Blantyre says no to Chakwera

Lazarus Chakwera flops in Blantyre

…only 500 people attend MCP rally

Malawi Congress Party (MCP) leadership had a rude awakening in the city of Blantyre as residents of the city refused to show up for their rally.

Lazarus Chakwera Blantyre Rally
Chakwera addressing a handful of the crowd

The opposition MCP was holding a rally at Nyambadwe Primary school in Blantyre following mass rallies they had in Lilongwe and Mzuzu respectively.

However at Nyambadwe in Blantyre the MCP rally was largely shunned as there were few people with photographic evidence indicating that some had been ferried to the venue.

Local media reports that only 500 people or even less attended the rally in Blantyre where the MCP were holding to press the regime of Peter Mutharika to reduce its powers.

The rally was different from the previous ones that the party has held not only due to the turnout but also because its political bedfellow, the opposition People’s Party (PP) was not in attendance. It held a parallel rally in Makhetha.

A social commentator Emily Luwani has since warned the MCP that it risks losing the 2019 election if it keeps to perform dismally in the southern region.

“This is evidence that MCP has a long way to go, it had to get an audience considering that it’s in the opposition and the alternative to DPP,” Luwani said.

Luwani added that the party should not give up but aim to strengthen grassroots structures.

At the rally MCP leader Lazarus Chakwera told Malawi leader Peter Mutharika to reduce the powers of the executive.

Advertisement

358 Comments

 1. Bodza limenelo,oyamba kukhala ndi anthu ochepa akhalatu chakwera.kunali anthu zedi coz anakapemphera ku chilomoni catholic asanayambe kuchezera anthu.

 2. akulu-akulu aMalawi24 cheek if ur journalist are well qualified otherwise mukudzionongera mbiri then pipo will loss their interest on u

 3. Kkkkkkkk chakwera cannot convice pple to attend his rally as bad as he is.he cannot head the leadership of this country.let him know we are not happy with his mcp even if he can knock to every door,he cannot accepted and voted to power.kagwere uko mbusa wabodza.

 4. What statics r u uzing? Ine pano u ddnt consult me to hear my views if am for chakwera or not …so dot rush to make such premature conclusions…the crystal clear fact iz dat people have lost interest in these scruplous…corrupt coated politians. #realdemocrat

 5. kwa ine tsindikuwona vuto apa!! a malawi24 mnzinkhara ndi chikondi pa anthu,mtsawononge dziko lanthu kuzer pa udani, mnsankhare ngati kaine…….!!!!

 6. kkkkkkk koma kuchemererako mkumachemerera MCP misala chan angaiwale ndan nkhanza za MCP kumadulitsa card mwana wa m’mimba . imfa yovuta yosaiwalika ija Agadama ,Chiwanga, Nsangala ndi Amatenje mukuona ngat taiwala et . chipani chamwanzicho agalu ,timalephera kupita kunsika chifukwa cha chard anyani . M CP sidzalowaso m’boma bola pang’ono UDF . mukuona ngat anthu tilipofe tabadwa dzulo zonse achita a Tembo tikuzidziwa bwino. MCP ? what is MCP? fokofu . ikanjala sinabwere tse ndi DPP ai ndikusintha kwa nyengo basi . why south africa ikudandaulaso za chilala koma dziko lolemera .pano mitengo ya zakudya inakwera kwambili 10kgs ufa anthu amagula 20R pano ndi 80R imene ili 3500MK =10kgs nde njalao wabweretsa ndi Zuma ? . kupusa basi . mukufuna mukalo m’boma muzizaphaso anthu .

 7. Kwachaaa kwachaa zanziii boma LA abambo ako ndithu amene akusapota MCP alibe umulungu and kungowina MCP ine ndiwaku Zambia mpaka idzatuluke

 8. Angaiwale ndi ndani nkhanza mudapanga inu kunali achiwanga,amatenje,asangala ndi agadama kuthidzimula mapfumu nkati nkumati ine MCP zakuthako ndithu Malawi say no to zinyau,makhadi mix zanziii

 9. Mayaz musaname man Chakwera akutsika ma weight osanamapo apa msonkhano wa anthu 500 ndye masanje angoleka basi madimbi amenewo

 10. Hahahaha!choncho nkumati kwachaa!kwachaaa!zopusa eti?masana omwe kwacha!kwacha!anthu adaseguka maso inu kwacha kale mukadali kwacha!kwacha!! Kikkkkkki kumwela sazathekaso amakumbukira mawu uja oti wakumpoto,ndi wakumwera kwao.

 11. Mukhalira yomweyo yonzoza MCP, agalu inu Mitumbo yanu, MCP inapha Amako ndi Atate ako? Mudzidya madeya choncho ngati Nkhumba, Simunati mumva Madz i

 12. Aaaaaaah A chakwera Muli inu kuti muli pa mpando umenewu wina akugeya zomwe mukugeyazo mungata? ALOMWE ALOMWE ALOMWE
  yambisani dzina TAKE CARE 2019 ITS CLOSER

 13. U people talking foolish things about people from central region coz of the MCP party kumeneko ndikusowa umunthu mudziganizire life its unpridictable game ndani ankaziwa kut JB angalamulire inuso a Malawi 24 it seems that u are giving us unverifyd media take care.

 14. Msonkhano wa Dpp kumazaza apolice,asilikali,a PMF, ogulisa malonda, ma fumu ochita kukakamizidwa akajomba kumupanga devalue,ma Mp ndiponso ena amachita kuwakawatenga msonkhano uli ku mulanje kukatenga anthu mpaka kuchitipa malawi 24 ndi galaxy osamawamvera mcp ndi boma kale

 15. Msonkhano wa Dpp kumazaza apolice,asilikali,a PMF ma Mp ndiponso ena amachita kuwakawatenga msonkhano uli ku mulanje kukatenga anthu mpaka kuchitipa malawi 24 ndi galaxy osamawamvera mcp ndi boma kale

 16. A reporter counting people at a rally until he reached 500 is something untrue. People keep coming to a rally from the start to the end. Therefore this post is baseless

 17. Mmalo mokonza vuto akadzudzulidwa atsoleri a ku Malawi amalimbana ndi ofotokoza chilungamoyo. Koma chikazachitika chitsankho ndiye kuyamba kulongolora kumati atibera mavoti. Kaya, Khalani choncho.

 18. Forgive Malawi24 the highest qualified staff Ali ndi STD 8 certificate, sanakhozenso masamu ,instead of 50000 akuchotsera, mbuli za ku ma tea Estates izi.

 19. Malawi 24 chitani manyazi. Mudziyankhula zinthu zenizeni not zabodza. Did u count then one by one? Check zomwe akuonetsa pa TV. Shame on u!!!

 20. Kkkkk ine ndine wakumpoto koma dpp inandilowa. Kwambiri nthawi yomwe timapita kukavota timasekedwa koma atangolengeza kut dpp yawina ndinasangalala mot pano sindikudaso nkhawa. Tili. M. Boma antho akwatho kumupoto vuto. Sitiganiza koma kunyozana kusankhana mitundo

 21. mcp ndi chipani cha anthu a nyau. Since Gwanda dump mcp this party had never won a parliamentary seat here in southern region. u wil never rule malawi one region. mcp is regional party cha achewa

 22. you cant compare a state president’s rally with an opposition president. the president has the machinery , for instance, ferrying people from different places to hoodwink us that he is loved by many. again, not all who go there are the ruling Party ‘s sympathizers, some just go to see him as the state president or just to get entertained. after all, with what happened in mzuzu, those pangas, people are likely to be scared.

  1. Kufa ndi njala? Kkkkk, kodi ku MCP ali ndi ma Estate eti? Kapena adzidzatenga dolar zammatumba mwawo ndikugulira chimanga? Zikanakhala zakumpingo bola

 23. Anthu akamati mcp nchipani chachikulu sindimatha kumvesa kuti amayangani chani. kumwela chilibe phungu/khansala ndimozi yemwe, kumpoto chili ndi phungu ndi khansala mmodzi tikabwela pakati pano madela ena aphungu ngogawana ndizipani zina. Ndiye funso nkumati kukula kwachipani kuli pati? komanso akamalila kuti abeledwa ndimaona ngati mitu yao sigwila. Kodi chipani chingawine ndimavoti amaboma 5? only central district . zinazi amalila koma pansi pantima akuziwa chowona chenicheni.

 24. How can I explain this testimony to the public about a great man who help me out in serious illness I have HIV AID for good 3year and I was almost going to the end of my life due to the way my skin look like all I have in my mind is let me just give up because life is not interesting to me any longer but I just pray for God every day to accept my soul when ever I’m gone lucky to me my kids brother run to me that he found a doctor in the internet who can cure HIV online he help me out on everything, the doctor ask for my details, so he can prepare the herbal medicine for me from his temple after all he ask is done one week later I started getting more stronger my blood start flow normally for 4 to 5 days I start getting Wight before 6 days my body start developing my skin start coming up after 8 days which he told me that i will be completely healed, I went for HIV test and I was tested negative I’m so happy that I can say I’m not a HIV patient if you have HIV/AID or any sickness he can still help you in getting your ex-back to you please contact him via his email: [email protected], or whatsapp him on +2348143143878.

 25. Anthu akamati mcp nchipani chachikulu sindimatha kumvesa kuti amayangani chani. kumwela chilibe phungu/khansala ndimozi yemwe, kumpoto chili ndi phungu ndi khansala mmodzi tikabwela pakati pano madela ena aphungu ngogawana ndizipani zina. Ndiye funso nkumati kukula kwachipani kuli pati? komanso akamalila kuti abeledwa ndimaona ngati mitu yao sigwila. Kodi chipani chingawine ndimavoti amaboma 5? only central district . zinazi amalila koma pansi pantima akuziwa chowona chenicheni.

 26. Wina anali uko!!! amvekere KoKoliko!!! Kwaaachaaa!!!!!!!!! Inu!!! Lero!!!. iyaaa!!!Zakalekaleeee!!! Chipani chinapita kalekale ndi Mwiniwake KAMUDZU amachisogolera bwinobwino Osati Unyang’anya uli lerowu. kkkkkkkk ndi manena kawirikawi kuti,Olo atandiyika Doom nkamwa Sindinga Votere MCP.kkkkkkk Aliposo Wina!!!??.

 27. 500 pipo das gud news,nd njala wabweretsa petuloyi anthu sadakwanitse kupita on empty stomach ena anali kokasakaka chakudya,ena maganyu.koma I dnt belive a reporter can physically count anthu pa msokhano.osamanamizidwa pilizi

 28. Makosana tisaiwale kut na ku blantyre ndi komwe chipan cha MCP chinagwirisa magobo makolo anthu padzana.komanso kuzaza bwanj ngat kut kumwera kuli mdindo wamkulu?mmesa maudindo onona anapasana aku lilongwe okhaokha,aziona.ngat achakwera akufuna kuwina 2019 apange dzina blantyre ndi kumwera konse kut zisazachitike zomapeza 200 votes m’boma la mulanje

 29. Heeehedee!500 wo kuphatikiza ndi akwakauma kkk ndikukayika ngati panavinidwa magule chifukwatu azimayi akumwera nyimbo zamcp anayiwala kalekale . Pa 500 po 100 atumbuka a Msowoya kkk

 30. Zimenezo ndiye zabodza, i was there but am not a suppoter of Mcp kunali anthu osati ana amene mukunena inuwo ayi ndipo tonse amene tinapita kumsokhano umenewo tinachokela mmakwathu aliyense yekha yekha osati za Dpp zomachita kuwatuta anthu mma lolly ayi. Ndiye osamanamiza anthu pomalemba zabodza zanuzi apa.

  1. Iwe ndesunamvetse sanati kunalibe anthu ayi koma nonse pamodzi kuphatikiza ndiomwe anabwera nawo akwakauma mumakwana 500 ngakhale Capital fm yatchula figure yomweyo .ngati iwe siwa mcp ndekut ulimgulu la ana umaganiza Yudas chakwela wabweretsa nyau kt ukawone

 31. Mutha kuipitsa chipanichi mmene mungathere, atola nkhan mutha kunama mmene mungathere komabe mudzazindikira kut MCP NDI DILU

 32. Iwas passing by and decided to stop and listen what chakwera and his mcp what they want to deliver once elected in 2019. It was full of shame ndipo anthu 500 sanakwane… only vehicles for mcp mps from Central region were all over kuposa anthu. These vehicles of mps and central region mcp officials came with supporters and were seated close to msanja…..Advert or no advert, this is southern region we dont want u. We hurt u so much. Enawa azingokunamiza u are too. young politically to convince southern region vote. Takhalapo ndi ma political Ingineer they civic educated us on hw to differenciate btween afool and acaring leader. It will take another century for southernors to think about mcp. What pained me was that instead of focusing on hw mcp can transform malawi if elected, the whole mcp shamelessly led by stupid chakwera wasted my precious time telling me about violence in mzuzu kkkkk This is Stupid and childish. Wakuwuza ndani kuti kuno ku mmwera we are violent… are u sure all the way from lilongwe to tell us to stop violence like what happened @ mnzuzu… What astupid camp. Malawi will never be led by u fools. never!

 33. Iwas passing by and decided to stop and listen what chakwera and his mcp what they want to deliver once elected in 2019. It was full of shame ndipo anthu 500 sanakwane… only vehicles for mcp mps from Central region were all over kuposa anthu. These vehicles of mps and central region mcp officials came with supporters and were seated close to msanja…..Advert or no advert, this is southern region we dont want u. We hurt u so much. Enawa azingokunamiza u are too. young politically to convince southern region vote. Takhalapo ndi ma political Ingineer they civic educated us on hw to differenciate btween afool and acaring leader. It will take another century for southernors to think about mcp. What pained me was that instead of focusing on hw mcp can transform malawi if elected, the whole mcp shamelessly led by stupid chakwera wasted my precious time telling me about violence in mzuzu kkkkk This is Stupid and childish. Wakuwuza ndani kuti kuno ku mmwera we are violent… are u sure all the way from lilongwe to tell us to stop violence like what happened @ mnzuzu… What astupid camp. Malawi will never be led by u fools. never!

 34. MCP,this is New MCP,the only clean party at our time. Udf,Dpp,PP are dirty Parties, the Cashgaters.Recycled Politicians have Ruined our country they must step down,Recycled politicians are those From Muluzi Udf to Bingu Dpp to PP to Dpp again.Oooo step down.You have more Harm to malawians.

 35. MCP,this is New MCP,the only clean party at our time. Udf,Dpp,PP are dirty Parties, the Cashgaters.Recycled Politicians have Ruined our country they must step down,Recycled politicians are those From Muluzi Udf to Bingu Dpp to PP to Dpp again.Oooo step down.You have more Harm to malawians.

 36. MCP,this is New MCP,the only clean party at our time. Udf,Dpp,PP are dirty Parties, the Cashgaters.Recycled Politicians have Ruined our country they must step down,Recycled politicians are those From Muluzi Udf to Bingu Dpp to PP to Dpp again.Oooo step down.You have done more Harm to malawians.

 37. MCP,this is New MCP,the only clean party at our time. Udf,Dpp,PP are dirty Parties, the Cashgaters.Recycled Politicians have Ruined our country they must step down,Recycled politicians are those From Muluzi Udf to Bingu Dpp to PP to Dpp again.Oooo step down.You have done more Harm to malawians.

 38. Pathoko pinu imwe wa malawi 24 wamuphalilani ninjani kuti kwanguwevye wanthu mukhaula ndinjala ifekuno chimanga chiliko chambiri kma musaiwale chakwela 2019 ndi boma

 39. Pathoko pinu imwe wa malawi 24 wamuphalilani ninjani kuti kwanguwevye wanthu mukhaula ndinjala ifekuno chimanga chiliko chambiri kma musaiwale chakwela 2019 ndi boma

 40. Mw24 full of monday journalists.Anakutumani kuti Mukawerenge Number Ya Anthu Anafika Ku Msonkhanoko?Mwapasidwa Zingati?CHAKWERA Wathu Musiyeni.

 41. Mw24 full of monday journalists.Anakutumani kuti Mukawerenge Number Ya Anthu Anafika Ku Msonkhanoko?Mwapasidwa Zingati?CHAKWERA Wathu Musiyeni.

 42. Osamakonda Kukhulupilila Amalawi 24,ndi Anthu Abodza Ngati Mufuna Zoona Tsekulani Station Yodziwika Bwino Ija,osati Atolankhani Omanamiza Munthu Woti Anali Konko,timadziwa Ife Kuti Munama Chifukwa Ntchito Zanu Tikuzidziwa .

 43. Osamakonda Kukhulupilila Amalawi 24,ndi Anthu Abodza Ngati Mufuna Zoona Tsekulani Station Yodziwika Bwino Ija,osati Atolankhani Omanamiza Munthu Woti Anali Konko,timadziwa Ife Kuti Munama Chifukwa Ntchito Zanu Tikuzidziwa .

 44. kunena zoona nthawi ino si yokopa anthu pa misonkhano, njala idakalipobe. Musayembekezele kuti anthu ambiri angapezeke pa msonkhano wa MCP. Ndizoona zomwe alemba a Malawi24. Komanso MCP ilibe moralo ku south ,MCP ilibe phungu ngakhale khansala ku mwela ,khulupilirani zomwe atolankhani akunena.

 45. kunena zoona nthawi ino si yokopa anthu pa misonkhano, njala idakalipobe. Musayembekezele kuti anthu ambiri angapezeke pa msonkhano wa MCP. Ndizoona zomwe alemba a Malawi24. Komanso MCP ilibe moralo ku south ,MCP ilibe phungu ngakhale khansala ku mwela ,khulupilirani zomwe atolankhani akunena.

 46. Chakwela yemweyo basi.apa amalawi tinachita nkusadziwa ndipo ulendo ukubwelawu,sitidzalolaso satana kutinyenga kubetsa vote yathu pazinthu zosathandiza ndipo tikupempha ambuye kuti adzatitsegulire maso athu tidzakhale wopenya,mtima wathu kuti tikazindikire wosatiso tidzalire kachikena

 47. Chakwela yemweyo basi.apa amalawi tinachita nkusadziwa ndipo ulendo ukubwelawu,sitidzalolaso satana kutinyenga kubetsa vote yathu pazinthu zosathandiza ndipo tikupempha ambuye kuti adzatitsegulire maso athu tidzakhale wopenya,mtima wathu kuti tikazindikire wosatiso tidzalire kachikena

 48. Blantyre never said no to chakwera.. Koma a mcp ddnt advertise it properly… I stay cloz to nyambadwe but i ddnt knw.. Blantyre ddnt say no to chakwela.. U the one who said no to chakwela.. Blantyre haz denied..

 49. Blantyre never said no to chakwera.. Koma a mcp ddnt advertise it properly… I stay cloz to nyambadwe but i ddnt knw.. Blantyre ddnt say no to chakwela.. U the one who said no to chakwela.. Blantyre haz denied..

  1. kkkk true bro thats why out of 4million pple 500 said yes .advert yanji umafuna maradio ali mbwee matv chanel mbwe daily kumalengeza timamva mamega phone amayenda navo kungoti kumwera zayudas aaa ndikutali

 50. Kodi anthu 500 wo anali achipani chanji? ndi amene munawatumiza kuti akamvere nawo mfundo za MCP kapena? zoona zake mzoti Chakwera mukumuopa ambili anthu onse aja angakhale 500? inu ndi abodza ndiithu!

 51. Kodi anthu 500 wo anali achipani chanji? ndi amene munawatumiza kuti akamvere nawo mfundo za MCP kapena? zoona zake mzoti Chakwera mukumuopa ambili anthu onse aja angakhale 500? inu ndi abodza ndiithu!

 52. Atolankhani abodza inu olowa ntchito chifukwa zochita zavuta,mukafuna kulemba nkhani lembani zimene munaona zokha zokha ,ndichifukwa chani mumalowelela ndale m’malo mogwila ntchito .munazolowela vamahala, inu musanabweletse nkhani imeneyi ena atatiuza kale zoona, anzanga page limeneli ayamba bodza musamatsekule.

 53. Atolankhani abodza inu olowa ntchito chifukwa zochita zavuta,mukafuna kulemba nkhani lembani zimene munaona zokha zokha ,ndichifukwa chani mumalowelela ndale m’malo mogwila ntchito .munazolowela vamahala, inu musanabweletse nkhani imeneyi ena atatiuza kale zoona, anzanga page limeneli ayamba bodza musamatsekule.

  1. Inu anthu ngat kale amachita nkhaza idali nthaw yomweyo pano zinthu zili chonch:dzina lachipan ndilomwerija lot mcp koma olamulira ake ndiena choncho iweyo usavutike 2019 Chakwera More Fire

  1. Inu anthu ngat kale amachita nkhaza idali nthaw yomweyo pano zinthu zili chonch:dzina lachipan ndilomwerija lot mcp koma olamulira ake ndiena choncho iweyo usavutike 2019 Chakwera More Fire

 54. 500….? sunday xul…. chani..,?

  a Malawi chonde tiyeni tizikondana owerengayo amawerenga bwanji ngati msonkhanowo umachitikira ku stadium….?

 55. 500….? sunday xul…. chani..,?

  a Malawi chonde tiyeni tizikondana owerengayo amawerenga bwanji ngati msonkhanowo umachitikira ku stadium….?

 56. Ndinthawi yabwino kuti muunike mavuto omwe ali ku chipani chanu nthawi isanafike….

 57. People were fearing this DPP Panga government when there counter political paties are doing rallies like this they bring Panga and start slashing people like what happened in Mzuzu some past days

 58. People were fearing this DPP Panga government when there counter political paties are doing rallies like this they bring Panga and start slashing people like what happened in Mzuzu some past days

  1. inu dpp ndiyakumwera alekelanji kumenya uko anapanga zija ndi a pp kafaction kakudana ndi Ulad musa dpp ili ndianthu okwanira owinila mavote

  2. Mukungotaya nthawi yanu mcp sinakwanila…. akufunika aphunzire bwinobwino ndalezi. 2019 sinafike nkomwe koma ayamba kale ma alliance kkkk what for…?

  3. kkkkkkkk koma yudasi mpaka kulamulila 8t. uyunso atuluka ngati Tembo, mcp lelonso! Tembo atalephela 2004 anapanganso ngwilizano 2009 ndi udf koma akadaziwa sakadatero. Ndiye uyunso yudasi scaliot walephela 2014 apanganso ngwilizano 2019 ndiye azaonanso zomwe zidaona nzake mbuyomu, ndikayangana kwa osusa sindikuona chipani chomwe chingapikisane pachokha ndi Dpp nkuwina, olo ataphatikizana ali kutali kwambili

 59. Ndikuganiza kut ngati pansonkanowo panali anthu 500, kwaine ndi chiyambi chabwino chifukwa nsonkhano wa Peter wamuthalika atati ma MP ake asatenge anthu kuchokera mmaboma onse akumwera kuno nde pangakhale anthu angati?

 60. Ndikuganiza kut ngati pansonkanowo panali anthu 500, kwaine ndi chiyambi chabwino chifukwa nsonkhano wa Peter wamuthalika atati ma MP ake asatenge anthu kuchokera mmaboma onse akumwera kuno nde pangakhale anthu angati?

  1. #amalunga theory imeneyo idzibwera pazipani monga Afford,mdu,mdp etc nt Mcp mwatani kodi ?nthawi yakamuzu msonkhano uli kunsanje anthu amachoka kukaronga mchinji just to give support ngakhale yudas wanuyo amayenda nawo akwakauma ndimwambo wake

  2. Vuto la Mcp ktmwela kuno alibe mazilo m’mizimu. Timangomvela pa wailesi, m’manyuzipepala ndi paneti Mcp ikutokota koma m’mizimu mulibemo. Ine ndinaimanawo za makhansala ku Luchenza kuno, atandipeza aMcp ndikundipempha kuti ndiimilire Mcp ndinakana chifukwa mtengo sulimba opanda mizu. Ndinawauza Mcp kulibe kuno ndikamathamangisidwa ndithawila kuti ? Poti ndine woyima pandekha mundipwetekesa sindifuna.

 61. you guys are not serious..how did u count up to 500 people.did u put them on a line or u took a sample.by the way,u didn’t even have cameras to evidence this nonsense u are talking about..this is why u’ll see no growth.zodiak shall remain the trusted source of information

 62. you guys are not serious..how did u count up to 500 people.did u put them on a line or u took a sample.by the way,u didn’t even have cameras to evidence this nonsense u are talking about..this is why u’ll see no growth.zodiak shall remain the trusted source of information

  1. Amwene masamu nga Approximations simunapange nawo olo nga Average nanga minimum ndi maximum munamvapo ngati pagulu sawerenga 1,2,3,4,5 ayi njirazake ndizomwdzo kuteroko 500 ndimaxmum figure mwina sakukwananso nambalayo ndichimene akutanthauza i think wamva

 63. kodi anthu inu wolemba zolembazi mumakonda bodza bwanji?ili ndi bodza la mkunkuniza blantyre singakane olemekezeka bwana chakwera. mudzilemba za ufulu omwe tikukumana nawo pamoyo wathu mdziko muno.apa osamalemba zonyoza ena pakuti MULUNGU safuna dziwanda dzoteledzi.

 64. kodi anthu inu wolemba zolembazi mumakonda bodza bwanji?ili ndi bodza la mkunkuniza blantyre singakane olemekezeka bwana chakwera. mudzilemba za ufulu omwe tikukumana nawo pamoyo wathu mdziko muno.apa osamalemba zonyoza ena pakuti MULUNGU safuna dziwanda dzoteledzi.

  1. vuto la achewa saenda amakakamila kukhala ndikugwila ntchito kwao pamene alomwe ndi nsanje to chitipa. Ndiye poti kachipanika nkapacentral kasova kazingowina maboma five okha

  2. Usandiseketse M’bale, tereku wayiwala kuti majority mmalawimuno ndi achewa?
   Vuto la alomwe ndiloti alingati chule odumpha popanda gwembe.
   Muziwona 2019 Uno.
   Inu mukunena zamchewa? Congress Sichipani Cha Achewa ayi koma cha amalawi. Inu Kuyendayendaku Sikusowa Pokhala Komaso Polima, Mkuwona timakulembani ntchito ife apacentral ndi northern regions?
   Tawawoneni abale athu kummwera konko aliphe coz anaakhazika kale pomwe inu ndi ma late comers ndipo thats the reason you run for cashgates. Achewa Tiri posepose koma mcp mchipani cha mitundu yonse.
   Inu mwachepa simungapange triblisim, sorry.

  3. Hahahahhaha uziti mcp chinali chipani cha amalawi tili mu one party system pano chinasala pakati pokha. chili ndi aphungu angati kapena makhansala angati kumwela? Nanga kumpoto chili ndi aphungu kapena makhansala angati? Ndiye uzikliuza dziko lelo kuti ndichipani cha amalawi, mukuona ngati boma mungatenge ndi 5 district only. Ukukambanso za 2019 tinaonelatu ma bye election apitawa munapeza mipando ingati yoti dpp nkuitutumusa? chipani chinapita ndikamuzu ichi tidakwilila limozi ndipo zoti yudasi scaliot nkuzalamulilanso iwala mbale.

 65. kodi anthu inu wolemba zolembazi mumakonda bodza bwanji?ili ndi bodza la mkunkuniza blantyre singakane olemekezeka bwana chakwera. mudzilemba za ufulu omwe tikukumana nawo pamoyo wathu mdziko muno.apa osamalemba zonyoza ena pakuti MULUNGU safuna dziwanda dzoteledzi.

 66. kodi anthu inu wolemba zolembazi mumakonda bodza bwanji?ili ndi bodza la mkunkuniza blantyre singakane olemekezeka bwana chakwera. mudzilemba za ufulu omwe tikukumana nawo pamoyo wathu mdziko muno.apa osamalemba zonyoza ena pakuti MULUNGU safuna dziwanda dzoteledzi.

  1. Pa_anthu_500_wa_200anali_ongulisa_malonda_mandasi,thobwa_mizimbe_mpaka_ena_kumaphika_zibwente_konko!!!,mcp,pp,ppm,aford,umodzi,ngwilizano_wanu_ulibe_phindu_hahahahahahaha_wina_alira,muziona_zosapota_enanu.

  2. Ngatidi kudali chomwechi kunali tiwanthu ukadaziwa sukanaikanso izi nzochitisa manyanzi. Nsonkhano wa mcp paokha sikungakhale wanthu mwina atamaphatikizana ndi pp mwina azionako tiwanthu tochulukilapo.

  3. Ngatidi kudali chomwechi kunali tiwanthu ukadaziwa sukanaikanso izi nzochitisa manyanzi. Nsonkhano wa mcp paokha sikungakhale wanthu mwina atamaphatikizana ndi pp mwina azionako tiwanthu tochulukilapo.

  4. Ngatidi kudali chomwechi kunali tiwanthu ukadaziwa sukanaikanso izi nzochitisa manyanzi. Nsonkhano wa mcp paokha sikungakhale wanthu mwina atamaphatikizana ndi pp mwina azionako tiwanthu tochulukilapo.

  5. Ngatidi kudali chomwechi kunali tiwanthu ukadaziwa sukanaikanso izi nzochitisa manyanzi. Nsonkhano wa mcp paokha sikungakhale wanthu mwina atamaphatikizana ndi pp mwina azionako tiwanthu tochulukilapo.

 67. Hahahahaha, ili ndi bodza lenileni. Pamalo pakafka Dr Chakwera sipamanama. Munamuona Chakwera akupereka malorry kt adzituta anthu m’madera? Musamapusitsike amalawi anzanga. Chabwino, anthu 500 anabwera okha, imagin akanatuta anthu kwina ngat m’mene amachitira Pitala, kukanakhara anthu angat? More fire Chakweraaaa!

 68. Hahahahaha, ili ndi bodza lenileni. Pamalo pakafka Dr Chakwera sipamanama. Munamuona Chakwera akupereka malorry kt adzituta anthu m’madera? Musamapusitsike amalawi anzanga. Chabwino, anthu 500 anabwera okha, imagin akanatuta anthu kwina ngat m’mene amachitira Pitala, kukanakhara anthu angat? More fire Chakweraaaa!

  1. Dzose zimapangisa ndi Ndalama Nanga mcp Athuwo angawatutire muchani? Ma Landrover omwe aja!! Anasiya Malemu Kamudzu iiiiiii!!!Lerooooo!!!Amangwetu muyisovenge.

  2. ndalamazake mitsonkho yathuyo!! ….mnsonkhano akamapangra ku zomba amakatenga anthu ku thyolo ndi ku mulanje…….ati kukadzadze….SIKUNYENGA NDICHALA KUMENEKO!

  3. Anthu omwe amakawatuta kummulanje ndikwinako ndiomwenso amamuvotela inu salani ndindale zachikale zoti tisatute anthu pamene anzanu amaiwelengela patali. Ndinkona olo mp alibe kumwela ndikupepela kwake kumeneku kosafuna kututa wanthu kukamvela mfundo zake

  4. Kkkkkk mcp imangotenga anthu pagalimoto nkukawatula nkuwapha kumwanza basi.zopusa.nanunso kutengeka,be smart,choose good and be good,throw mcp away think twice uzalira 2019 ndi congress yakoyo.

  5. pepani a mcp nonse musanyengeke ndi agalatia wanuyo kt ku bt muzaphulako azinyada pakati pompano maka kwa osazindikira ngati inu anthu anyau/agule

 69. Mabodza Awa Ine Andikonda.Inu A Malawi24 Mwandienjeza.Bwanji Ngat Page Yakutopetsani Mungochita Delete,ifetu Sitingadwale Mutatero.

 70. Mabodza Awa Ine Andikonda.Inu A Malawi24 Mwandienjeza.Bwanji Ngat Page Yakutopetsani Mungochita Delete,ifetu Sitingadwale Mutatero.

  1. Phiri,,Madise,,Chivo and Edson kodi mukadagonabe??? guys zukani,ngati mumaganiza kuti MCP izatenga boma iwalani anthu amene akhala akuzudzidwa ndi MCP akadali moyo and ali ndi ana awo and so amawauza zimene zidali kuchita KAMUZU and JOHN TEMBO ngati inu makolo anu samakuuzani amakulankhwirani iwalani kuti mcp izawina

  2. Kamuzu and tembo r no longer incharge of the party we got new blood,gustav kaliwo, msowoya ,chakwera al hav clean recods mcp boma come 2019

  3. Kamuzu and tembo r no longer incharge of the party we got new blood,gustav kaliwo, msowoya ,chakwera al hav clean recods mcp boma come 2019

  4. Kamuzu and tembo r no longer incharge of the party we got new blood,gustav kaliwo, msowoya ,chakwera al hav clean recods mcp boma come 2019

 71. u had a job to count one by one?? nt true, am a chakwera fan and am here in brantyre bt i dnt attend due 2 othr reason posibly timaopa anzathu a zikwanje aja..

 72. u had a job to count one by one?? nt true, am a chakwera fan and am here in brantyre bt i dnt attend due 2 othr reason posibly timaopa anzathu a zikwanje aja..

  1. Since He Started Campain If That Time Was Preaching Gospel Up To Now God Could Reward Him But Now He Is Leading People To Hero

  2. Since He Started Campain If That Time Was Preaching Gospel Up To Now God Could Reward Him But Now He Is Leading People To Hero

 73. Bwanji osawawonetsa anthu 500 mwanenawo apa ndee ndadziwa kuti mumasowa zochita ndipo MBOLI Zanu chinantindi chosechija chimataniko

 74. Bwanji osawawonetsa anthu 500 mwanenawo apa ndee ndadziwa kuti mumasowa zochita ndipo MBOLI Zanu chinantindi chosechija chimataniko

Comments are closed.