UDF against calls for Mutharika to resign

Advertisement
Ken Ndanga

The United Democratic Front (UDF) has said it is against calls for President Peter Mutharika to resign arguing that the Democratic Progressive Party (DPP) administration can solve the country’s problems.

Ken Ndanga
Ndanga: Mutharika will solve the country’s problems.

UDF spokesperson Ken Ndanga told the media that the party wants to help DPP in running the country hence it does not believe in giving government ultimatums.

The UDF spokesperson was reacting to calls by Malawi Congress Party, People’s Party, and AFORD for Mutharika to resign saying he has failed to solve the country’s economic challenges.

According to Ndanga, the DPP cannot run the government alone since it tackles a lot of things which are of public interest.

He added that calling for Mutharika’s resignation is not a good idea since government needs the support of other political parties in order to deal with the economic problems the country is grappling with.

On why his party was not represented at the rally which the other opposition parties organised on Sunday, the UDF spokesperson said the party was not invited hence had no way of knowing the aim of the political rally.

Advertisement

255 Comments

 1. If there are new vote let’us just vote 4 (boma loti silidalowepo pamalawi chifukwa zipani zakale njira zose amaziziwa zobela ndalama so its better to change.) (mimi kutoka ku tz)

 2. Udf nde chianinso? Palibe cha nzeru anganene awa, mu ulamuliro wao adabweretsa njala ya dzaoneni mdziko lino komaso kuba too much, ngati lero tikukamba za cashgate inayambitsa ndi Udf, ndalama za ma Donors kumangolowa mu account ya president zoona? Dpp nde mbola, mavuto onsewa wina nkumati alibe problem. Winanso nkumati olo atasintha president mavuto sangathe, PP inasintha zinthu Bingu ataononga in 1 year, njala, kukwera kwa zinthu beyond our expectations wina nkumati zili bwino zoona? A change of gvt is overwhelmingly needed for suffering Malawians.

 3. Amalawi azanga kunena zoona umphawi unatizowera komanso sitimalikonda dziko lathu .pali chosapotera apa anthu mmene akuzuzikiram. Boma na likuphera kulipira mfumu k2500-R50 ya Rsa nchani chimenecho.Anthu inu zoona mmene akuondera amalawi chifukwa cha umphawi wina nkumati msiyeni akulamula bwino zoona?. Guys school yanuyi siyikuthandiza ndizochitika za dziko anthu kuchimiziku akuvutika koopsa.Ine ndinali ku Mlw koma ndinaona anthu akuvutikira iiiiiiii zoopsa . Kkkkkk or inu amalawi mumasankha zimenezi bwanji kodi mmmh simuona.kuphunzira ndi utsogoleri nzosiyana .

 4. UDF ndi chipani chotsutsa chokhacho chimene chili chozindikila m’Malawi muno.Ndi chokhachonso chimene chingathe kuyendetsa bwino dzikoli chitalowanso m’boma.Atsogoleri ake ndi okhwima nzeru,opanda dyera komanso okonda mtendere ndikufunila dziko lawo zabwino.Osati MCP,PIPI,AFORD,atsogoleri ake ndi adyera koopsa,osakonda dziko lawo koma maudindo basi.Mufune musafune,DPP kutuluka,tidzalowesa UDF,eetu!

 5. Dziko silituluka pa hr, min,day, aweek, amonth even ayr. To run Country is deffer than running acompang,bussiness, family or even club so when u think u can manage mmmmmmmm u will see the same Malawi goimg for war soon

 6. Akulu akulu tamayamikani inu nthawi ya UDF chimanga sichinakwere mmene chakwerera panopa iwe ukunyoza UDF ulibe nzeru DPP malibe chimene ikupanga panopa.

 7. maganizo anga ndaakuti peter muthalika aimilile chigawo chakumwela komanso chakwela aziimilila chigawo chapakati nde mai joice banda akaimilile chigawo chakunpoto sono ineyo TONY CHIRWA ndikhale oyang’anila athwatatu amenewa akakumana ndimamvuto mzigawo zawo ine monga tate wankulu ndiziwona mene ndingathesele mavuto omwe angapezeke madelawo, mukuwona bwanji pamenepa simaganizo abwino amenewa akuluakulu.

 8. maganizo anga ndaakuti peter muthalika aimilile chigawo chakumwela komanso chakwela aziimilila chigawo chapakati nde mai joice banda akaimilile chigawo chakunpoto sono ineyo TONY CHIRWA ndikhale oyang’anila athwatatu amenewa akakumana ndimamvuto mzigawo zawo ine monga tate wankulu ndiziwona mene ndingathesele mavuto omwe angapezeke madelawo, mukuwona bwanji pamenepa simaganizo abwino amenewa akuluakulu.

 9. The Muluzi’s Are Clever And Better.Thats The Only Way They Can Destroy Dpp And Get And Snatch Their Power Back From The Mutharikaz.

 10. Not only udf,but all wise pple aswell.why steping down?greedy dogs like to say so.is it fair to put blame to dpp on the situation the country is facing?what connections are there? Learn to speak the truth to shame the devil.every tyme u entatain the satan instead of praising God.shame.

 11. Zimaoneka zophweka zanko akamalamulira ngat mu2 ukulephela kuyendetsa cipani cako nde kulibwanj dziko tiyen tingogwilana manja titukule dziko la2 osat kumango lodzana dzala tiyen tidzuke amalaw kwacha

 12. Zimaoneka zophweka zanko akamalamulira ngat mu2 ukulephela kuyendetsa cipani cako nde kulibwanj dziko tiyen tingogwilana manja titukule dziko la2 osat kumango lodzana dzala tiyen tidzuke amalaw kwacha

 13. United Developed Fools {UDF} Toilet tissue ya alomwe, akasetera will throw you away without looking into the great job you are doing now. without vision the colour yellow will soon disappear.

 14. UDF knows wats neither good nor bad. even if the pasta won 2014 election., hunger wud av be a problem azwel. dont hate DPP. if you r clever enough tel pple other issues dat u wil manage after wining 2019 election not hunger. Just pray for Malawi n not criticising our president. Tinamuvotera coz ma qualities onse a leadership ali nawo…

 15. Utiki utiki, kkkkkkkkk, eti chipani cha Dad! Lero UDf yangokhala ngati mtengo wa kachere, kumera pa unzake! UDF, UDF lero? Zakale kale izi, chipani cha UDF, chidatuluka m’boma ndi mwini wake chair basi!

 16. Kodi inu mungoti nkhaza za Mcp munaliko inu thuza lenileni zongovela akuti tatiwu iformation yose ya MCP Tandiwuzeni Mp ali wavula zakale

  1. olo atandithira doom nkamwa sindingavotele chipani cha nkhanza cha MCP. Ndikaganiza za abale amene chipani chimenechi chidapha ndikuzunza! !!!!!!!

  2. olo atandithira doom nkamwa sindingavotele chipani cha nkhanza cha MCP. Ndikaganiza za abale amene chipani chimenechi chidapha ndikuzunza! !!!!!!!

  3. Wena Fotseke kkk oloni Agogo ako tafusa matumba achimanga omwe amapezeka mnyumba mwawo evin feterezar amalandila angati tafuse kapena ulibe agogo eti? Mkoneka ukutero tandiwuze ndangati anafapo ndinjala mulamuliro wa Big man Dr H kamuzu Banda mowanyadila timatero ife akubanja.nde Tandifuse ulamuliro uti anthu sanafepo ine siwandale koma ndine zika ya Mw

  4. Wena Fotseke kkk oloni Agogo ako tafusa matumba achimanga omwe amapezeka mnyumba mwawo evin feterezar amalandila angati tafuse kapena ulibe agogo eti? Mkoneka ukutero tandiwuze ndangati anafapo ndinjala mulamuliro wa Big man Dr H kamuzu Banda mowanyadila timatero ife akubanja.nde Tandifuse ulamuliro uti anthu sanafepo ine siwandale koma ndine zika ya Mw

 17. Dats a welcome development,this country needs big brains to comment on issues of public interest,not mbuli zophunzira as chilima said.

 18. Sikuti ngati mukuti asachoke pampando ndiye kuti pali chamzeru chomwe chikuchitika ai.Koma ngakhale atachoka pampando angabwere ndikusintha zinthu akhala ndani ndipo ali kuti?Poti onse ayesedwa kale palibe wamzeru.Basi tingokweza maso kumwamba basi

 19. Koma mitu yanuyo imaganiza?????? Mukundiuza kt kupanga resgn njala mavuto zitha??? Mawa muzakhala ndinu dziko likukunyerani kuyendesa…….

 20. opusa iwe amuthandize mzilu naweso unazolowela kukanda pathako ndi umphawi chupiti achoke akapume oko mundu muja munayamba kuvutikila ndi mkulu wake muja mukavotelaso bwampini ngati ameneyu kudzapitilizaso mavuto

 21. Mr speaker sir, why can u pliz invoke section 65 on these UDF guys as they have left their seats to government seats? U r unfair pliz

 22. udf chipani cha mbala ndi zigawenga chikutinso chani apa?malawi wanga wafikadi pododedwa ngati mpira ambuye tangobwerani mudzaweluze

 23. [READ MY STORY. ON HOW I GOT MY HIV CURED].
  Truthfully, i was tested HIV + positive for the past 8 years. I keep on managing the drugs i usually purchase from the health care agency to keep me healthy and strengthen, i tried all i can to make this disease leave me alone, but unfortunately, it keep on eating up my life. So last Two Months i came in contact with a lively article on the internet on how this Powerful Herb Healer get her well and healed. So as a patient i knew this will took my life one day, and i need to live with other friends and relatives too. So i copied out the Dr Collins the herbal healer’s contact and I contacted him immediately, in a little while he mail me back that i was welcome to his Herbal Home whereby all what i seek for are granted. I was please at that time. And i continue with him, he took some few details from me and told me that he shall get back to me as soon as he is through with my work. I was very happy as heard that from him, as i was just coming from my friends house, Dr Collins called me to go for checkup in the hospital and see his marvelous work that it is now HIV negative, i was very glad to hear that from him, so quickly rush down to the nearest hospital to found out, only to hear from my hospital doctor called Browning Lewis that i am now HIV NEGATIVE. I jump up at him with the a test note, he ask me how does it happen and i reside to him all i went through with Dr Collins. I am now glad, so i am a gentle type of person that need to share this testimonies to everyone who seek for healing, because once you get calm and quiet, so the disease get to finish your life off. So i will advice you contact him today for your healing at the above details: Email ID: [email protected] or you can also add him up on whataspp +2349036950737. CONTACT HIM NOW TO SAVE YOUR LIFE AND DOCTOR ALSO CURE ALL KIND OF DISEASE AND SICKNESS: [email protected] AS HE IS SO POWERFUL AND HELPFUL TO ALL THAT HAVE THIS SICKNESS.

 24. [READ MY STORY. ON HOW I GOT MY HIV CURED].
  Truthfully, i was tested HIV + positive for the past 8 years. I keep on managing the drugs i usually purchase from the health care agency to keep me healthy and strengthen, i tried all i can to make this disease leave me alone, but unfortunately, it keep on eating up my life. So last Two Months i came in contact with a lively article on the internet on how this Powerful Herb Healer get her well and healed. So as a patient i knew this will took my life one day, and i need to live with other friends and relatives too. So i copied out the Dr Collins the herbal healer’s contact and I contacted him immediately, in a little while he mail me back that i was welcome to his Herbal Home whereby all what i seek for are granted. I was please at that time. And i continue with him, he took some few details from me and told me that he shall get back to me as soon as he is through with my work. I was very happy as heard that from him, as i was just coming from my friends house, Dr Collins called me to go for checkup in the hospital and see his marvelous work that it is now HIV negative, i was very glad to hear that from him, so quickly rush down to the nearest hospital to found out, only to hear from my hospital doctor called Browning Lewis that i am now HIV NEGATIVE. I jump up at him with the a test note, he ask me how does it happen and i reside to him all i went through with Dr Collins. I am now glad, so i am a gentle type of person that need to share this testimonies to everyone who seek for healing, because once you get calm and quiet, so the disease get to finish your life off. So i will advice you contact him today for your healing at the above details: Email ID: [email protected] or you can also add him up on whataspp +2349036950737. CONTACT HIM NOW TO SAVE YOUR LIFE AND DOCTOR ALSO CURE ALL KIND OF DISEASE AND SICKNESS: [email protected] AS HE IS SO POWERFUL AND HELPFUL TO ALL THAT HAVE THIS SICKNESS.

 25. A udf ndinu mnayambisa kuba muboma.malonda onyasa aziwalo za anthu,azimayi kudulidwa mabele and noboday was arrested.malawians hvnt forgotten ur mess.just keep qwiet and for 2019.

 26. A udf ndinu mnayambisa kuba muboma.malonda onyasa aziwalo za anthu,azimayi kudulidwa mabele and noboday was arrested.malawians hvnt forgotten ur mess.just keep qwiet and for 2019.

 27. I think wonderson is right that Udf is well organised because it is bzy supporting government to develop this country. Mcp and Pp’s is bzy decampaining the ruling party. Me wonder, why Mcp bzy now? Does it means that there is no time for development but campainging any time? Last time Dpp yabela Mavoti kenako, Federalism, iyayi Peter atule pansi, pano Impitchment che Chakwera power hungry chonchi bwanji? Kungoti pyeeee!! Nkhaza za Mcp yakale basi. To much voiceless like un empty tine. We are following U with interest.

  1. Ndiponso Nkhanza zimene a MCP akuwonetsa pano zikusonyeza kuti atati atenga boma amalawi tizdazuzidwa zedi ngati mene makolo athu adazuzidwila

 28. Not that dpp can solve problems but so that you can continue fattening your bellies. Clueless selfish politicians.

 29. TO THE WHOLE WORLD NIGERIAN PEOPLE HAVE DEVELOP A SYSTEM WHEREBY THEY SAY THEY CURE HIV AND AIDS, CANCER AND MORE THEY SAY THEY ARE HERBALIST THEY PUT THEIR EMAIL ADDRESS PROTECTED AND THEY USE WHATSSAP NUMBER WHEN YOU CONTACT THEM THEY ASK FEW QUESTIONS THEY ARE MANY BUT THEIR CONVESATION IS THE SAME THEIR COUNTRY CODE IS +234 THEY CREATE A FAKE ACCOUNT OF A WOMAN ON FACEBOOK AND THEY USE THE INFORMATION LIKE THE FOLLOWING [READ MY STORY. ON HOW I GOT MY HIV CURED]. Truthfully, i was tested HIV + positive for the past 8 years. I keep on managing the drugs i usually purchase from the health care agency to keep me healthy and strengthen, i tried all i can to make this disease leave me alone, but unfortunately, it keep on eating up my life. So last Two Months i came in contact with a lively article on the internet on how this Powerful Herb Healer get her well and healed. So as a patient i knew this will took my life one day, and i need to live with other friends and relatives too. So i copied out the Dr Collins the herbal healer’s contact and I contacted him immediately, in a little while he mail me back that i was welcome to his Herbal Home whereby all what i seek for are granted. I was please at that time. And i continue with him, he took some few details from me and told me that he shall get back to me as soon as he is through with my work. I was very happy as heard that from him, as i was just coming from my friends house, Dr Collins called me to go for checkup in the hospital and see his marvelous work that it is now HIV negative, i was very glad to hear that from him, so quickly rush down to the nearest hospital to found out, only to hear from my hospital doctor called Browning Lewis that i am now HIV NEGATIVE. I jump up at him with the a test note, he ask me how does it happen and i reside to him all i went through with Dr Collins. I am now glad, so i am a gentle type of person that need to share this testimonies to everyone who seek for healing, because once you get calm and quiet, so the disease get to finish your life off. So i will advice you contact him today for your healing at the above details: Email ID: [email protected] or you can also add him up on whataspp +2349036950737. CONTACT HIM NOW TO SAVE YOUR LIFE AND DOCTOR ALSO CURE ALL KIND OF DISEASE AND SICKNESS: [email protected] AS HE IS SO POWERFUL ONCE YOU ARE IN CONTACT WITH THEM THEY WILL ASK THE FOLLOWING QUESTIONS YOUR NAME WHERE ARE YOU FROM KIND OF DISEASE YOU ARE SUFFERING FROM HOW CAN THEY DELIVER THE MEDICINE TO YOU THEY WILL ASK YOU TO SEND THEM MONEY $200 DOLLARS FOR PREPARATION OF THE MEDICINE THEY SAY THEY WANT TO BUY ITEMS FROM THE SELLER THEY GIVE YOU THEIR WESTERN UNION ACCOUNT ONCE YOU SEND THE MONEY THEY BLOCK YOU ON WHATSSAP THIS IS HOW THEY ARE STEALING MONEY FROM PEOPLE THEY PUT THEIR STUPID STORIES ON NYASATIMES, MALAWI24 AND MANY PLEASE DO NOT SEND YOUR MONEY TO THEM TOGETHER WE CAN END THIS LETS FIGHT BACK TO THEM BY FIRING BACK WITH ……. PLEASE DO NOT SEND MONEY TO THEM FROM NIGERIA POLICE SERVICES AND THEY ARE HUNTING THEM USING THEIR MOBILE

 30. Looool UDF is worse it can happen again to take over your time is gone.why can we try MCP mayb things will change not UDF

 31. Indedi ayise…koma ndi mmene dzilili apa boma ilili..bolaso UDF IJA ibweleleso..if is not came back..mo of malawi is going to be xpre..nanga taonani Randi aganest kwacha one to..fortyfive thats no seccc man UDF CAME BACK .Brathers

 32. Indedi ayise…koma ndi mmene dzilili apa boma ilili..bolaso UDF IJA ibweleleso..if is not came back..mo of malawi is going to be xpre..nanga taonani Randi aganest kwacha one to..fortyfive thats no seccc man UDF CAME BACK .Brathers

 33. Anthu otoletsa ma bin inu a UDF jst blind following that idiot dude fucked off ! Try to reason mutulukamo shortly bomamo demet !

 34. Anthu otoletsa ma bin inu a UDF jst blind following that idiot dude fucked off ! Try to reason mutulukamo shortly bomamo demet !

 35. Kodi mavuto anjalawa athu atengelapo popangila kanpeni kutitola eti inu a UDF mukafune owapusisa musiyeni amalizise machimo akewo kodi anakakhala ntumiki wina walosela kuti pitayo amwalila afta 30dayz ndi angati omwe munakabwela kumati eee ine ndifa malo mwa pita nsiyeni zikunvuta muthu chifukwa amalawi timaphwekesa tchito yanzathu mmalo moti timuthandize nzelu koma kutukwana tizikhala chonchi npaka kale inu mavuto onsewa pomwe achokela simukupaona chaka chatha nvula inakokolola mbewu chaka chino nvula ikuvutavuta nde inu a UDF basi matako manganemangane kuti mukwanisa zithu mukazitenga kuti osamatitola amalawife ndife nzika eni thaka zichepe mudikile 2019 muzasakhidwe bwsi not tikwanisa kukwanisa chani kubaso

 36. Kodi mavuto anjalawa athu atengelapo popangila kanpeni kutitola eti inu a UDF mukafune owapusisa musiyeni amalizise machimo akewo kodi anakakhala ntumiki wina walosela kuti pitayo amwalila afta 30dayz ndi angati omwe munakabwela kumati eee ine ndifa malo mwa pita nsiyeni zikunvuta muthu chifukwa amalawi timaphwekesa tchito yanzathu mmalo moti timuthandize nzelu koma kutukwana tizikhala chonchi npaka kale inu mavuto onsewa pomwe achokela simukupaona chaka chatha nvula inakokolola mbewu chaka chino nvula ikuvutavuta nde inu a UDF basi matako manganemangane kuti mukwanisa zithu mukazitenga kuti osamatitola amalawife ndife nzika eni thaka zichepe mudikile 2019 muzasakhidwe bwsi not tikwanisa kukwanisa chani kubaso

 37. The problem with you politicians is that you say let us join hands when there is crisis. But when you open a 5km road you eveen climb Mulanje mountain and say we are the only one. So being the only one what are you crying for? Apologise for the wrong doing then seek for assistance.

 38. The problem with you politicians is that you say let us join hands when there is crisis. But when you open a 5km road you eveen climb Mulanje mountain and say we are the only one. So being the only one what are you crying for? Apologise for the wrong doing then seek for assistance.

 39. devu zosezo kudandaula za njala mpaka liti. waulesi asadye . musiyini amalize 2019 tione ngati mungawine. kulalata sikukupindulilan. mzakomoka kuzafika pa chisankho pitala kuztengaso boma. inu mukuchedwa ndi kulalata .

 40. UDF and DPP are both parties of crooks and are the parties who have worsened our poverty here in Malawi. They have been robbing us Malawians

 41. Inenxo ndilibe polobulemu,coz palibe munthu azathetse mavuto olo chipani sichizathetsa mavuto,ndiufumu wa mulungu wokha utazathetse mavuto,moti munthu wanzeru ndikumalimbana ndi andale akuziwa kt palibe chomwe angachite,masiku osiliza kuzakhala njala mumaona ngat malawi masiku osiliza sizakhalako njalayo?kikkkkk ana anjoka inu mukanganilanj pomwe mbuye wanu anakuuziranitu zizindikilo za masiku osiliza

 42. …….UDF is ryt, lets unite and find a way forward to solve this crisis, removing president will worsen the situation..! let president go to u.s.a and beg for kenya maize and he must declair malawi a state of emergency coz of this hunger….thats my contribution as of now….zikomo

  1. Ngakhale Litakhala Banja Kuti Lafika Poter, I Don’t Think It’s Proper To Ask Those Who Admire Your Wife To Assist U To Resolve Ur Family Problems.Nditakhala Ine, I Can Just Give Chance To My Friiends To Try .

 43. I agree its high time we decided where we belong we better agree and belong to one understanding. Better be Democrats, Republicans, Liberal. We waste time for there is no way a President can resign we better decide

 44. Amalawi tiyeni tisegule maso ndikuyamba kuganiza mwanzeru. Inuuu simalawi yekha amene akukumana ndimavuto osiyanasiyana, koma taonani mmene anzathu akuchitila kukonza zinthu. For insance dziko la china nalo likukumana ndimavuto ngat omwewa. Kma aku-china akambirana kugwira ntchito limodzi kut asove mavuto awo. Pamenepo mmalawi akungong’ambika kukamwa ali “achoke-achoke” nde mpaka liti kkkkk malawi fuko langa lokondeka tatsekula maso ako ndikuyamba kuganiza mwanzeru. Pamavuto iwala zandale koma kupeza njila mmm

  1. Kumalawi ndizobvuta kugwilira ntchito limodzi coz anthu ake ndiodzikonda.Zikamayenda amadzitukumura kwambiri ndipo amaona ngati mmdziko muno mulibenso ena amnzeru,zikawasokonekera ngati mmene zafikiramu ndipamene amafuna opanda nzeru aja kuti apange contribute their views.Bvuto kumalawi atsogoleri olamura, amafuna anzawo zinthu zikathina.kkkkkkkk musova.

 45. Ndimulungu ekha amene angakwanise kuthesa mabvuto onsee otsati munthu ai, palibe wina koma tingosamira kwa mulungu kuzera mwa mwana wake yesu khristu basi

 46. nkhani koma imeneyo makape muli m’madzi woyeeeeeee, woyeeeeeee ,woyeeeeeeeeeeee , iwe ndi iwe kagwereni uko!

 47. UDF kumeneko ndiye timati kubwela.A UDF akudziwa kusatila ndale m’mene zimayendela inu ndikukumbutseni kuti 1994 UDF defeated MCP and AFORD with a wide margin.After 5 years,Bakili Muluzi defeated mgwilizano wa MCP ndi AFORD.Late Bingu did the same under DPP. MCP ndi chipani chogwedezeka PP ndiye idkomoka kale,it it tainted with cashgate.There is nothing you can learn from MCP only nkhaza ndi kulalata.PP Uladi Mussa will teach you new tricks of how to steal money from the capital in seconds.Atupele stay where you are learn how to govern people of malawi so that in future never make the mistake like your father did seeking for the third term. DPP well orginised,UDF is organised no defections like PP..

 48. Kodi mumatafuna zintuwitsa eeti, ithink its now good time for we the youth to show our anger with mass demo. Its not fair 80thousand passport, some one should resign no future for poor youth

 49. UDf chipani chosamva,never learn from its past mistakesBakili anagulitsa boma kwa dpp,lero mwanayu wagulitsaso chipani kwa dpp yomweyo,Rip udf

 50. The UDF is against resignation of Peter Because Its Leader Atupele Has Also Told O Resign By UDF supporters. Atupele Anangowagwiritsa Ntchito Ma Sapota A UDF mpaka pano samaonekanso koma pa lampeni amkati amaganizira moyo wa anthu osauka koma olo za njalayi sanalankhule bola zake ndi bambo ake zikuyenda.Atupele Si Wandale Koma Wa Dama Amangofuna Maudindo Osati Kukhazikika Pa Ndale .Zoona Mu Ndale Combination Angakhale UDF ndi DPP .

 51. aaaaaa UDF my foot so ashamed of that party u cowards couldn’t stand the heat nde makadzipatika kwa Pharaoh.

  Big up Mr Lucius Banda u are the true son Of Yellow remaing

  1. Lucius ndale anaziyamba kalekale, amadziwa chimene akupanga ndipo amapanga zokomera amalawi onse,samanyengelera,ndiolimba mtima yes he is true soldier of the land,Malawi.

 52. Mm wise people support the point UDF is saying. If we say muthalika should resign we should consider both positive and negative consequences. It is not only Malawi facing these problems but look at how other countries are working to solve there problems!
  China is one of countries facing economical problems but the have organised a meeting and descus how all together will work and agree to work to gether. Pamenepo m’malawi angong’ambika kukamwa ndikukuwa “achoke!! Achoke! Instade of trying to work together kkkkk malawi country dzuka malawi dzuka

 53. Start visiting villages…pipo are dieing of starvation, go to RTD….go to immigration, go to the filling stations everything is high today…….& this lyf is hard to live…..cos of this poor adminstration…. (DPP)

 54. Wina olo afune olo adzafune 2019 udf boooooooooooooooooooooma

 55. UDF you are right. Soon it will solve economical problem by raising fuel price, Raising passport from 48,000.00 to 80,000.00

  Kkkkkkkkkkkkk. So funny Boma Ilo!!!!!!!! Lyo lyo.l

 56. Udf oyeeeeeeee 2019 kuti waaaaaaaa oyeeeeeee sanasanali tembo anali kumangochi kuma kwacha kwacha mixalaeti

 57. Anzathu odala mukumwa madzi am’botolo anzanu ife tikusowa yogula wokoman ,nkumati zikuenda mukumuonetsa ngati wanzeru komatu mutati mufike kumidzi kuno nkuona mmene anthu akufela ndi njala simkadalankhula zoti pitala cannot resgn , makamaka inu a UDF amene mukudyela tebulo limodzi munthalika mudzaona polekela tikatenga boma ife otsutsafe.

 58. Am A Ud3 Supporter But I Wil Agree With U Only If U Will Iie To Me What U Wil Do After Resignation Of Pete Mathanyula Ka Njala,cz U Sold The Party To Dpp,by The Way U A All Fools,

 59. UDF ndiye inatidyetsa mizu ya nthochi sindingaiwale ine mix Muluzi fake money end of that anatisiya mu chipululu m’malo mokafika kukenani ndiye tingakumveni pomwe tinapempha Nsomba inu ndi kutifungatitsa chinkhanira means Dpp

 60. ya dziko ndianthu ake shame somtyms i wonder anthu mumadandaula magetsi akathima kulibwanji nanga ife anthu akumuziwa mavutowa tikukumana nao bwanji pano mukuti mulibe polobulemu hu mulindiumunthu koma wina kumavomereza zopusazo shame think ov our granny omwe aliku midzi mowoyu u think akumva chimodzimodzi mukumveramo mulibe chisoni ndinthu if i may ask since the dpp government come to power asinthapo zitizo

 61. these guyz know exactly they talkin about,,,,,anthu ena amangowona mavuto pa surface,,osaonakaye kut zinthuzo zikuyambira pati

 62. Zazi a UDF its too late inu nde simuzalamulanso dziko la Malawi munagulitsa chipani ku Dpp mufuna chimanga chizakhaleso cha yellow mmunda

  1. Iwe Masinja zikukuonetsa kuti ndiwe mbuli ndipo wosankha mtundu. Pepa ngati ndakukhumudwitsa koma ichi ndiye chilungamo. Malawi kuti atukuke akufuna anthu enieni osasankha mtundu.

  2. masinja listen ukamati chimanga yellow wat do.u.mean mwina ndiwe mwana pepa yellow ife tinadya ngakhale kamuzu ali moyo yellow maize it does not mean udf yadzala mmunda vula ndi chisomo cha Mulungu not president.

 63. UDF is well organised than the rest of the opposition parties that means they think critical and fundamental ways of developing the country not just blah blah it wont help and benefit citizens of Malawi,Thumbs up yeloooo!!

  1. Well organised??? Mmmmmmm, ngati UDF kuli munthu wokhwima pandale ndiye ndimmodzi yekha, Lucius Banda basi not enawo ma recycled politicians, Lucius ndiakatundu…

 64. UDF inu nokha ndiye musamayankhule kanthu chipani chatha ichi munachipinyolisa ku DPP kutha ngati makatani, kufoila kikkkk!

 65. UDF inu nokha ndiye musamayankhule kanthu chipani chatha ichi munachipinyolisa ku DPP kutha ngati makatani, kufoila kikkkk!

 66. UDF ??? does it still exists ?? or it’s part of of DDP ? you have both failed the country so you have no say.. we are counting down to 30 days… step down osakakamira izi

 67. UDF ??? does it still exists ?? or it’s part of of DDP ? you have both failed the country so you have no say.. we are counting down to 30 days… step down osakakamira izi

Comments are closed.