An 18 year-old Malawian young man in Dowa district is in police custody for beating his father to death.
The young man, identified as Lewis Kachigamba, beat his father Genesis Kachigamba, 44, who was abusing the young man’s mother.
According to a source, on the day of the incident Genesis was drunk and was insulting his wife.
This angered Lewis who started to beat the father.
The drunken father got unconscious and died on the spot.
A post-mortem conducted at Dowa District Hospital revealed that the man died due to internal bleeding.
Lewis will appear before court soon to answer charges of murder.
Both Lewis and Genesis come from Topaizi village, T/A Msakambewa in Dowa.
Kukula mopusa
Kukula mopusa
Tsoka lobadwanalo
Tsoka lobadwanalo
akiller! go 2 hel
Koma Ku dowa,sikuzathekasoooo
Kodi mmalo molimbana kuthetsa njala koma kumanga anthu basi? zoofoila zokhazokha!!!
Let the boy go to school,he is clean than aunt Tio.
In defence of his lovely mum, he killed.
so bad young boy
don’t judge him before kuva mbali yake mwina inali mbama imodzi yokha.. poti moyo wamasikuano..
I think kundende kulibe facebook sakuwona zomwe mukulembazi ng’ooooooh. komanso ndi nfana ampitisa ku Mikuyu, Kachere, kapena Mpemba. azikagona pa bho kudya chimodzi modzi. mwamulila. nanga mdalayo anakapha sten-yo?. Love for His mum. koma samadziwa kut zifika pamenepo.
Kuweluza mkwamwini ok
Go To Hail Man!
Zako izo my father was passed away when iwas 10 yrs ndimalakalaka ndili nawo
mwanayo sanalakwe coz he was fighting for the gender Violence,so Kaliati save him
Akafere kundende galu ameneyu.achinyamata kutengera zopusa kwambiri.chinzanu ndi ichi chakhapidwa kunochi.dere tachiika dzulo dzuloli.
Xizikufunikaxo police bt kuotcha nd petro ameneyo…
Chitsilu chamwana ena akuso makolo iyeyo ndi kumapha makolo ake asatuluke ameneyo ena aphunzileko
Asovadi mwana opanda khalidwe ameneyo bambo ndiosithanisana manja!! apitedi ku ndende!!!
So u just said abusive father’ then why the boy should be in police for this abusive dad’s death i thought he deserved it
Kkkkkkk Bamboyo Mwati amachita ‘Abuse’ Mkazi wao? Tanditanthauzireni mawu amenewa mu chichewa,”the Man started abusing his wife.”
Osamapanga chiganizo utapsa mtima zosatira zake amakhara ma regret taona u killed ur only blood shame on u ask God to forgive u
Anthu ena munabadwa bwanji munthu waphedwa mukuchita like tiyeni timve chisoni chifukwa achinyamata alero zachuluka zosuta tiyeni tiziganiza before u mark (LIKE)
Zomvesa chisoni
No Comment
http://shareduty.com/?id=664
aaa can see ur gud at killin people Boma likuyenera kut likutumize ku Nigeria ukathane ndi Boko Halamu
Chamba
De best solution iz dat ada awa aphedwe nkukamuotchaaa coz dis iz useless. tachioneni kupusa ngat chiphuyaaa
[READ MY STORY. ON HOW I GOT MY HIV CURED].
Truthfully, i was tested HIV + positive for the past 8 years. I keep on managing the drugs i usually purchase from the health care agency to keep me healthy and strengthen, i tried all i can to make this disease leave me alone, but unfortunately, it keep on eating up my life. So last Two Months i came in contact with a lively article on the internet on how this Powerful Herb Healer get her well and healed. So as a patient i knew this will took my life one day, and i need to live with other friends and relatives too. So i copied out the Dr Collins the herbal healer’s contact and I contacted him immediately, in a little while he mail me back that i was welcome to his Herbal Home whereby all what i seek for are granted. I was please at that time. And i continue with him, he took some few details from me and told me that he shall get back to me as soon as he is through with my work. I was very happy as heard that from him, as i was just coming from my friends house, Dr Collins called me to go for checkup in the hospital and see his marvelous work that it is now HIV negative, i was very glad to hear that from him, so quickly rush down to the nearest hospital to found out, only to hear from my hospital doctor called Browning Lewis that i am now HIV NEGATIVE. I jump up at him with the a test note, he ask me how does it happen and i reside to him all i went through with Dr Collins. I am now glad, so i am a gentle type of person that need to share this testimonies to everyone who seek for healing, because once you get calm and quiet, so the disease get to finish your life off. So i will advice you contact him today for your healing at the above details: Email ID: [email protected] or you can also add him up on whataspp +2349036950737. CONTACT HIM NOW TO SAVE YOUR LIFE AND DOCTOR ALSO CURE ALL KIND OF DISEASE AND SICKNESS: [email protected] AS HE IS SO POWERFUL AND HELPFUL TO ALL THAT HAVE THIS SICKNESS..
Let’s not judge him until we hear his side of the story. Am strongly against what he did but it will be better to look at the issue with full knowledge of the whole incident.
Una masimba kakhulu mbut
Kma abro akanati ena apangezimenezi inumusanabadwe mukuganiza kuti mukanamuona Malawi inu? ndithuilinditsoka ndiyepopeza MWATENGELA LAMULOKUMANJA uzionawakulawatha mbale
Mwanayotu ndikuona kuti amangofuna kumuphunzitsa mdalayo ndi makofi. Analibe cholinga chowapha koma kungoti mowawo wangothandizirapo. Midala inai ikayatsa imathoka bad. Amukhululukire sadzawaphanso.
Angomukhululukiradi sadzayambiradi zowaphazo.
Ana a masiku ano chamba. Nde usovadi njala, udzudzu, tsikizi momo for 15 yrs
The boy doesnt deserve custodial sentence, he needs to be acquited, he doesnt posses an danger to the nation. He had no intensions of killing he acted out of provocation, he would nit bear seeing his mum abused always. I pity him. wish you a fair trial boy stay strong. dont let anger overtake you again
Vry stupid man y? y? eish karanga mwana iwe tsoka rimener
mmmmm
Aaai tisakunyozeni a chimwene. inuso kumbali yanu mwachita ndithu.
Mwana wopusa kwambiri mulungu akulange ndithu
Nonsense
kape usovenge
don’t worry upeza ena bambo ku Zomba prison
Mwawe dziko ulivano
Ambuye akuone ambwana.
Koma ameneyu ali ndi tsoka… Anzako pano tikulira, moyo ukukhala ovuta kukhala opanda bambo… Mmmm Ambuye akuone mwapadera sure
Koma ameneyu ali ndi tsoka… Anzako pano tikulira, moyo ukukhala ovuta kukhala opanda bambo… Mmmm Ambuye akuone mwapadera sure
Mwana otembeledwa bambo ako akulela kuyambila tsiku lomwe anakuika mmimba mwa amayi ako mpaka kufika tsiku lomwe unawapha aaaaa chitsilu chamwana kapike basi chitsilu.
Mwana otembeledwa bambo ako akulela kuyambila tsiku lomwe anakuika mmimba mwa amayi ako mpaka kufika tsiku lomwe unawapha aaaaa chitsilu chamwana kapike basi chitsilu.
Malawi alibwanji? Akita ameneyo wapha bambo ake kkkkkkkkklk
Malawi alibwanji? Akita ameneyo wapha bambo ake kkkkkkkkklk
Mmmmm danger
Mmmmm danger
Mwana watsoka uyu
Mwana watsoka uyu
Bola ukanawapha m’masenga, mtima wako udzankhala opanda mtendele
Bola ukanawapha m’masenga, mtima wako udzankhala opanda mtendele
ooooh mwana iwe amzako kusilila uli ndi ababa. basi iwe kupha dala. ambuye akukhululukile ndithu kalanga ine umasiye kuwawa.
ooooh mwana iwe amzako kusilila uli ndi ababa. basi iwe kupha dala. ambuye akukhululukile ndithu kalanga ine umasiye kuwawa.
uziona wekha kuphamadala khalidwe loipa
uziona wekha kuphamadala khalidwe loipa
Zovetsa chisoni ameneyo life prison.
Zovetsa chisoni ameneyo life prison.
chitsiru cha mwana
chitsiru cha mwana
2 bad,how do you feel now after your job(killing)
2 bad,how do you feel now after your job(killing)
yooo mapeto adzikoli nde tikuwaona tokha
yooo mapeto adzikoli nde tikuwaona tokha
Patricide, pitty! whats was wrong with ur father. Up to the extent of killing em, so bad ameneyo life emprisonment with hard labour . Inject him with parrafin azikatupa
Patricide, pitty! whats was wrong with ur father. Up to the extent of killing em, so bad ameneyo life emprisonment with hard labour . Inject him with parrafin azikatupa
mwana opanda nkhalidwe,kupha atate ake oti aledzela osangokawatsekela nyumba bwanji ngati amavutitsa kuti ukawathela nkuwayankhula mwapadela kuti asinthe.nanga chonchi murder case yaikodola yekha iyi
mwana opanda nkhalidwe,kupha atate ake oti aledzela osangokawatsekela nyumba bwanji ngati amavutitsa kuti ukawathela nkuwayankhula mwapadela kuti asinthe.nanga chonchi murder case yaikodola yekha iyi
Mesa amafuna kuoneka bolo young pano fodya anasuta watha ali mukagowelo konunkha kodzadza udzudzu ndi nsabwe
kkk Dolo osati Bolo
Iyayi ine ndikunena Bolo Young osati dolo amafuna kuoneka wadzimphamvu ngati Bolo
Mesa amafuna kuoneka bolo young pano fodya anasuta watha ali mukagowelo konunkha kodzadza udzudzu ndi nsabwe
kkk Dolo osati Bolo
Iyayi ine ndikunena Bolo Young osati dolo amafuna kuoneka wadzimphamvu ngati Bolo
http://shareduty.com/?id=664
Something is wrong with u, they should punish u severely,
Something is wrong with u, they should punish u severely,
Waisova man enafe tikulakalaka abambo anamwalira 1991 sindinawaone mmaso nde iweyo ukamawapha shame on u ngati chilipo anakulakwira osakambirananawo bwinobwino bwa?? Uli ndi soka ndithuu
Waisova man enafe tikulakalaka abambo anamwalira 1991 sindinawaone mmaso nde iweyo ukamawapha shame on u ngati chilipo anakulakwira osakambirananawo bwinobwino bwa?? Uli ndi soka ndithuu
http://shareduty.com/?id=664
Eee! Kaya muli ndi azibambonu musova!
Eee! Kaya muli ndi azibambonu musova!
ndiye mpaķa kumpha koma man dzakadzo 18 year usolve
ndiye mpaķa kumpha koma man dzakadzo 18 year usolve
So bad
So bad
Mmmmh Such Is Not Good That Means Killing His Second God
Mmmmh Such Is Not Good That Means Killing His Second God
rip madalaaa kkkkkkk aaaah tatopaa nazoo ifeee
Iwe chitsiru kwabasi,,wangonditalikira nkanakuzizimusa ndi BAGELA
rip madalaaa kkkkkkk aaaah tatopaa nazoo ifeee
Iwe chitsiru kwabasi,,wangonditalikira nkanakuzizimusa ndi BAGELA
kakakakakaka hihihigigihihiiii usovaa aiseeeee wuuuuuuu
damn dud…….
damn dud…….
Charge of murder?Osati manslaughter?Ok whatever