At a time when Malawi Police Service continues to warn people against mob justice, an irate mob in Mwanza district chose to ‘deal’ with a man they caught stealing their own way.
According to Police, the people on 23rd December caught a man aged 47, whose names are yet to be given was caught breaking into a house together with his accomplice.
‘’They managed to break into two houses and when they were breaking into a third house, they were caught by the angry community members. The deceased friend managed to escape and the mob beat up the culprit severely to death.’’ Malawi Police Service posted on Facebook.
According to police, the slain thief died after he unceasingly bled internally.
‘’The Malawi Police Service is advising the general public however, to desist from taking the law into their own hands.’’, police have advised.
Mlingo olingira mzako mawa azakulingira womwewo, tiziganiza pochita zinthu amalawi.
Aphedwe basi
nde wakumana ndi iphing pple
ithink anakanga ibu risation.
mbava assostion of malawi ( mbam)
Malawi police inali kale
Good idea umakolola zomwe walima
Chimene chimawawa ndichakuti akubawa akatipanga chipongwe kaya kutikhapa kaya kugwiririla achibale anthu kaya kutipha kumene akathawa a Police sapanga kanthu koma mumadandaula bwanji tikapha wakubayo?Kodi bwanji a Police osamawauzanso akubawa kuti azingoba katundu koma asamaphe mwini nyumbayo?
Watch out 2 u mwanza people!! Are you mad?
osapanga brai
Okuba aziphedwa osauka okha a cashgate ai?
Kkkkk zilibwino
They Wll Not Suspect Him Again
kkkk yea he is gone for good. No more suspecting
u say his names are yet to be known but is aged 47. Who told u his age?
Signs Of The End
CHIMENE CHIKUNYASA MAU OKUTI AKUGANUZILIDWA KOMA ANTHUWO ACHITA KWAPEZA RED HANDED AKUCHITA ZONYANSA NDE NKUWONA ANTHU AKUNGOLANGA OKHA DEMOCRANCY IJA NDIMENEYI TIYENI NAYO OSADANDAULA
it is a bad development that mob justice is growing throughout the country. i for one i dont support it coz there is no reason regardless of the offence that someone be killed by pipo just bcoz he or she was caught in an illegal act. despite the fact that malawi police is corrupted still there is a need to hand over suspected individuals to them.
Ntchito ndi ina ili yonse yamanja mukagwila mbava kong’onthani
Pano Malawi uphawi inamukwana ndie wina azigotenga zaulele a @ ngati mukufuna kuziwa zambili news zakunja masewelo ndizina pitan pa Facebook page yanu=#ziripati_cd_com
taking somebody’s life?, mmmmm nothing can b exchanged by life, malawi ndakudandaulani
its really a bad act act!!! i hate it
kill is nt way to reduce crime
Zinazi zikumaonjeza kwambiri, nanga munthu amugwira koyamba kuti amaba then kanthawi pang’ono umu ona watulukiranso ndi zimene anthu amakwiya nazo kwambiri ndi chifukwa chake anthu akumawatengera malamuro kumanja kwawo.
Zoona tatopa nazo mbava izi wina atengerepo phunziro
wosayiwala ntose Kumalawiko ndi akuba
okuba onse aphedwe! basi.
Kkkkk! Wanya nako.
Thanks mwanza God bless you people
mukapeza wakuba iphani, ku police kulibe chilango
Ndikufunika kuti ndiphe mbala INA yake, I don’t trust police.
good work done
mwaiyamba bwino Xmas, muli boh
Ine sindikugwirizana nazo poti nokha mmati malawi is a God fearing country koma bola atagwira mbavayo akanangompasa chilango choti iye asazaiwale chimtengere iye kukulapa machimo ake. Ambuye atikhululukire tonsefe poti nafeso tingazaweruzidwe ndimweso omwe taweruza nawo mzathuyu
nkhaza zimezo
Ztamatere mbava zingachepe…pakufunikad kumangokupha osamusia ndmoyo…acita booo…congrants
anthu amenewa akalowa mnyumba amtha kupha kugwlilira nde akapezeka asowe bas
Mwina kapena akanangomukhapa mikono, osamupha iyayi, cholinga azikhala akuziwa kuti kubadi sikwabwino
zomvetsa chisoni.
Wauma munthuyi kodi zibakela zokhazokha zimenezi????? Si embalm yimeneyi
…the police has urged the people not to take the law into their own hands… Which law, yoti usabe or usaphe? Yambani mwawaphunzitsa akubawo kuti asamabe, apo bii… atha onse!
Killing mmaidziwa inu? as far as how de congestion is in our prisons,I think dis cud solve de problem of congestion in our prisons & pano ma magistrate alipo ochepa!hahahaha dis is jxt another penel code of easiest sentence! Mwanza….mwapulumutsa ndalama za boma
chonde abale ake Amuthu waphedwayi kabwezeni basi adzazolowera. zithu. sakumasamala wina akatola walakwa. bwezerani modzimodzi
chondeeeee anthu aku mwanza mawa mkatipherekoso mbava zapa NDILANDE tatopa nawo ife asaaaaaaa!
i call that justice…… i have no sympathy 4 these thieves….
Mupheso ma gays onese alimugulu lambavazi
Komatu muzapha Yesu chifukwa azabwela ngati mbava.
yusuf ndiye yesu adabwera mokuba
Good move go a head
please we should not be taking law into our own hands…let the law of the land play is role…What about the thieve politicians living in the glass house has any of you throw stone to the glass house
adakakhala kuti adabwelapo pakhomo pako nkukubela mau wanenawa sudakasilira kudzawayankhulanso,akuba ndi anthu achabechabe osafunikilanso dziko
Kwasala inu ma gey komanso inu mumazembela akazi azinzanu MUZAFA IMFA YOWAWA.
nkhani ina iyi abale chonde mpaka kunyenga akaziayin.com
Mwaza,the Most Succesful District In The Year 2015 ,keep It Up!! Do The Same 2016
This is what we want, mbava ndi m’dan wa chitukuko, keep on killing all the remaining behind.
ngakhale ongonana amuna okhaokha….
????
akafika akanena zooona kwa anzake onse ankhalidwe ngt uwu Ameneyi sazayambilaso
YONSE BOOOOOOOOOOOOOOOOOOOOOOOOOH
Zinazi nzoziyamba dala,imfa ngati imeneyi oro Mulungu imamvetsa chison-kuphedwa kokuba,what a big shame!ma warning for those who think their so smart,don’t even think of doing it cos you’ll be nxt.anthu pano alusa .
Koma mwalangadi guys.X-mas ya boooooo
KEEP IT UP MWANZA,ANTHU A ULESIWA AKUSOWESA NTENDERE
achita bwino kwambiri,i edge all pipo to do the same
Anaba chani? mwina sichikufana ndikuchosa moyo wake!
Kaya anaba sipuni kuba ndikuba,chimozimozi tchino lilibe Wet Silichepa,lochepa laling’o ndi Gehena basi.
indimba.com
Ok mwapaya kawalala yayi chawama maningi
Ndikape, Anzake Amaba Mtauni Kuti Apolisi Aziwapulumutsa.. Kkkkkk Congrats!
Good pple.. keep t up
I support Mwanza residents, continue ndi ufulu wanu.
Mwaitha anthu akumwaza kumangolangiratu da same should apply to gay pipo
Mwaitha anthu akumwaza kumangolangiratu da same should apply to gay pipo
Well done killed thief
kkkkkkkk kkkkkk wasemphana nayo X-mas kkkkk
Koma #yohane saionad uyu ya chaka chino…my be next year azai3la
Achita bwino,apolisi akuMalawi ntchito yawo ndimowa osati kugwira akuba
nice development….!!! thumb up….do the xem to xo cald APM
I hail the killing of this guy as an important milestone towards reducing crime rate in Malawi.
pamenepa ndiye kuti chiwelengero (headcount) cha mbava chachepa ndi imodzi. kkkkkk
Welldone Mwanza residents. Ma Gays nso tiziwapanga choncho.
I will b so happy gay akazaotchedwa.
Yeah tikuyenera kupanga zoti azunguwo amvese kuti we are not ready
Athu amenewa kumawatero.. Thumb up mwanza
NAMFENSO KUNO TIKAMPEZA WAKUBA TIMUPHA CHIFUKWA TATOPA KUSEWENZERA AKAWALARA,
Mwaitha aku mwanza
Nkhaniyi yavuta akagwidwa mukapita naye kupolisi atuluka ndiye athu atani?
Apolice anatha mphamvu ndie mumati anthu atani? Azidikira zifwambazo? Aaaa
The first advice should go to those who have the desires of stealing that they should desist from stealing from the angry mob then to the public which has lost trust in the corruptive Malawi Police Services that they should desist from taking laws into their hands.
Thieve now breath a sigh of relief as they hear of taking them to police. Alot of thieves are getting assisted by police officers and some thieves are police officers. Police desist from breaking complainants hearts by avoiding receiving bribes.
Mob justice is evil. We shall realise the mement one of our relations gets killed innocent.
Too bad
Still some won’t learn a lesson