In a bid to have a competitive side next season, Malawi’s 2015 Carlsberg Cup Champions, Mighty Wanderers, are eyeing four players from relegated FISD Wizards FC.
In a social media post after his team’s victory over Wizards on Sunday, Nomads vice team manager, Steve Madeira, said it is time to do business with Peter Mponda’s side since they have been relegated.
He wrote: “[Levison] Maganizo, [Ernest] Tambe, [Isaac] Mwale and [Brighton] Munthali are too good to go down to play in Nsejjere, we might speak to Peter Mponda to do business.”
FISD have been relegated from the Super League following their 3-1 loss on Sunday to Wanderers and will be going back to Nsejjere Southern Region Football League, a season after being promoted.
makape inu afodyabullets zoona tim kumaipasa zina lachi2 chot enafe timagwirisa ntchit pokatrainer kkkkkkkk
Ngati aliko abwino agulidwe basi
Paja bullets next season ikusesa zikho zonse
Koma ndifodya adzisuta ku Nyasa buletiku anthuwa sapenga awa? Isiyeni Noma team ya anthu ozindikira iyi.
Let us do what ever we can do.what are you talking about? ukamagula chovala umakhala kuti ulibe choti ungavale?
muzchedwa nd kugula ma player ife tkutenga ligi
gulani pyanu ife team yathu njabwino and we re not panicking with that
Gulani muwakatamuse
Banja langongole mwaliyiwala nthawi yomweyi.
buy them those r best players 2016 wina anva m’bebe.NOMA 4 LIFE KKKKKKKKK
#Memory iwe wanu anakatola kangat ku mzuzu mukusewera ndi mzuni??????? Mpaseni mwana mpata akuthandizeni more over chipuwa ndi mwana wa fisd wachinyisa kwambiri ndi chipuwa kkkkkkkkk
Paja neba sumagula koma kuoda chifukwa ukagula u mak use of it koma ukaoda zina zimayamba kuonongeka ndizija umazipitisanso ku loan zija
usawi chichi…..ine olo atandithira dumu mkwamwa sindingapite kunoma…..ulendo okatha umenewo….mchiyani chomwe alibe kuti agulenso ma prayer ena….zamkutu basi….kufuna kupha ma player basi…
U can’t come 2 wanderers coz u r not a player. Luk at ur legs they r fragile
whatever the case l dont mind….wht is wanerers after all
Mudzawadyetsa chan anawa poti inu chili chonse mumachita loan?
Ife chathu nchiyembekezo mwainu bas mmat mugula kenako timva zot ndi roan bwanji simutiuza zowona? Ife masapota
Timu Ndimaplayer
Kkkk neba tsopano mungotenda team yonseyo muphatikizane chifukwa kusewera mu super league simasewera
Ku nankhaka wotchinga pa goal la nyasa united adatola mpira katatu muwukonde.Apaseni a nyasa goal boyi uyu.
Keeper yemweyo anoma anakanika kumuchinyatu paja and which is on kuxhinyidwa 3 ndi Blue eagles and kuchinyidwa 3 ndi mzuni?
kuchinyidwa 3-0ndi blue eagles mkopasa manyazi.Tinalephera kumuchinya coz inu mudalowa 12 kuphatikiza ngoleka,Mwayiwala
kuchinyidwa 3-0ndi blue eagles mkopasa manyazi.Tinalephera kumuchinya coz inu mudalowa 12 kuphatikiza ngoleka,Mwayiwala abudul??
milan kachingwe u r right best players r zea oredy bt exectv are u gvng the players an apetiser -4 hardwork????akuvtkapa ground nd ena odwelera ndnu amaudindo,,,sinthan nkhalog…….Nyererf moto unandi proud of u guyz
Tangokonzani team yomweyo zinazi ayiii!!!!
osapanga mantain squad imene muli nayoyo bwanji anyamata mwagula kumene ndiye mukufuna muonjezere ena pamene coordination ikumakuvutani.a BB titenganso chikho mu 2016
Sizikugwilizana man.
ndipo ndiye @ Memo
zikugwirizana!! Ma player 60 aja mukufunanso ena a ntchito chani?? Muwasonkhanise onsewo then mupange select ndipo tikunyenyerani limozi
Ntchito kuononga ma player bax mix
Mudakapikulabe? yesani kupanga maintain team yanu. You already have good players honestly. Plz. Don’t buy just bcoz you hv money…….learn from Bullets
Season ino tachititsidwa manyazi ngati kuti sitinatenge cup. Timkafuna super league, koma tinalephera kupenga, mapuleya a bwino kuposa team iliyonse mdziko muno koma maseweredwe mbola, tilibe odziwa kuchinya pa free kick, bwenzi tili ndi ma points ambiri. Ine ndikuti ma player agule osapitilira 5 komanso ena aulesi aone msana wanjira, ma player omwe ndi ma sapota a Wanderes ndi ochepa koma akukhalira ntchito kumene kunja ndiye amaphonya dala pa golo. Choncho mpofunika kumatenga ku Wanderes Youth ma player chifukwa ndiye ana enieni a Manoma omwe angamapange zofuna zathu akalowa mubwalo la za masewero, magazi ao, mu mtima mwao ndi maganizo ao ndi a Wanderes ndithu.
sanudi kaliyati sulumba ndi ena ali pa loan mugula ndichani cashgate fc
Pa loan kapena kugula? Pajatu zogula sikwenikweninso
N’zofunikira Zimenezo
gulani zimenezo manoma tipange matimu awiri A ndi B,B izisewera ndi bullets coz bullets simatha mpira A izisewera ndi matimu ena
BIBI imati bola kutsogolo tikachinye nanji panopa adaledzera ndi ndudu zasponsor @2010, UMBONI 3_0 ndi blue eagles, sankauona ataledzebwa nazo ndudu or titi fodya.
kkkk ukuziwa kale ndaona mboba
Umboni wonanso ndiwa ku Mzuzu Noma3-0Nzuni
Umboni wonanso ndiwa ku Mzuzu Noma3-0Nzuni
hahaha mfana osamayesa opposite
bb inamenyedwa 3-0 ndi team ya pa #3 nanga mpaka ka mzuni komweka takathizimula zanazaka?
nanunso tikuonerani ndi ana tawavinira chinamwaliwa kuti nanu mupanga nawo bwanji?
Ma player achan? Onse omwe tlnao aja atan? takwakobas
Ma prayer achan? Onse omwe tlnao aja atan? takwakobas
tiye natoni timafanato… ntasize yanu kkkk
Munakagulabe,simunatengelebe phunzilo eti?kuti kugula mwa chipiku sikuthandiza?
Zoona zake noma ndi dilu
gulani good for fisd players
Maplayer alipo okwanira palibe chifukwa chogulira ma player ena, what for? Ofunika kungoipanga build up Noma ili bwino kale.
Kkkkk maloto achumba.
Yaa Dats Exactly W@ We Need Titolele Timamfana Taboh Kt Seaso Ya Chaka Cha Mawa Tizaiyambe Ndikuimaliza Bho.
Gud idea
ndukuonjezeranso kuti maplayer asagule ku team imodzi ai koma akanotola mwapondiapo kuti asankhe abwino osati kutenga gulu laanthu ochokera mbali imodzi ai chifukwa izi sizingatithandize konse
ndizofunika zoonadi koma player ameneo ndi aserious kuti aseweradi molimba kapena angofuna malipilo basi chifukwa ndie asaononge team ai nanunso osankha maplayer onesesani kuti mwagula player ofunika osati kugula ndie azizatinvetsa kuwawa mutu ndithu
we can have all the best Players in the world but with poor Administration we will keep on loosing the ball. Focus on administratives issues.Noma has better players already
anatenga 14 players pa loan last season, zawakanika akufuna aonjezerenso ena 4? zinthu sizisintha adzapitilira ntchito yawo yosasa jekete la bwana BB kumbuyo
Thats Gud #Manoma