Transfer News: Nomads targeting four Fisd Wizards players

Advertisement
Brighton Munthali
Brighton Munthali
Munthali: Also wanted at Nomads,

In a bid to have a competitive side next season, Malawi’s 2015 Carlsberg Cup Champions, Mighty Wanderers, are eyeing four players from relegated FISD Wizards FC.

In a social media post after his team’s victory over Wizards on Sunday, Nomads vice team manager, Steve Madeira, said it is time to do business with Peter Mponda’s side since they have been relegated.

He wrote: “[Levison] Maganizo, [Ernest] Tambe, [Isaac] Mwale and [Brighton] Munthali are too good to go down to play in Nsejjere, we might speak to Peter Mponda to do business.”

FISD have been relegated from the Super League following their 3-1 loss on Sunday to Wanderers and will be going back to Nsejjere Southern Region Football League, a season after being promoted.

Advertisement

58 Comments

 1. makape inu afodyabullets zoona tim kumaipasa zina lachi2 chot enafe timagwirisa ntchit pokatrainer kkkkkkkk

 2. #Memory iwe wanu anakatola kangat ku mzuzu mukusewera ndi mzuni??????? Mpaseni mwana mpata akuthandizeni more over chipuwa ndi mwana wa fisd wachinyisa kwambiri ndi chipuwa kkkkkkkkk

 3. usawi chichi…..ine olo atandithira dumu mkwamwa sindingapite kunoma…..ulendo okatha umenewo….mchiyani chomwe alibe kuti agulenso ma prayer ena….zamkutu basi….kufuna kupha ma player basi…

 4. Ife chathu nchiyembekezo mwainu bas mmat mugula kenako timva zot ndi roan bwanji simutiuza zowona? Ife masapota

 5. milan kachingwe u r right best players r zea oredy bt exectv are u gvng the players an apetiser -4 hardwork????akuvtkapa ground nd ena odwelera ndnu amaudindo,,,sinthan nkhalog…….Nyererf moto unandi proud of u guyz

 6. osapanga mantain squad imene muli nayoyo bwanji anyamata mwagula kumene ndiye mukufuna muonjezere ena pamene coordination ikumakuvutani.a BB titenganso chikho mu 2016

 7. Mudakapikulabe? yesani kupanga maintain team yanu. You already have good players honestly. Plz. Don’t buy just bcoz you hv money…….learn from Bullets

 8. Season ino tachititsidwa manyazi ngati kuti sitinatenge cup. Timkafuna super league, koma tinalephera kupenga, mapuleya a bwino kuposa team iliyonse mdziko muno koma maseweredwe mbola, tilibe odziwa kuchinya pa free kick, bwenzi tili ndi ma points ambiri. Ine ndikuti ma player agule osapitilira 5 komanso ena aulesi aone msana wanjira, ma player omwe ndi ma sapota a Wanderes ndi ochepa koma akukhalira ntchito kumene kunja ndiye amaphonya dala pa golo. Choncho mpofunika kumatenga ku Wanderes Youth ma player chifukwa ndiye ana enieni a Manoma omwe angamapange zofuna zathu akalowa mubwalo la za masewero, magazi ao, mu mtima mwao ndi maganizo ao ndi a Wanderes ndithu.

 9. gulani zimenezo manoma tipange matimu awiri A ndi B,B izisewera ndi bullets coz bullets simatha mpira A izisewera ndi matimu ena

  1. BIBI imati bola kutsogolo tikachinye nanji panopa adaledzera ndi ndudu zasponsor @2010, UMBONI 3_0 ndi blue eagles, sankauona ataledzebwa nazo ndudu or titi fodya.

 10. Yaa Dats Exactly W@ We Need Titolele Timamfana Taboh Kt Seaso Ya Chaka Cha Mawa Tizaiyambe Ndikuimaliza Bho.

 11. ndukuonjezeranso kuti maplayer asagule ku team imodzi ai koma akanotola mwapondiapo kuti asankhe abwino osati kutenga gulu laanthu ochokera mbali imodzi ai chifukwa izi sizingatithandize konse

 12. ndizofunika zoonadi koma player ameneo ndi aserious kuti aseweradi molimba kapena angofuna malipilo basi chifukwa ndie asaononge team ai nanunso osankha maplayer onesesani kuti mwagula player ofunika osati kugula ndie azizatinvetsa kuwawa mutu ndithu

 13. we can have all the best Players in the world but with poor Administration we will keep on loosing the ball. Focus on administratives issues.Noma has better players already

 14. anatenga 14 players pa loan last season, zawakanika akufuna aonjezerenso ena 4? zinthu sizisintha adzapitilira ntchito yawo yosasa jekete la bwana BB kumbuyo

Comments are closed.