Lazarus Chakwera’s position as Malawi Congress Party (MCP) president has come under further scrutiny as the party’s officials have intensified efforts to remove him.
Following an application by some members of the MCP, the High Court in Lilongwe has ordered the party to hold a convention in the next 90 days.
The members sought the court’s intervention after getting tired of the party’s leadership and its failure to solve wrangles within the party.
However, MCP spokesperson Jessie claims she is yet to be informed about the court order.
But lawyer for the disgruntled MCP officials insisted that they the court has granted them the order.
Ku machenjera pa Malawi
Ku machenjera pa Malawi
ndifebe a m c p
mupherana zaweni guys all of u r poor they know wht r they doing
Matsiku osiliza!
Za ziii
Za mcp mukafuse antcheya alibe nacho mawu
Za mcp mukafuse antcheya alibe nacho mawu
Chakwera sangakhale mtsogoleri wa dziko coz alibe mfundo zanzeru. Tingosankhadi wina kuti azatiimire 2019.
Chakwera sangakhale mtsogoleri wa dziko coz alibe mfundo zanzeru. Tingosankhadi wina kuti azatiimire 2019.
Mutilephela,simungatikwanitse taaaaa!!!!
Palibe wabwino pa dziko lapatsi.
ngati zinakanika a TEMBO ndiye awa iiiiiii
It will not come to pass
Lero munthu wakuMalawi wasanduka chitonzo kwa anthu andale zomventsa chisoni anthu amene akuti ndiophunzira zochita zawo kuposanso amene sadaphunzire zosowa za dzikoli mukuzizidziwa bwino koma mukuchita chikuwawe anthu amene mwini wake Mulungu anawaika m dziko limeneli kukhala kwawo tsiku ndi tsiku inu andale kumenyana nkhondo yandale kuyambira Chaka cha 1994 zipani zolamulira kumangochita kampeni mmalo molamulira dziko kuba chuma cha anthu olimbikira omwe inu mumati osauka ganizani dzikoli lili ndi anthu abwini omwe mukuwasandutsa kukhala amphawi ndindale zosakhalabwino ngati ndi ndalama siyani ndalezo mudzikadya .ndalamazo osati kunzunza ntundu wamwini wake Mulungu anaukonda ndikuudalitsa ndintendere atsogoleri opanda nzeru mukufuna kusokoneza ntendere umeneu koma sizitheka mpaka mulephera koma wina adzalamulira dzikoli ndipo mudzasilira Komanso opanda zimaphunziro zonunkhazo zomwe za ononga dziko lathu lokongolali mpaka kutiposa Burundi ndi Rwanda
Chakwera Sangamuthe Ndi Madala amene aja!!!
Chakwera is weak.He is not fit to lead MCP.
dyera chakwera
[READ MY STORY. ON HOW I GOT MY HIV CURED].
Truthfully, i was tested HIV + positive for the past 8 years. I keep on managing the drugs i usually purchase from the health care agency to keep me healthy and strengthen, i tried all i can to make this disease leave me alone, but unfortunately, it keep on eating up my life, this is what i caused myself, for allowing my fiance make sex to me unsecured without protection, although i never knew he is HIV positive. So last Two Months i came in contact with a lively article on the internet on how this Powerful Herb Healer get her well and healed. So as a patient i knew this will took my life one day, and i need to live with other friends and relatives too. So i copied out the Dr Collins the traditional healer’s contact and I contacted him immediately, in a little while he mail me back that i was welcome to his Herbal Home whereby all what i seek for are granted. I was please at that time. And i continue with him, he took some few details from me and told me that he shall get back to me as soon as he is through with my work. I was very happy as heard that from him, as i was just coming from my friends house, Dr Collins called me to go for checkup in the hospital and see his marvelous work that it is now HIV negative, i was very glad to hear that from him, so quickly rush down to the nearest hospital to found out, only to hear from my hospital doctor called Browning Lewis that i am now HIV NEGATIVE. I jump up at him with the a test note, he ask me how does it happen and i reside to him all i went through with Dr Collins. I am now glad, so i am a gentle type of person that need to share this testimonies to everyone who seek for healing, because once you get calm and quiet, so the disease get to finish your life off. So i will advice you contact him today for your healing at the above details: Email ID: [email protected] or you can also add him up on whataspp +2349036950737. CONTACT HIM NOW TO SAVE YOUR LIFE AND DOCTOR ALSO CURE ALL KIND OF DISEASE AND SICKNESS: [email protected] AS HE IS SO POWERFUL AND HELPFUL TO ALL THAT HAVE THIS SICKNESS…
Anamezedwa kale awo ubusa ndi ndale sizimozi tangochosanipo zina laubusalo uyo ndi politian not Reverend
Ndingofuna kufusa kwa inu amene mukuti wasiya za god kodi amene amakhala mtsogoleri wadzi akapita ku gahena? Kapena amene amakhala mfumu ya mmudzi olo ya dela wa ku gahena? Ndikawona bible muli mafumu kunali mfumu Davite, fumu solomo osewa fumu kwitoliyo ndambiri Osewa moti samatumikira God? Mtsogoleri wabwino amasankha ndi mulungu siyizi zikuvutazi zosankhidwa mwachinyengo God sangakupatse mzeru zoyendetsera Dziko.FUMU SOLOMO Anapempha mzeru kwa God ndipo anayipatsa mzeru fumu solomo nde apa Chakwera alibe problem apeter ndamene ali ndi problem

tambala wakuda kapena bakha wakuda kkkk
tambala wakuda kapena bakha wakuda kkkk
Mvuto lili ndi Nyasand ndilimeneri munthu kulakwitsa mmalo momukhazika pansi ndi kupeza mayankho koma achoke timanga malawi? Ndiye mkumati 2019 nkhuku yakuda boma masewela ake amenewa? .Abalamula matchona osadziwika kwawo omwewa nanga tithawila kuti

Ife a DPP tili pheeee,2019 Boma wina afune 0lo asafune
Ife a DPP tili pheeee,2019 Boma wina afune 0lo asafune
Kkkkkkkkk ayisova
Kkkkkkkkk ayisova
Chakwera asakhepo mulungu ndi zadziko,ngati mumamukonda chakwera muuzene zabwino za mbuye not zapadziko akutangwanika ine ake olamula ali pheeee,alilongosola dziko ndi peter basi
Chakwera asakhepo mulungu ndi zadziko,ngati mumamukonda chakwera muuzene zabwino za mbuye not zapadziko akutangwanika ine ake olamula ali pheeee,alilongosola dziko ndi peter basi
Munthu wa Mulungu wasiya kuwelenga Bible lero akuwerenga ma novelo….josephy nkasa pa repeat
Munthu wa Mulungu wasiya kuwelenga Bible lero akuwerenga ma novelo….josephy nkasa pa repeat
Indeed do what the Lord say , just leave it bcoz is not side .
Indeed do what the Lord say , just leave it bcoz is not side .
mulungu anatuma #yona kuti akalalikire uthenga wa yesu,, koma iye anakana kunyonzera mapeto ake chinsomba chachikulu chinameza #yona…..abusa musamale mdziko muno mulibe nsomba yomwe inameza yona koma muli zambiri zomwe zitha kukumedzani mpaka kuchotsa moyo…#bwerelaniKuCHURCH pastor plzzzzzz…
Kkkkk koma Fanny
Kkkkk koma Fanny
Kikkkkki zoona fanny mu nyanjamo mulidi chinsomba alimo ache Felix Jumbe,ache dzoole mwale,ngati abusa akufuna aziwe zambiri kuti mmenemo muli ng’ona awafutse ache louis chimango,ulendo wa malemu zanja limodzi mwana wa pa dedza,che ntaba pa nathenje,che majoni pa lilongwe,che kutsaira.
Absolutely
Ati afuna aonetsese,akawafunse achafukira kut pano akuthamangira kuti?
abusa akundimvesa chison kwambiri…
Yona sanatumidwe kukalalikila uthenga wa Yesu KuIraq ayi tiyeni takambe zoona osati bodza
jomba pita uko,,,ukudziwa chani iwe za bible…inu ntchito yanu si kupolama basi iyaaaa #demet!!!!!
Kaya wina afune kaya asafune Chakwela ndi mtsogoleli wa chipan cha MCP bas winawe wagwanao , mungowadyela adpp o koma sizsintha kanthu kwachaaaaaaaaaaaaaaaa.
mukati muzalaweko boma nde muzaphanatu…ngati mukukwenyana pano
Azikalalikila basi
Mchotseni ameneyo oipa kusiya ubusa kuyamba ndale zoona
Tiyeni nazo mkamaliza mtiuza mcp chipani chamagaz anapha alone gadama, dick matenje sitiiwalatu paja
Amfuse #Yona ofuna kuthawa ntchito ya Mulungu,inu ndie m’mezedwa ndi mbewa ndithu
Mkholokolo izi inu osamataya nazo nthawi.
chipani chatsoka ngat chmenecho…chipani chofuna kubwezera zoipa kudzko..chipani cha yudasi.
M.C.P blood is M.C.P blood,ngakhale mutayankhula zotani simungatichotse pambuyo pa our loved leader D.r. Chakwera ndipo sikuyamba kumva nkholokolo zikuvutika ndi nsanje.They were there even in the tym of our former leader J.Z.U but they did not succeed.Ee! Mukunamatu,
Alibwino,koma vuto ndi chipanicho chifukwa hesh chinatengedwa ainiayake kumanda
chipani cha MCP mulungu wamwambamwamba adachikana ,zomwe zikuchitikazi nzosadabwisa makamaka pa mbiri ya chipanichi.I always feel sorry for the man of god,Dr Reverend Chakwela for associating with the deadly ,bloody ,notorious MCP instead of serving almighty god. Malangizo anga ndi akuti papa Chakwela bwelelani ku gulu la mulungu mukamachita makani ndi MCP muzaona zomwe adaona aujeni aja for sure.
am agree wth u
chipani ichi chili ndi mbili zonyasa
Maxon What You Have To Know Is The Bible Says You Shall Know Them By Their Fruits,and If You Love The World And The Things Of The World The Love Of God Is Not In You
Dont foget all parties and people in them came from mcp hence them r notorius too
Dont foget all parties and people in them came from mcp hence them r notorius too
Tachilozani chipani chomwe inu mukuti ndi chabwinocho?
Abale kunena zoona Zipani za PP ndi MCP zakhala zikulimbilana maudindo before and after elections.DPP ndi UDF kulibe mikangano kapena kutengelana ku bwalo la milandu. Makhalidwe a tsogoleli azipani za PP ndi MCP ndiomvesa chisoni ndi manyazi ,akulola bwanji kuti anthu agawanike. Oyambitsa mikangano amayenela kuchotsedwa muchipani. People can’t learn from the late Bingu.
Munthu wa mulunngu kusiya kutumikira mulunngu koma ndale umasata chani? kodi nyimbo ya ndirande anglican ija unayimverapo yoti zimandikwanira? Bwanji osatengera chisanzo cha wachikulire a john chilembwe ? Do you you are wiser or luckier than john chilembwe?
All these wrangles in MCP Leadership ndi DPP party tells lies to opposition party followers with money kuti agawanitse chipani knowing the party is getting more popular and power than DPP so to achieve it ama user system yoyambanitsa iyo nkukhala poterepo kumaonera as if they are not involved kuli achina Dausi,Ntaba amatha bodza
Kkkkkkkkk mudziwamudziwa
simunati…mwayamba kale kunjenjemera dpp zikugwirizana bwanji ndi abusa anu opusawo??? muwauze abwerere ku kachisi wa mulungu akalape ….mulira simunati
Mwangoyambapo sizizatheka kut Chakwela atenge mpando waupresdent kuno kumalawi mwina akayambenso ubusa ukumudikila
osatheka nde Gwenembe uti angayendetse chipani poti onse Mmadeya
kuthawa utumiki wa chauta kumapanga ndale mukuona ngati zingaende?? mukawerenge nkhani ya Yona, akuluwa anathawa ntchito ya chauta
This things are coming from outside and they want succede either
klkkkkkkk Why u wainting 4!!? Remove him!!.
chakwera is man of God
kkkkkkkkkkkk………pliz mcp veterans,mutenge political holiday, which will earn you a clean history in politics. …mwakula nd it seems like you dont know where you are going nd how to move from where you are………chipanichi chakalamba ,kapena find a new leader,koma from another region ,osati Achewa,mukumachulusa mapokoso and it seems like ndinu anthu olongolola kwambiri.
MUSATISOKONEZELE CHIPANI ENANU ANY TIME MUKHALA PA LOW .
Hahahahahaha kkkkkk ndale zapa mpanje zichotsanani.
Hahahahahahaha zataninso nanga?
Zotumidwa
Kkkkkkk baibulo limanena kuti masiku otsiliza kuzakhala kucita zinthu zosiyanasiyana kuzakhala mtundu ndi mtundu kuwukilana ndizitu kaya makandanani
dzenje lokumbira wina umagweramo wekha
If chakwela is failing to put together it’s members in mcp how can he help us Malawians
Who do you think can?
If u r being funded by somebody akupweteketsa
Expect DPP to rule forever
[READ MY STORY. ON HOW I GOT MY HIV CURED].
Truthfully, i was tested HIV + positive for the past 8 years. I keep on managing the drugs i usually purchase from the health care agency to keep me healthy and strengthen, i tried all i can to make this disease leave me alone, but unfortunately, it keep on eating up my life. So last Two Months i came in contact with a lively article on the internet on how this Powerful Herb Healer get her well and healed. So as a patient i knew this will took my life one day, and i need to live with other friends and relatives too. So i copied out the Dr Collins the herbal healer’s contact and I contacted him immediately, in a little while he mail me back that i was welcome to his Herbal Home whereby all what i seek for are granted. I was please at that time. And i continue with him, he took some few details from me and told me that he shall get back to me as soon as he is through with my work. I was very happy as heard that from him, as i was just coming from my friends house, Dr Collins called me to go for checkup in the hospital and see his marvelous work that it is now HIV negative, i was very glad to hear that from him, so quickly rush down to the nearest hospital to found out, only to hear from my hospital doctor called Browning Lewis that i am now HIV NEGATIVE. I jump up at him with the a test note, he ask me how does it happen and i reside to him all i went through with Dr Collins. I am now glad, so i am a gentle type of person that need to share this testimonies to everyone who seek for healing, because once you get calm and quiet, so the disease get to finish your life off. So i will advice you contact him today for your healing at the above details: Email ID: [email protected] or you can also add him up on whataspp +2349036950737. CONTACT HIM NOW TO SAVE YOUR LIFE AND DOCTOR ALSO CURE ALL KIND OF DISEASE AND SICKNESS: [email protected] AS HE IS SO POWERFUL AND HELPFUL TO ALL THAT HAVE THIS SICKNESS
Ndiye chibwana icho ndi chipani
bodza la mtondo wadooka! my mcp is intact!
Kaya Zinamani. Koma Ine Ndibanja Langa Ndi A Mtundu Wanga Tidzasapota Chakwera. Profesor Odzichepetsa, Okonda Dziko Lake, Oganizira Anthu Osauka, Koma Inu Zineneni, 2019 Boma!!!!!
Mukulumana nokhanokha musanalowe pampandopo kkkk kaya
chakwela woyeeeeeee
chakwela woyeeeeeee
chakwela woyeeeeeee
inu inu mcp m’malo mogwirilizana mwayamba kulimbana zinthu zoponda pake
inu inu mcp m’malo mogwirilizana mwayamba kulimbana zinthu zoponda pake
inu inu mcp m’malo mogwirilizana mwayamba kulimbana zinthu zoponda pake
Ngat mukukanika kugwiriza nokha, nanga mutakhala pampando kuzakhala bwanji….
Ngat mukukanika kugwiriza nokha, nanga mutakhala pampando kuzakhala bwanji….
Ngat mukukanika kugwiriza nokha, nanga mutakhala pampando kuzakhala bwanji….
Chakwera MoFaya!!!!
Chakwera MoFaya!!!!
Chakwera MoFaya!!!!
This Guy z jst gud 4 nothing. Plz bring us a Vibrant leader who can revamp our Mighty MCP. Baba TEMBO the Puludzu was a great man, osati izi zopeperazi. Malawian politics needs Jack up folks, koma uyu akupha Chipani uyu ndithu.
Walemba mmadzi we r for Chakwera
Walemba mmadzi we r for Chakwera
Walemba mmadzi we r for Chakwera
Ena adyera musaononge Chipani.Panopa New MCP ndi chipani chokacho chilibe mbiri ya CASHGate,ndikuti New MCP

Ndithu ndithu
DPP iyi
Kkkkkkk Wina akuti amufuse Puludzu
Kkkkkkk Wina akuti amufuse Puludzu
Kkkkkkk Wina akuti amufuse Puludzu
Zayambika lero kkk
Zayambika lero kkk
Zayambika lero kkk
Ndikutha kuwona kuti 2019 mfumu ya mafumu ikudza kudzaweluza balimbanani muthela momo ndipo yesu akupezelani pompo pandalepo kaya

Kukanganira dziko limeni likupita kumapeto.pepani asawona inu.sunama mbale wanga
Peters threat. Zosatheka zimebezo.Yambani kaye convention yanu inu a dpp chifukwa anthu anavota molakwisa.
Anthu anavota molondola koma dpp inabela mavoti thats why tili ndi boma lopanda ntchito
Right.
kubwelakunso mudzalira chimodzimodzi .
Muyamba inu posachedwapaso.
Vote imakhala yolondola imapotoka ndi anthu adyera

Chakwera president 2019 hoyeeeeee
Chakwera president 2019 hoyeeeeee
Chakwera president 2019 hoyeeeeee
mhmmm…. mwati chani…?
mhmmm…. mwati chani…?
mhmmm…. mwati chani…?
Musova
Musova
kkkkkkkkk pyoooooooooo
kkkkkkkkk pyoooooooooo
kkkkkkkkk pyoooooooooo
sangakhale olo zitavuta maka
sangakhale olo zitavuta maka
sangakhale olo zitavuta maka
Amufunse Puluzu
Amufunse Puluzu
Amufunse Puluzu
Peterz threat
Peterz threat
Peterz threat
oh yes..he has to go is useless azikalalikila uko ni dyela lakelo
Kaya zanu izo agalatiya opusa inu. Anakunyengani ndan?
Kaya zanu izo agalatiya opusa inu. Anakunyengani ndan?
Kaya zanu izo agalatiya opusa inu. Anakunyengani ndan?
MCP woyeeeeeee
MCP woyeeeeeee
MCP woyeeeeeee
Msiyeni adzakhale President 2019
Msiyeni adzakhale President 2019
Msiyeni adzakhale President 2019