akuti strong warning. koma ma xul a jounalism atsekedwe ndithu na ngati anthu akuphunzira this kind of reporting kkkkkkkkkk

 51. There Is No Football In Malawi Dont Wasting Our Manoma Maule Ngati Mumadziwa Football Lets Play With Tp Mazembe Muone Bundles Of Goals Ten Zero

 52. There Is No Football In Malawi Dont Wasting Our Manoma Maule Ngati Mumadziwa Football Lets Play With Tp Mazembe Muone Bundles Of Goals Ten Zero

  1. Ku England Matimu Amakhala Ndi Ma Jersey Awiri Awiri.Kuno Its Only Noma Enanu Mumavalabe Same Colours! Wake Up.Home Tizimenyera Ya Orange Ndi Black Away Blue En White.

  1. Ku England Matimu Amakhala Ndi Ma Jersey Awiri Awiri.Kuno Its Only Noma Enanu Mumavalabe Same Colours! Wake Up.Home Tizimenyera Ya Orange Ndi Black Away Blue En White.

Comments are closed.