The United Democratic Front (UDF) has said it is against calls for President Peter Mutharika to resign arguing that the Democratic Progressive Party (DPP) administration can solve the country’s problems.
UDF spokesperson Ken Ndanga told the media that the party wants to help DPP in running the country hence it does not believe in giving government ultimatums.
The UDF spokesperson was reacting to calls by Malawi Congress Party, People’s Party, and AFORD for Mutharika to resign saying he has failed to solve the country’s economic challenges.
According to Ndanga, the DPP cannot run the government alone since it tackles a lot of things which are of public interest.
He added that calling for Mutharika’s resignation is not a good idea since government needs the support of other political parties in order to deal with the economic problems the country is grappling with.
On why his party was not represented at the rally which the other opposition parties organised on Sunday, the UDF spokesperson said the party was not invited hence had no way of knowing the aim of the political rally.
If there are new vote let’us just vote 4 (boma loti silidalowepo pamalawi chifukwa zipani zakale njira zose amaziziwa zobela ndalama so its better to change.) (mimi kutoka ku tz)
Silly
Though a leader of UDF is in a cabinet, but they are right.
Though a leader of UDF is in a cabinet, but they are right.
UDF yakha m’boma kwa zaka khumi. Ikudziwa bwino lomwe vuto la Malawi.
UDF yakha m’boma kwa zaka khumi. Ikudziwa bwino lomwe vuto la Malawi.
Azapeleka yeka Peter mutharika ku udf zaka zeke zikakwana tikudikila tupele azalamule basi
Azapeleka yeka Peter mutharika ku udf zaka zeke zikakwana tikudikila tupele azalamule basi
udiefu yake iti
Vandale ivi vabwekabweka, palije icho ningayowoyapo vizeleza viwanthu ivi.
Udf nde chianinso? Palibe cha nzeru anganene awa, mu ulamuliro wao adabweretsa njala ya dzaoneni mdziko lino komaso kuba too much, ngati lero tikukamba za cashgate inayambitsa ndi Udf, ndalama za ma Donors kumangolowa mu account ya president zoona? Dpp nde mbola, mavuto onsewa wina nkumati alibe problem. Winanso nkumati olo atasintha president mavuto sangathe, PP inasintha zinthu Bingu ataononga in 1 year, njala, kukwera kwa zinthu beyond our expectations wina nkumati zili bwino zoona? A change of gvt is overwhelmingly needed for suffering Malawians.
Amalawi azanga kunena zoona umphawi unatizowera komanso sitimalikonda dziko lathu .pali chosapotera apa anthu mmene akuzuzikiram. Boma na likuphera kulipira mfumu k2500-R50 ya Rsa nchani chimenecho.Anthu inu zoona mmene akuondera amalawi chifukwa cha umphawi wina nkumati msiyeni akulamula bwino zoona?. Guys school yanuyi siyikuthandiza ndizochitika za dziko anthu kuchimiziku akuvutika koopsa.Ine ndinali ku Mlw koma ndinaona anthu akuvutikira iiiiiiii zoopsa . Kkkkkk or inu amalawi mumasankha zimenezi bwanji kodi mmmh simuona.kuphunzira ndi utsogoleri nzosiyana .
UDF ndi chipani chotsutsa chokhacho chimene chili chozindikila m’Malawi muno.Ndi chokhachonso chimene chingathe kuyendetsa bwino dzikoli chitalowanso m’boma.Atsogoleri ake ndi okhwima nzeru,opanda dyera komanso okonda mtendere ndikufunila dziko lawo zabwino.Osati MCP,PIPI,AFORD,atsogoleri ake ndi adyera koopsa,osakonda dziko lawo koma maudindo basi.Mufune musafune,DPP kutuluka,tidzalowesa UDF,eetu!
Dziko silituluka pa hr, min,day, aweek, amonth even ayr. To run Country is deffer than running acompang,bussiness, family or even club so when u think u can manage mmmmmmmm u will see the same Malawi goimg for war soon
Ine ndilibe problemu kaiwe UDF and DPP tili rimodzi kkkkkkkkk muku chedwa.
He wanna do. To resign
Kodi Chilipo?Bootlicker.
Dpp.udf are both parties crooks they can not solve problem in cauntry because they have one thing that its causes poverty
DPP BOMA
UDf iyiwale ndiyomwe inationongela zinthu.
Akulu akulu tamayamikani inu nthawi ya UDF chimanga sichinakwere mmene chakwerera panopa iwe ukunyoza UDF ulibe nzeru DPP malibe chimene ikupanga panopa.
Atupele sold the UDF to DPP so what do you expect from them?
maganizo anga ndaakuti peter muthalika aimilile chigawo chakumwela komanso chakwela aziimilila chigawo chapakati nde mai joice banda akaimilile chigawo chakunpoto sono ineyo TONY CHIRWA ndikhale oyang’anila athwatatu amenewa akakumana ndimamvuto mzigawo zawo ine monga tate wankulu ndiziwona mene ndingathesele mavuto omwe angapezeke madelawo, mukuwona bwanji pamenepa simaganizo abwino amenewa akuluakulu.

yelloooooooooooo ilowe bwalo basi awa zawakanika ndithu.
yelloooooooooooo ilowe bwalo basi awa zawakanika ndithu.
Tigwirane Manja? Tizigwirana Manja Wina Akufuna Kumwalira,mungonena Chani? Udf Zonse Zikuchitikaz Sakuona Pano Passport K80,000 From K48,000 Chilungamo Chimenecho?
Tigwirane Manja? Tizigwirana Manja Wina Akufuna Kumwalira,mungonena Chani? Udf Zonse Zikuchitikaz Sakuona Pano Passport K80,000 From K48,000 Chilungamo Chimenecho?
The Muluzi’s Are Clever And Better.Thats The Only Way They Can Destroy Dpp And Get And Snatch Their Power Back From The Mutharikaz.
Vindere vyakufikapo wa udf mose na dpp
A Udf na dpp ndimwe vindere vyakufikapo
Not only udf,but all wise pple aswell.why steping down?greedy dogs like to say so.is it fair to put blame to dpp on the situation the country is facing?what connections are there? Learn to speak the truth to shame the devil.every tyme u entatain the satan instead of praising God.shame.
Zimaoneka zophweka zanko akamalamulira ngat mu2 ukulephela kuyendetsa cipani cako nde kulibwanj dziko tiyen tingogwilana manja titukule dziko la2 osat kumango lodzana dzala tiyen tidzuke amalaw kwacha

Is there aparty called u d f in Malawi ? If yes , who is the leader of udf party and where is
Adyesedwa cigaba agalu
UDF mbuziiiiiiii
Sometimes I tend to wonder how on earth can MCP ever have a chance to rule Malawi again??? Never and I swear Never.
What else can udf say,,,it is last kicks of a dying horse
ine nzapita kumwamba posachedwa ine,,,,ine nzapita kumwamba posachedwa pena lero Yesu akubwera pena mawa Yesu akubwera ine nzapita kuchanya posachedwa
Mayaz resign for what??
udf yopanda nzeru ati akufuna u vp, mbuli ayawo
kodi paja kuli chipan chotchedwa udf kkkkkkkkkl
UDF ndi kanyama kanji kodi?
Mukudya nawo simungaone chifukwa choti achokele
United Developed Fools {UDF} Toilet tissue ya alomwe, akasetera will throw you away without looking into the great job you are doing now. without vision the colour yellow will soon disappear.
UDF Mutha ngati makatani inu..maplan adakuthelani
It’s almost impossible to bite a finger that feeds you
Bravo UDF,For sure current situation is not for DPP but it is a nation issue of Malawi
UDF knows wats neither good nor bad. even if the pasta won 2014 election., hunger wud av be a problem azwel. dont hate DPP. if you r clever enough tel pple other issues dat u wil manage after wining 2019 election not hunger. Just pray for Malawi n not criticising our president. Tinamuvotera coz ma qualities onse a leadership ali nawo…
UDF ndendaninso ameneyu.
Utiki utiki, kkkkkkkkk, eti chipani cha Dad! Lero UDf yangokhala ngati mtengo wa kachere, kumera pa unzake! UDF, UDF lero? Zakale kale izi, chipani cha UDF, chidatuluka m’boma ndi mwini wake chair basi!
Kodi mulipobe??????????
Mmmmmm inu a UDF ndiye ai simudzalikowaso boma inu
Kodi inu mungoti nkhaza za Mcp munaliko inu thuza lenileni zongovela akuti tatiwu iformation yose ya MCP Tandiwuzeni Mp ali wavula zakale
olo atandithira doom nkamwa
olo atandithira doom nkamwa
olo atandithira doom nkamwa sindingavotele chipani cha nkhanza cha MCP. Ndikaganiza za abale amene chipani chimenechi chidapha ndikuzunza! !!!!!!!
olo atandithira doom nkamwa sindingavotele chipani cha nkhanza cha MCP. Ndikaganiza za abale amene chipani chimenechi chidapha ndikuzunza! !!!!!!!
Wena Fotseke kkk oloni Agogo ako tafusa matumba achimanga omwe amapezeka mnyumba mwawo evin feterezar amalandila angati tafuse kapena ulibe agogo eti? Mkoneka ukutero tandiwuze ndangati anafapo ndinjala mulamuliro wa Big man Dr H kamuzu Banda mowanyadila timatero ife akubanja.nde Tandifuse ulamuliro uti anthu sanafepo ine siwandale koma ndine zika ya Mw

Kkkkkkkkk mukulira ma cashget
Dats a welcome development,this country needs big brains to comment on issues of public interest,not mbuli zophunzira as chilima said.
Sikuti ngati mukuti asachoke pampando ndiye kuti pali chamzeru chomwe chikuchitika ai.Koma ngakhale atachoka pampando angabwere ndikusintha zinthu akhala ndani ndipo ali kuti?Poti onse ayesedwa kale palibe wamzeru.Basi tingokweza maso kumwamba basi
Koma mitu yanuyo imaganiza?????? Mukundiuza kt kupanga resgn njala mavuto zitha??? Mawa muzakhala ndinu dziko likukunyerani kuyendesa…….
opusa iwe amuthandize mzilu naweso unazolowela kukanda pathako ndi umphawi chupiti achoke akapume oko mundu muja munayamba kuvutikila ndi mkulu wake muja mukavotelaso bwampini ngati ameneyu kudzapitilizaso mavuto
You are part and parcel of gvt side
Mr speaker sir, why can u pliz invoke section 65 on these UDF guys as they have left their seats to government seats? U r unfair pliz
Kkkk ukuba ndiokuba bass
Akuyenera kutelo basi.
UDF moto moto, DPP woyeeeeeeee
dead UDF
udf chipani cha mbala ndi zigawenga chikutinso chani apa?malawi wanga wafikadi pododedwa ngati mpira ambuye tangobwerani mudzaweluze
[READ MY STORY. ON HOW I GOT MY HIV CURED].
Truthfully, i was tested HIV + positive for the past 8 years. I keep on managing the drugs i usually purchase from the health care agency to keep me healthy and strengthen, i tried all i can to make this disease leave me alone, but unfortunately, it keep on eating up my life. So last Two Months i came in contact with a lively article on the internet on how this Powerful Herb Healer get her well and healed. So as a patient i knew this will took my life one day, and i need to live with other friends and relatives too. So i copied out the Dr Collins the herbal healer’s contact and I contacted him immediately, in a little while he mail me back that i was welcome to his Herbal Home whereby all what i seek for are granted. I was please at that time. And i continue with him, he took some few details from me and told me that he shall get back to me as soon as he is through with my work. I was very happy as heard that from him, as i was just coming from my friends house, Dr Collins called me to go for checkup in the hospital and see his marvelous work that it is now HIV negative, i was very glad to hear that from him, so quickly rush down to the nearest hospital to found out, only to hear from my hospital doctor called Browning Lewis that i am now HIV NEGATIVE. I jump up at him with the a test note, he ask me how does it happen and i reside to him all i went through with Dr Collins. I am now glad, so i am a gentle type of person that need to share this testimonies to everyone who seek for healing, because once you get calm and quiet, so the disease get to finish your life off. So i will advice you contact him today for your healing at the above details: Email ID: [email protected] or you can also add him up on whataspp +2349036950737. CONTACT HIM NOW TO SAVE YOUR LIFE AND DOCTOR ALSO CURE ALL KIND OF DISEASE AND SICKNESS: [email protected] AS HE IS SO POWERFUL AND HELPFUL TO ALL THAT HAVE THIS SICKNESS.

Atupele was given ‘CHIBANZI’ so its obvious that UDF will always support DPP
Atupele was given ‘CHIBANZI’ so its obvious that UDF will always support DPP
UDF can’t do anything against DPP coz they r married n we don’t want Udf anymore even wen baby is the driver
UDF can’t do anything against DPP coz they r married n we don’t want Udf anymore even wen baby is the driver
A udf ndinu mnayambisa kuba muboma.malonda onyasa aziwalo za anthu,azimayi kudulidwa mabele and noboday was arrested.malawians hvnt forgotten ur mess.just keep qwiet and for 2019.
A udf ndinu mnayambisa kuba muboma.malonda onyasa aziwalo za anthu,azimayi kudulidwa mabele and noboday was arrested.malawians hvnt forgotten ur mess.just keep qwiet and for 2019.
It is simple to judge than to rule more fire Dpp
It is simple to judge than to rule more fire Dpp
Lucius Banda Sangachite Nawo Zopusa Zotere.. Lucius Ndiye Mtsogoleri Wa UDF Wodalirika, Wosati mbuli zinazi zotengeka ndi madzi a mu cup
Lucius Banda Sangachite Nawo Zopusa Zotere.. Lucius Ndiye Mtsogoleri Wa UDF Wodalirika, Wosati mbuli zinazi zotengeka ndi madzi a mu cup
Akanayankhula lucius banda bola zikanamvekako, ku udf ngati kwasala munthu ndiyeyu basi zinazo mbuzi
Akanayankhula lucius banda bola zikanamvekako, ku udf ngati kwasala munthu ndiyeyu basi zinazo mbuzi
Go to hell! UDF.
Go to hell! UDF.
Inu a udf zanu zinatha tasiyirani anzanu a dpp
I think wonderson is right that Udf is well organised because it is bzy supporting government to develop this country. Mcp and Pp’s is bzy decampaining the ruling party. Me wonder, why Mcp bzy now? Does it means that there is no time for development but campainging any time? Last time Dpp yabela Mavoti kenako, Federalism, iyayi Peter atule pansi, pano Impitchment che Chakwera power hungry chonchi bwanji? Kungoti pyeeee!! Nkhaza za Mcp yakale basi. To much voiceless like un empty tine. We are following U with interest.
Ndiponso Nkhanza zimene a MCP akuwonetsa pano zikusonyeza kuti atati atenga boma amalawi tizdazuzidwa zedi ngati mene makolo athu adazuzidwila
Mbale iwe ndiye tikuona mofanana . Mr chakwela akuona 20190 kuchedwa ndichifukwa akufuna kulowela pawindo m’mboma
Mbale iwe ndiye tikuona mofanana . Mr chakwela akuona 20190 kuchedwa ndichifukwa akufuna kulowela pawindo m’mboma
Not that dpp can solve problems but so that you can continue fattening your bellies. Clueless selfish politicians.
Better #MCP koma UDF ayi plz eish eish eish?
TO THE WHOLE WORLD NIGERIAN PEOPLE HAVE DEVELOP A SYSTEM WHEREBY THEY SAY THEY CURE HIV AND AIDS, CANCER AND MORE THEY SAY THEY ARE HERBALIST THEY PUT THEIR EMAIL ADDRESS PROTECTED AND THEY USE WHATSSAP NUMBER WHEN YOU CONTACT THEM THEY ASK FEW QUESTIONS THEY ARE MANY BUT THEIR CONVESATION IS THE SAME THEIR COUNTRY CODE IS +234 THEY CREATE A FAKE ACCOUNT OF A WOMAN ON FACEBOOK AND THEY USE THE INFORMATION LIKE THE FOLLOWING [READ MY STORY. ON HOW I GOT MY HIV CURED]. Truthfully, i was tested HIV + positive for the past 8 years. I keep on managing the drugs i usually purchase from the health care agency to keep me healthy and strengthen, i tried all i can to make this disease leave me alone, but unfortunately, it keep on eating up my life. So last Two Months i came in contact with a lively article on the internet on how this Powerful Herb Healer get her well and healed. So as a patient i knew this will took my life one day, and i need to live with other friends and relatives too. So i copied out the Dr Collins the herbal healer’s contact and I contacted him immediately, in a little while he mail me back that i was welcome to his Herbal Home whereby all what i seek for are granted. I was please at that time. And i continue with him, he took some few details from me and told me that he shall get back to me as soon as he is through with my work. I was very happy as heard that from him, as i was just coming from my friends house, Dr Collins called me to go for checkup in the hospital and see his marvelous work that it is now HIV negative, i was very glad to hear that from him, so quickly rush down to the nearest hospital to found out, only to hear from my hospital doctor called Browning Lewis that i am now HIV NEGATIVE. I jump up at him with the a test note, he ask me how does it happen and i reside to him all i went through with Dr Collins. I am now glad, so i am a gentle type of person that need to share this testimonies to everyone who seek for healing, because once you get calm and quiet, so the disease get to finish your life off. So i will advice you contact him today for your healing at the above details: Email ID: [email protected] or you can also add him up on whataspp +2349036950737. CONTACT HIM NOW TO SAVE YOUR LIFE AND DOCTOR ALSO CURE ALL KIND OF DISEASE AND SICKNESS: [email protected] AS HE IS SO POWERFUL ONCE YOU ARE IN CONTACT WITH THEM THEY WILL ASK THE FOLLOWING QUESTIONS YOUR NAME WHERE ARE YOU FROM KIND OF DISEASE YOU ARE SUFFERING FROM HOW CAN THEY DELIVER THE MEDICINE TO YOU THEY WILL ASK YOU TO SEND THEM MONEY $200 DOLLARS FOR PREPARATION OF THE MEDICINE THEY SAY THEY WANT TO BUY ITEMS FROM THE SELLER THEY GIVE YOU THEIR WESTERN UNION ACCOUNT ONCE YOU SEND THE MONEY THEY BLOCK YOU ON WHATSSAP THIS IS HOW THEY ARE STEALING MONEY FROM PEOPLE THEY PUT THEIR STUPID STORIES ON NYASATIMES, MALAWI24 AND MANY PLEASE DO NOT SEND YOUR MONEY TO THEM TOGETHER WE CAN END THIS LETS FIGHT BACK TO THEM BY FIRING BACK WITH ……. PLEASE DO NOT SEND MONEY TO THEM FROM NIGERIA POLICE SERVICES AND THEY ARE HUNTING THEM USING THEIR MOBILE
UDF inatha basi akungolira
A udf akudya ndi Peter sangavomeleze kuti apange resign
Spurs 2-2 Arsenal. Leicster pa top
MCP OYEH!
mmmm UDF,mseru. mmmmmUDF pioneers of Cashgate, UDF accidential President,Accidential Party.
nde pp ndi mcp simbavaso? kdi madolo simukuwaziwa asogoleri achi mw eti.
mbuli ya DPP mbuli ya UDF nosenu mlibe nzelu mwawabela amalawi kwakwana bolan BINGU anal hello
Looool UDF is worse it can happen again to take over your time is gone.why can we try MCP mayb things will change not UDF
Udf ilipo kodi ? Ndimaganiza kuti chinatha ngati makatani
the only better guy in UDF is Lucius Banda ,
the only better guy in UDF is Lucius Banda ,
Indedi ayise…koma ndi mmene dzilili apa boma ilili..bolaso UDF IJA ibweleleso..if is not came back..mo of malawi is going to be xpre..nanga taonani Randi aganest kwacha one to..fortyfive thats no seccc man UDF CAME BACK .Brathers

Anthu otoletsa ma bin inu a UDF jst blind following that idiot dude fucked off ! Try to reason mutulukamo shortly bomamo demet !
Anthu otoletsa ma bin inu a UDF jst blind following that idiot dude fucked off ! Try to reason mutulukamo shortly bomamo demet !
Kodi mavuto anjalawa athu atengelapo popangila kanpeni kutitola eti inu a UDF mukafune owapusisa musiyeni amalizise machimo akewo kodi anakakhala ntumiki wina walosela kuti pitayo amwalila afta 30dayz ndi angati omwe munakabwela kumati eee ine ndifa malo mwa pita nsiyeni zikunvuta muthu chifukwa amalawi timaphwekesa tchito yanzathu mmalo moti timuthandize nzelu koma kutukwana tizikhala chonchi npaka kale inu mavuto onsewa pomwe achokela simukupaona chaka chatha nvula inakokolola mbewu chaka chino nvula ikuvutavuta nde inu a UDF basi matako manganemangane kuti mukwanisa zithu mukazitenga kuti osamatitola amalawife ndife nzika eni thaka zichepe mudikile 2019 muzasakhidwe bwsi not tikwanisa kukwanisa chani kubaso

Man mukumvesa koma boboh nkhaniyi
english yavuta kuimva apa pepani ofunika school kaye a UDF sikugwilizana ndi maganizo oti prezideti atule udindo pansi mwina. mwina zavekano pamenepo
english yavuta kuimva apa pepani ofunika school kaye a UDF sikugwilizana ndi maganizo oti prezideti atule udindo pansi mwina. mwina zavekano pamenepo
UDF?? kkkkkkkkkkkk! sibola apitilize a DPP omwewo! Mbuli za UDF zingalamule boma?
UDF?? kkkkkkkkkkkk! sibola apitilize a DPP omwewo! Mbuli za UDF zingalamule boma?
The problem with you politicians is that you say let us join hands when there is crisis. But when you open a 5km road you eveen climb Mulanje mountain and say we are the only one. So being the only one what are you crying for? Apologise for the wrong doing then seek for assistance.

Nalema na DPP na UDF zipani zonsezi ni zakuba. MCP nde game!!
Nalema na DPP na UDF zipani zonsezi ni zakuba. MCP nde game!!
UDF motomoto za DPP zathu zomwe izi
UDF motomoto za DPP zathu zomwe izi
Malawi is dying zitsilu zina zizikavoteraso olakwikawo likely kuti simzavotaso zamanyi
Not surprising, one of their own is in cabinet.
Zachabechabe
Mbuli za UDF dyela basi stumped pipo
Same paties r useless, the don’t think for 2morrow
2019 Atupere
Bola Lucius akhale president wa UDF Atupele aaaaa dyera anabetsa chipani
Progressive opposition
Ndi dziko lonse koma poti wako ndiamene ali pamphuno
chipani ichi anthu ake amadziwa ndale,
chipani ichi anthu ake amadziwa ndale,
Fuck UDF
Kkkk kodi UDF idakalipo mmayesa inamezedwa ndi DPP!
UDF WOYEEEEE
UDF the party that I personally supported and even convinced my many of my friends to join without seeking any recognition is now going into extinction like makatani
u.d f ndi chani nangati kuli chipani chopanda tsogolo ndi u.d.f chipani cha dyeral
devu zosezo kudandaula za njala mpaka liti. waulesi asadye . musiyini amalize 2019 tione ngati mungawine. kulalata sikukupindulilan. mzakomoka kuzafika pa chisankho pitala kuztengaso boma. inu mukuchedwa ndi kulalata .
UDF and DPP are both parties of crooks and are the parties who have worsened our poverty here in Malawi. They have been robbing us Malawians
Yes
Inenxo ndilibe polobulemu,coz palibe munthu azathetse mavuto olo chipani sichizathetsa mavuto,ndiufumu wa mulungu wokha utazathetse mavuto,moti munthu wanzeru ndikumalimbana ndi andale akuziwa kt palibe chomwe angachite,masiku osiliza kuzakhala njala mumaona ngat malawi masiku osiliza sizakhalako njalayo?kikkkkk ana anjoka inu mukanganilanj pomwe mbuye wanu anakuuziranitu zizindikilo za masiku osiliza
meaning that iwo sangatheeeee kkkk
Chipani kutha ngati makatani
Ok bt nalema nandale zapamalawi ine
…….UDF is ryt, lets unite and find a way forward to solve this crisis, removing president will worsen the situation..! let president go to u.s.a and beg for kenya maize and he must declair malawi a state of emergency coz of this hunger….thats my contribution as of now….zikomo
Ngakhale Litakhala Banja Kuti Lafika Poter, I Don’t Think It’s Proper To Ask Those Who Admire Your Wife To Assist U To Resolve Ur Family Problems.Nditakhala Ine, I Can Just Give Chance To My Friiends To Try .
udf inatha ngati makatani
kokoliko zakalekale , kokoliko lero!
Iwe atupele mbuyako anatisiya mchipululu,iwe ndi mbuyako ndinu mbatata bolanso lucius
I agree its high time we decided where we belong we better agree and belong to one understanding. Better be Democrats, Republicans, Liberal. We waste time for there is no way a President can resign we better decide
Amalawi tiyeni tisegule maso ndikuyamba kuganiza mwanzeru. Inuuu simalawi yekha amene akukumana ndimavuto osiyanasiyana, koma taonani mmene anzathu akuchitila kukonza zinthu. For insance dziko la china nalo likukumana ndimavuto ngat omwewa. Kma aku-china akambirana kugwira ntchito limodzi kut asove mavuto awo. Pamenepo mmalawi akungong’ambika kukamwa ali “achoke-achoke” nde mpaka liti kkkkk malawi fuko langa lokondeka tatsekula maso ako ndikuyamba kuganiza mwanzeru. Pamavuto iwala zandale koma kupeza njila mmm
Kumalawi ndizobvuta kugwilira ntchito limodzi coz anthu ake ndiodzikonda.Zikamayenda amadzitukumura kwambiri ndipo amaona ngati mmdziko muno mulibenso ena amnzeru,zikawasokonekera ngati mmene zafikiramu ndipamene amafuna opanda nzeru aja kuti apange contribute their views.Bvuto kumalawi atsogoleri olamura, amafuna anzawo zinthu zikathina.kkkkkkkk musova.
Ndimulungu ekha amene angakwanise kuthesa mabvuto onsee otsati munthu ai, palibe wina koma tingosamira kwa mulungu kuzera mwa mwana wake yesu khristu basi
nkhani koma imeneyo makape muli m’madzi woyeeeeeee, woyeeeeeee ,woyeeeeeeeeeeee , iwe ndi iwe kagwereni uko!
http://cashpackets.com/link.php?ref=74506
UDF kumeneko ndiye timati kubwela.A UDF akudziwa kusatila ndale m’mene zimayendela inu ndikukumbutseni kuti 1994 UDF defeated MCP and AFORD with a wide margin.After 5 years,Bakili Muluzi defeated mgwilizano wa MCP ndi AFORD.Late Bingu did the same under DPP. MCP ndi chipani chogwedezeka PP ndiye idkomoka kale,it it tainted with cashgate.There is nothing you can learn from MCP only nkhaza ndi kulalata.PP Uladi Mussa will teach you new tricks of how to steal money from the capital in seconds.Atupele stay where you are learn how to govern people of malawi so that in future never make the mistake like your father did seeking for the third term. DPP well orginised,UDF is organised no defections like PP..
UDF ndidilu!!!mcp & pp no moo!!!kkkkkkki
Kodi mumatafuna zintuwitsa eeti, ithink its now good time for we the youth to show our anger with mass demo. Its not fair 80thousand passport, some one should resign no future for poor youth
He’s not showing styles if dictatorship BUT we are making him to be a dictator?
UDf chipani chosamva,never learn from its past mistakesBakili anagulitsa boma kwa dpp,lero mwanayu wagulitsaso chipani kwa dpp yomweyo,Rip udf
Nonsense UDF
The UDF is against resignation of Peter Because Its Leader Atupele Has Also Told O Resign By UDF supporters. Atupele Anangowagwiritsa Ntchito Ma Sapota A UDF mpaka pano samaonekanso koma pa lampeni amkati amaganizira moyo wa anthu osauka koma olo za njalayi sanalankhule bola zake ndi bambo ake zikuyenda.Atupele Si Wandale Koma Wa Dama Amangofuna Maudindo Osati Kukhazikika Pa Ndale .Zoona Mu Ndale Combination Angakhale UDF ndi DPP .
wamisala anaona nkhondo…
aaaaaa UDF my foot so ashamed of that party u cowards couldn’t stand the heat nde makadzipatika kwa Pharaoh.
Big up Mr Lucius Banda u are the true son Of Yellow remaing
Lucius ndale anaziyamba kalekale, amadziwa chimene akupanga ndipo amapanga zokomera amalawi onse,samanyengelera,ndiolimba mtima yes he is true soldier of the land,Malawi.
Mm wise people support the point UDF is saying. If we say muthalika should resign we should consider both positive and negative consequences. It is not only Malawi facing these problems but look at how other countries are working to solve there problems!
China is one of countries facing economical problems but the have organised a meeting and descus how all together will work and agree to work to gether. Pamenepo m’malawi angong’ambika kukamwa ndikukuwa “achoke!! Achoke! Instade of trying to work together kkkkk malawi country dzuka malawi dzuka
Zimenezo amalankhula ndi anyawu, ife eni udf sitingalankhule zopepela ngati zimenezo. Udf ndi Dpp woyee
UDF
Ma banzi ali mkamwa angayankhulenso?
Kodi UDF idakalipo?
Galu samauwa mbuyache.
Start visiting villages…pipo are dieing of starvation, go to RTD….go to immigration, go to the filling stations everything is high today…….& this lyf is hard to live…..cos of this poor adminstration…. (DPP)
go and study the Bible thoroughly.
Wina olo afune olo adzafune 2019 udf boooooooooooooooooooooma
UDF you are right. Soon it will solve economical problem by raising fuel price, Raising passport from 48,000.00 to 80,000.00
Kkkkkkkkkkkkk. So funny Boma Ilo!!!!!!!! Lyo lyo.l
Stop talking nonses #UDF
please!
Udf oyeeeeeeee 2019 kuti waaaaaaaa oyeeeeeee sanasanali tembo anali kumangochi kuma kwacha kwacha mixalaeti
Mukudyeratu zanu
Paja udf ndi dpp,nawoso alibe problem
Mbalame zeni zeni!!
UDF is just a bunch of sellouts now
Afusj inu.
Kodi UDF ilipobe
Agaru inu!
mwati bwanji?
What is UDF?
Wat else u can say ,atidye nawo inu
Big up….Udf
Kkkkk
UDF nde yiti so? Inatha ngati ma curtain paja
how can thiefs solve the problems? Munamatu
Anzathu odala mukumwa madzi am’botolo anzanu ife tikusowa yogula wokoman ,nkumati zikuenda mukumuonetsa ngati wanzeru komatu mutati mufike kumidzi kuno nkuona mmene anthu akufela ndi njala simkadalankhula zoti pitala cannot resgn , makamaka inu a UDF amene mukudyela tebulo limodzi munthalika mudzaona polekela tikatenga boma ife otsutsafe.
Paja Gane ya #BULLETS ndi ZIM/DYNAMOS yatha bwa..:D?Zandalezi abale
Does UDF stil exist.
A Chair anati u president siufunika a Bongololo fififi this is sirious business bwana Peter mwaonatu?
Kodi do we have UDF in Malawi? Only Lucius banda
Aliyense kupereka maganizo ake, wina akuti ayi, wina akuti eya, tisawatsutse or kuwatukwana ayi. Nafenso tipereke maganizo athu.
Am not a UDF member, but thumbs up “UdF”.
Am A Ud3 Supporter But I Wil Agree With U Only If U Will Iie To Me What U Wil Do After Resignation Of Pete Mathanyula Ka Njala,cz U Sold The Party To Dpp,by The Way U A All Fools,
UDF ndiye inatidyetsa mizu ya nthochi sindingaiwale ine mix Muluzi fake money end of that anatisiya mu chipululu m’malo mokafika kukenani ndiye tingakumveni pomwe tinapempha Nsomba inu ndi kutifungatitsa chinkhanira means Dpp
umatha ayise!
same to u
Hahahaha adyelao kkkkkk
UDF DPP ZIIPANI ZA MALAWI
ya dziko ndianthu ake shame somtyms i wonder anthu mumadandaula magetsi akathima kulibwanji nanga ife anthu akumuziwa mavutowa tikukumana nao bwanji pano mukuti mulibe polobulemu hu mulindiumunthu koma wina kumavomereza zopusazo shame think ov our granny omwe aliku midzi mowoyu u think akumva chimodzimodzi mukumveramo mulibe chisoni ndinthu if i may ask since the dpp government come to power asinthapo zitizo
Kukweza misonkhotu abwana
sibwino anganizire anthu amene ali amalawi ovutika ndalama akazitenga kut
wat z ua point? had t bn iwe nd prezdent ukadapanga chan? shame
these guyz know exactly they talkin about,,,,,anthu ena amangowona mavuto pa surface,,osaonakaye kut zinthuzo zikuyambira pati
Zazi a UDF its too late inu nde simuzalamulanso dziko la Malawi munagulitsa chipani ku Dpp mufuna chimanga chizakhaleso cha yellow mmunda
Iwe Masinja zikukuonetsa kuti ndiwe mbuli ndipo wosankha mtundu. Pepa ngati ndakukhumudwitsa koma ichi ndiye chilungamo. Malawi kuti atukuke akufuna anthu enieni osasankha mtundu.
masinja listen ukamati chimanga yellow wat do.u.mean mwina ndiwe mwana pepa yellow ife tinadya ngakhale kamuzu ali moyo yellow maize it does not mean udf yadzala mmunda vula ndi chisomo cha Mulungu not president.
Masinja mukamalankhula muziganiza osamatha mau
akuru akuru izizi ndi@mbava tatopa nawo
UDF is well organised than the rest of the opposition parties that means they think critical and fundamental ways of developing the country not just blah blah it wont help and benefit citizens of Malawi,Thumbs up yeloooo!!
Well organised??? Mmmmmmm, ngati UDF kuli munthu wokhwima pandale ndiye ndimmodzi yekha, Lucius Banda basi not enawo ma recycled politicians, Lucius ndiakatundu…
Kkkkkk @ Sylevester mwatero eti
Lucius banda osati agalu enawa
Ndikunena zoona@wonderson,Lucius ndiye UDF..
UDF ikuganiza bwino kupanga upandu ofuna kulanda boma sinzeru ndipo sizingasinthe zinthu
How old are you?
Thumb up Lucius band
Adakanena Lucius Banda bola bcz watsala yekha wambewu
boma likatula pasi Atupele atupatu!
Atupadi @ s Banda
Kodi pali kusiyana pakati pa udi efi ndi di pi pi?
Kodi pali kusiyana pakati pa udi efi ndi di pi pi?
UDF inu nokha ndiye musamayankhule kanthu chipani chatha ichi munachipinyolisa ku DPP kutha ngati makatani, kufoila kikkkk!
UDF inu nokha ndiye musamayankhule kanthu chipani chatha ichi munachipinyolisa ku DPP kutha ngati makatani, kufoila kikkkk!
Kani kachipani kameneka kanatha ngati katani ndipo simudzalamuliranso dziko lino abwantasa inu mxieee
Kani kachipani kameneka kanatha ngati katani ndipo simudzalamuliranso dziko lino abwantasa inu mxieee
Akudyera limodzi palibe chodabwitsa apa
Akudyera limodzi palibe chodabwitsa apa
Eee mukudziwa kuti mukati muwuwewuwe akumanganidi. Khalani chete kumene milandu ija angayifukulenso
Eee mukudziwa kuti mukati muwuwewuwe akumanganidi. Khalani chete kumene milandu ija angayifukulenso
UDF ??? does it still exists ?? or it’s part of of DDP ? you have both failed the country so you have no say.. we are counting down to 30 days… step down osakakamira izi
UDF ??? does it still exists ?? or it’s part of of DDP ? you have both failed the country so you have no say.. we are counting down to 30 days… step down osakakamira izi
I Doubt
I Doubt
kkkkkkkkk koma anthu andale amadziwana zochitika guys
kkkkkkkkk koma anthu andale amadziwana zochitika guys
Nsikidzi imapita ndi mtembo, UDF ipita ndi DPP blv me
Bliv me Dpp is going no where its only clever people who knows this
Nsikidzi imapita ndi mtembo, UDF ipita ndi DPP blv me
Bliv me Dpp is going no where its only clever people who knows this
Atiuza chani a UDF chipani anagulitsa
Atiuza chani a UDF chipani anagulitsa
Nsikidzi nde UDF, Mbuzi za anthu
Nsikidzi nde UDF, Mbuzi za anthu
Good man