Trouble in MCP

Advertisement
Lazarus Chakwera

Lazarus Chakwera’s position as Malawi Congress Party (MCP) president has come under further scrutiny as the party’s officials have intensified efforts to remove him.

Lazarus Chakwera.
Chakwera: MCP members want him removed

Following an application by some members of the MCP, the High Court in Lilongwe has ordered the party to hold a convention in the next 90 days.

The members sought the court’s intervention after getting tired of the party’s leadership and its failure to solve wrangles within the party.

However, MCP spokesperson Jessie claims she is yet to be informed about the court order.

But lawyer for the disgruntled MCP officials insisted that they the court has granted them the order.

Advertisement

167 Comments

 1. Lero munthu wakuMalawi wasanduka chitonzo kwa anthu andale zomventsa chisoni anthu amene akuti ndiophunzira zochita zawo kuposanso amene sadaphunzire zosowa za dzikoli mukuzizidziwa bwino koma mukuchita chikuwawe anthu amene mwini wake Mulungu anawaika m dziko limeneli kukhala kwawo tsiku ndi tsiku inu andale kumenyana nkhondo yandale kuyambira Chaka cha 1994 zipani zolamulira kumangochita kampeni mmalo molamulira dziko kuba chuma cha anthu olimbikira omwe inu mumati osauka ganizani dzikoli lili ndi anthu abwini omwe mukuwasandutsa kukhala amphawi ndindale zosakhalabwino ngati ndi ndalama siyani ndalezo mudzikadya .ndalamazo osati kunzunza ntundu wamwini wake Mulungu anaukonda ndikuudalitsa ndintendere atsogoleri opanda nzeru mukufuna kusokoneza ntendere umeneu koma sizitheka mpaka mulephera koma wina adzalamulira dzikoli ndipo mudzasilira Komanso opanda zimaphunziro zonunkhazo zomwe za ononga dziko lathu lokongolali mpaka kutiposa Burundi ndi Rwanda

 2. [READ MY STORY. ON HOW I GOT MY HIV CURED].
  Truthfully, i was tested HIV + positive for the past 8 years. I keep on managing the drugs i usually purchase from the health care agency to keep me healthy and strengthen, i tried all i can to make this disease leave me alone, but unfortunately, it keep on eating up my life, this is what i caused myself, for allowing my fiance make sex to me unsecured without protection, although i never knew he is HIV positive. So last Two Months i came in contact with a lively article on the internet on how this Powerful Herb Healer get her well and healed. So as a patient i knew this will took my life one day, and i need to live with other friends and relatives too. So i copied out the Dr Collins the traditional healer’s contact and I contacted him immediately, in a little while he mail me back that i was welcome to his Herbal Home whereby all what i seek for are granted. I was please at that time. And i continue with him, he took some few details from me and told me that he shall get back to me as soon as he is through with my work. I was very happy as heard that from him, as i was just coming from my friends house, Dr Collins called me to go for checkup in the hospital and see his marvelous work that it is now HIV negative, i was very glad to hear that from him, so quickly rush down to the nearest hospital to found out, only to hear from my hospital doctor called Browning Lewis that i am now HIV NEGATIVE. I jump up at him with the a test note, he ask me how does it happen and i reside to him all i went through with Dr Collins. I am now glad, so i am a gentle type of person that need to share this testimonies to everyone who seek for healing, because once you get calm and quiet, so the disease get to finish your life off. So i will advice you contact him today for your healing at the above details: Email ID: [email protected] or you can also add him up on whataspp +2349036950737. CONTACT HIM NOW TO SAVE YOUR LIFE AND DOCTOR ALSO CURE ALL KIND OF DISEASE AND SICKNESS: [email protected] AS HE IS SO POWERFUL AND HELPFUL TO ALL THAT HAVE THIS SICKNESS…

 3. Ndingofuna kufusa kwa inu amene mukuti wasiya za god kodi amene amakhala mtsogoleri wadzi akapita ku gahena? Kapena amene amakhala mfumu ya mmudzi olo ya dela wa ku gahena? Ndikawona bible muli mafumu kunali mfumu Davite, fumu solomo osewa fumu kwitoliyo ndambiri Osewa moti samatumikira God? Mtsogoleri wabwino amasankha ndi mulungu siyizi zikuvutazi zosankhidwa mwachinyengo God sangakupatse mzeru zoyendetsera Dziko.FUMU SOLOMO Anapempha mzeru kwa God ndipo anayipatsa mzeru fumu solomo nde apa Chakwera alibe problem apeter ndamene ali ndi problem

 4. Ndingofuna kufusa kwa inu amene mukuti wasiya za god kodi amene amakhala mtsogoleri wadzi akapita ku gahena? Kapena amene amakhala mfumu ya mmudzi olo ya dela wa ku gahena? Ndikawona bible muli mafumu kunali mfumu Davite, fumu solomo osewa fumu kwitoliyo ndambiri Osewa moti samatumikira God? Mtsogoleri wabwino amasankha ndi mulungu siyizi zikuvutazi zosankhidwa mwachinyengo God sangakupatse mzeru zoyendetsera Dziko.FUMU SOLOMO Anapempha mzeru kwa God ndipo anayipatsa mzeru fumu solomo nde apa Chakwera alibe problem apeter ndamene ali ndi problem

 5. Mvuto lili ndi Nyasand ndilimeneri munthu kulakwitsa mmalo momukhazika pansi ndi kupeza mayankho koma achoke timanga malawi? Ndiye mkumati 2019 nkhuku yakuda boma masewela ake amenewa? .Abalamula matchona osadziwika kwawo omwewa nanga tithawila kuti

 6. Mvuto lili ndi Nyasand ndilimeneri munthu kulakwitsa mmalo momukhazika pansi ndi kupeza mayankho koma achoke timanga malawi? Ndiye mkumati 2019 nkhuku yakuda boma masewela ake amenewa? .Abalamula matchona osadziwika kwawo omwewa nanga tithawila kuti

 7. Chakwera asakhepo mulungu ndi zadziko,ngati mumamukonda chakwera muuzene zabwino za mbuye not zapadziko akutangwanika ine ake olamula ali pheeee,alilongosola dziko ndi peter basi

 8. Chakwera asakhepo mulungu ndi zadziko,ngati mumamukonda chakwera muuzene zabwino za mbuye not zapadziko akutangwanika ine ake olamula ali pheeee,alilongosola dziko ndi peter basi

 9. Munthu wa Mulungu wasiya kuwelenga Bible lero akuwerenga ma novelo….josephy nkasa pa repeat

 10. Munthu wa Mulungu wasiya kuwelenga Bible lero akuwerenga ma novelo….josephy nkasa pa repeat

 11. mulungu anatuma #yona kuti akalalikire uthenga wa yesu,, koma iye anakana kunyonzera mapeto ake chinsomba chachikulu chinameza #yona…..abusa musamale mdziko muno mulibe nsomba yomwe inameza yona koma muli zambiri zomwe zitha kukumedzani mpaka kuchotsa moyo…#bwerelaniKuCHURCH pastor plzzzzzz…

  1. Kikkkkki zoona fanny mu nyanjamo mulidi chinsomba alimo ache Felix Jumbe,ache dzoole mwale,ngati abusa akufuna aziwe zambiri kuti mmenemo muli ng’ona awafutse ache louis chimango,ulendo wa malemu zanja limodzi mwana wa pa dedza,che ntaba pa nathenje,che majoni pa lilongwe,che kutsaira.

 12. Kaya wina afune kaya asafune Chakwela ndi mtsogoleli wa chipan cha MCP bas winawe wagwanao , mungowadyela adpp o koma sizsintha kanthu kwachaaaaaaaaaaaaaaaa.

 13. M.C.P blood is M.C.P blood,ngakhale mutayankhula zotani simungatichotse pambuyo pa our loved leader D.r. Chakwera ndipo sikuyamba kumva nkholokolo zikuvutika ndi nsanje.They were there even in the tym of our former leader J.Z.U but they did not succeed.Ee! Mukunamatu,

 14. chipani cha MCP mulungu wamwambamwamba adachikana ,zomwe zikuchitikazi nzosadabwisa makamaka pa mbiri ya chipanichi.I always feel sorry for the man of god,Dr Reverend Chakwela for associating with the deadly ,bloody ,notorious MCP instead of serving almighty god. Malangizo anga ndi akuti papa Chakwela bwelelani ku gulu la mulungu mukamachita makani ndi MCP muzaona zomwe adaona aujeni aja for sure.

  1. Maxon What You Have To Know Is The Bible Says You Shall Know Them By Their Fruits,and If You Love The World And The Things Of The World The Love Of God Is Not In You

  2. Abale kunena zoona Zipani za PP ndi MCP zakhala zikulimbilana maudindo before and after elections.DPP ndi UDF kulibe mikangano kapena kutengelana ku bwalo la milandu. Makhalidwe a tsogoleli azipani za PP ndi MCP ndiomvesa chisoni ndi manyazi ,akulola bwanji kuti anthu agawanike. Oyambitsa mikangano amayenela kuchotsedwa muchipani. People can’t learn from the late Bingu.

 15. Munthu wa mulunngu kusiya kutumikira mulunngu koma ndale umasata chani? kodi nyimbo ya ndirande anglican ija unayimverapo yoti zimandikwanira? Bwanji osatengera chisanzo cha wachikulire a john chilembwe ? Do you you are wiser or luckier than john chilembwe?

 16. All these wrangles in MCP Leadership ndi DPP party tells lies to opposition party followers with money kuti agawanitse chipani knowing the party is getting more popular and power than DPP so to achieve it ama user system yoyambanitsa iyo nkukhala poterepo kumaonera as if they are not involved kuli achina Dausi,Ntaba amatha bodza

 17. kuthawa utumiki wa chauta kumapanga ndale mukuona ngati zingaende?? mukawerenge nkhani ya Yona, akuluwa anathawa ntchito ya chauta

 18. kkkkkkkkkkkk………pliz mcp veterans,mutenge political holiday, which will earn you a clean history in politics. …mwakula nd it seems like you dont know where you are going nd how to move from where you are………chipanichi chakalamba ,kapena find a new leader,koma from another region ,osati Achewa,mukumachulusa mapokoso and it seems like ndinu anthu olongolola kwambiri.

 19. Kkkkkkk baibulo limanena kuti masiku otsiliza kuzakhala kucita zinthu zosiyanasiyana kuzakhala mtundu ndi mtundu kuwukilana ndizitu kaya makandanani

 20. [READ MY STORY. ON HOW I GOT MY HIV CURED].
  Truthfully, i was tested HIV + positive for the past 8 years. I keep on managing the drugs i usually purchase from the health care agency to keep me healthy and strengthen, i tried all i can to make this disease leave me alone, but unfortunately, it keep on eating up my life. So last Two Months i came in contact with a lively article on the internet on how this Powerful Herb Healer get her well and healed. So as a patient i knew this will took my life one day, and i need to live with other friends and relatives too. So i copied out the Dr Collins the herbal healer’s contact and I contacted him immediately, in a little while he mail me back that i was welcome to his Herbal Home whereby all what i seek for are granted. I was please at that time. And i continue with him, he took some few details from me and told me that he shall get back to me as soon as he is through with my work. I was very happy as heard that from him, as i was just coming from my friends house, Dr Collins called me to go for checkup in the hospital and see his marvelous work that it is now HIV negative, i was very glad to hear that from him, so quickly rush down to the nearest hospital to found out, only to hear from my hospital doctor called Browning Lewis that i am now HIV NEGATIVE. I jump up at him with the a test note, he ask me how does it happen and i reside to him all i went through with Dr Collins. I am now glad, so i am a gentle type of person that need to share this testimonies to everyone who seek for healing, because once you get calm and quiet, so the disease get to finish your life off. So i will advice you contact him today for your healing at the above details: Email ID: [email protected] or you can also add him up on whataspp +2349036950737. CONTACT HIM NOW TO SAVE YOUR LIFE AND DOCTOR ALSO CURE ALL KIND OF DISEASE AND SICKNESS: [email protected] AS HE IS SO POWERFUL AND HELPFUL TO ALL THAT HAVE THIS SICKNESS

 21. Kaya Zinamani. Koma Ine Ndibanja Langa Ndi A Mtundu Wanga Tidzasapota Chakwera. Profesor Odzichepetsa, Okonda Dziko Lake, Oganizira Anthu Osauka, Koma Inu Zineneni, 2019 Boma!!!!!

 22. This Guy z jst gud 4 nothing. Plz bring us a Vibrant leader who can revamp our Mighty MCP. Baba TEMBO the Puludzu was a great man, osati izi zopeperazi. Malawian politics needs Jack up folks, koma uyu akupha Chipani uyu ndithu.

 23. Ndikutha kuwona kuti 2019 mfumu ya mafumu ikudza kudzaweluza balimbanani muthela momo ndipo yesu akupezelani pompo pandalepo kaya

 24. Ndikutha kuwona kuti 2019 mfumu ya mafumu ikudza kudzaweluza balimbanani muthela momo ndipo yesu akupezelani pompo pandalepo kaya

 25. Ndikutha kuwona kuti 2019 mfumu ya mafumu ikudza kudzaweluza balimbanani muthela momo ndipo yesu akupezelani pompo pandalepo kaya

 26. oh yes..he has to go is useless azikalalikila uko ni dyela lakelo

Comments are closed.