Malawi’s ex ruling Peoples Party (PP) deputy publicist Moses Kunkuyu has resigned from the party, Malawi24 can confirm.
Kunkuyu, former Blantyre City South Member of Parliament, made the revelations a few minutes ago at a presser currently underway at Mount Soche Hotel in Blantyre
Kunkuyu, hit headlines as one of the youthful law makers in the August House during the Bingu wa Mutharika era before Mutharika died and Joyce Banda picked him as Minister of Information under.
He has since not cited reasons for his leaving PP.
Nothing z fo real!
Zayambikatu,tisiyeni amakawife tilongosole zakumunda kaye
Next is wakuda kamanga en change golo jst wait.
#kkkk mutiuza winanso akachoka
Nothing strange or breaking that’s political,watch him.
Ndale zomayamba chifukwa cha umphawizitu zimatero…..chonchi mukuononga mbiri ya achinyamata kuti achinyamata ake akumalowa ndale atalema ndi umphawi nde nzeru zikumathawa akaona ndalama……..khalani pansi basi musakasokonezenso kwina.
Konkuyu,umalimbana Ndi Pp Themu mwana wa jzu wachepa kapepese kwa jzu ndi pp Themu mcp ikuganizira,chita ngat sausage gwengwe uyambe campeini mcp 2019 idzakuganizira
kodi abro sausage Gwengwe pano zili pati? galu wa mwana amene uja tandiuzeni ndili patali
Pano akuchita busines ya kasukulu kaja amati alice gwede akumanyengerera anthu kuti adzaimire mcp next g elexions
Dyera nothing breaking or strange here Malawian politics at its best
Koma mmene wathera ibrahm matola pano,,,anapupuluma kudana ndi ung’ono
Koma mmene wathera ibrahm matola pano,,,anapupuluma kudana ndi ung’ono
He change the party bcz he knw that #DPP is millk& haney
He change the party bcz he knw that #DPP is millk& haney
Fall of Moses Nkukuyu wat ashame my son
Fall of Moses Nkukuyu wat ashame my son
Why z t a brekng news? Wat z a brekng? Z kunkuyu a figure now?
Ndisanve kuti mukukalowa Dpp cholinga mukabenso kapena kudya nao. Kususuka basi.
Atsala amayi, uladi, kamulepo ndi hon kalaile. If a Dpp tikumwa wamkaka
Atsala amayi, uladi, kamulepo ndi hon kalaile. If a Dpp tikumwa wamkaka
Tadziwa kuti muli moyo zikomo
Alipo mkulu ameneyu???? koma ndale mkanyama koipa heavie
IYE nde atani amayi adachisiya kalekale pano angopanga maganyu muSowetomu
Alipo mkulu ameneyu???? koma ndale mkanyama koipa heavie
Rubbish,stupid,So what ? myopic ,greedy ,liars,thieves,malawi politicins.Why dont you talk abt developing malawi ? We r tired of hearing of politicians changing parties,following where GVT pulse is, stupid.We want politicians who cn bring developments.
Mutha muona
inu tisiyeni tione za chilala chili dziko muno , ngakhale apresident akukana kuti mulibe njala ,
That is frastration. He Thought He would be the one to be the acting president.His dreams haven’t come true.
Recycled Politician Never Mind!
Dumping a sinking ship cannot be a breaking news
I don’t see any News breaking
AMADIKILA KUTI WINA ADZIPHE ,MKAZI NDI MWANA YEMWE .
Thats rubbish who cares, to me its not breaking news. Lavuta apa ndi khodi
Sangawine kwathu ku Dedza south MCP idamanga nthenje ife pambuyo pa Chakwera #2019 government in waiting
uwiiii! mkulu ameneyu alipobe et!
Its not bad he has areason.
MUNTHU MUNTHU…..AYA YA..YA..
…………Team Nyapapi…..
thus y I hate politics serious. wts all dis bullshit? I dnt blv in politics. akatero akaloweso DPP azikanena zabwino zabwino zokha zokha. ikadzaluzaso adzatuluka kukalowaso cholamula. pachiphwisi panu andale nonse!
kkkkkk ana gambula kusiya BT City kupita ku Home of MCP and lost miserably ndale paMalawi
kkkkkk ana gambula kusiya BT City kupita ku Home of MCP and lost miserably ndale paMalawi
Nanga enanu mukusaliranji ku PP ko?
Kkkk mr kumkuyu…what ajourney so which way? where to.Mwamudyeradyera JB mukumuthawa…Free advise, make adecision that will never let u down..Politics in malawi has destined aclimax of regionalisn and tribalism.The time u were in blantyre u could maintain ur seat if u were focusing onthe welfare of the pple and not wasting ur energy with political prostitution..Ofcourse you went to Dedza after u sensed danger of stiff competition.Now u made amistake to stand on a pp ticket in aconstituency where MCP is their culture..It could be better if u had decided to even stand as an independent…It is my hope that ku PP mwatengako zokwanira kuti muchite survive….leave politicts to politicians……..
Is this strange in politics, why u call it “BREAKING NEWS?”
“Breaking News” bcoz its happening just now
Ok, i see
nngti kuli mnthu wandyera munthu wake ndiyemweyu munthu siwandale amakofuna popezera ndalama basi osati pautsogoler palimbe munthu utsogoleri mulimbe.tikumuziwa nzeru zake sitsimtsogoleri.
Mnyamata ameneyu ma emotions anamutenga kwmbiri. Anasiya kuganiza
Relo malawi ndi malawi yamoto
tiyen tizingo kwatiwan amuna okhaokha bas akaziso chimodzimodzi osalimbanaso ndi ndary
Alibee influence
Tilibe nazo ntchito izi
Oooooww he was stiill around in the political circle???
Inu andale ndi athu adyera awa ndiye ife musatiuze kti breaking news timvaso kti ampatsa udindo ku dpp mxie cashgate country in the word
Kutha kwa kachipani
uku nkuyamba chabe,change golo ali mmbuyomo
Hahaha zake izo ine ndili nchipani changa msogoleri ndine vice mkazi wanga ku youth wing kuli mwana and none of us can resign our party coz we are united ndipo palibe analowa nchipani chathu ncholinga chozadyera nzake.
Dying slowly!
Mnakuuza usachoke kwa manase lero taone watha ngati makatani
Sorry!! sinpanga nawo ndale zanuzo
Politicians without principles and sense of direction!
Political Prostitution isn’t strange in Malawi n no need to call t a “breakng news”
Nayenso Ndi Change Goro, Waona Kut Umphawi Wayamba Kumuswa Akadyere Wena, Atha Ngati Makatani!
Moses kumkuyu aliponso koma NDE wasowatu go we’ll broda man
More resignations are yet to follow
Wamuphonya upulezidenti ongogwirizira kkkkkkkkkk
nde mpaka breaking news kape ngati uyu? hajahahaha
izitu olo munakati musatiuze kuteroku tilibe nazo ntchito
Ambiritu mtizipanimu ndi aganyu basi. tindalama ta cashgate akamanana muwaona akutuluka. Even osokosa pa fb ambiriwa ndi ulovatu basi. Akawalipirira rent ndiye iiii kutukwana anzaofe kwabasi. Mutipeze ku kongeresi kuno.
muthawa simunati
In simple language we just say it….pp yanyamuka!!
Ndikanakondwa ikanadzera ku Linthipe3 ikathere komweko.
Ulindsambi Wamudyeradyera Iwe Mayi Ovala Duku Uja Ukumuthawa,mmene Umayakhulira Mwathamo Muja Pa Radio,man Sibho!.
wazionera patali. chipani chilibe mudzu ichi
Its a free world and is gurranteed in the Constitution.
wachoka wa choka sizonyengerera umatilemera tachosako problem
Akusaka poti adyere uyu watha bac anatchuka udyo
No wonder…resighnation its not new in politics .Za ndale kuzilowelera utha kutha ndiwe.
zaziiii
Who z next? Kapena kwatsala ndani???
Who z next? Kapena kwatsala ndani???
nanga munthu ungati ndikayimira ku DZ kwa tembo uli wa PP or DPP?wamwa ink.
MCP bound, Ku Dedza
Did you see this Justin Kamwendo
It’s news mama, haven’t talked to him this year…
Njala kamakangolimani kumudzi
Ndiye ife titani?
Nanga a Moses ndi anthu oti zipani zingawafune? Olo munakapanda kutiuza. He is a useless brat.
zanu zimenezo! Cashgate yanuyo mumadya ndi ife??
za kunkuyu ife tidaiwala kale kale
Kutha mix makatani.kkk.yanyamukaaaa
Tilbe nayo ntchito
Chitha ngat makatani chipani chimenechi. Kunali chipani cha NDA chinathanxo choncho