Police in Malawi’s Mulanje district are keeping in custody a Radiographer at Mulanje Hospital for allegedly attempting to rape a woman.
Police identified the man as Kenneth Mkoningo, aged 28. Mulanje Police Spokesperson, James Kadadzera, said the suspect was on Wednesday examining a woman (name withheld) who had gone to the hospital to confirm whether she was pregnant or not.
“He told the woman to lie down on bed naked to scan her, then he started putting his fingers into the victim’s private parts while the other hand was caressing her breast,” said Kadadzera.
The woman later rushed to his husband who was outside and reported the matter to health officials at the hospital who reported Mkoningo to police.
Mkoningo hails from Benjamin Village Traditional Authority Kilipula in Karonga district. He will soon appear before court to answer charges of attempted rape.
Palibe nkhani apa!….. doctor amagwira ntchito yake
koma,amayi amenewo kungowagwira kumaliseche basi,nkuthamangira kukasuma?Bwanji samadziyyetsa wokha kwao?sono amganidza kuti ayedzedwa motani?kkkkkkkkkkkk zinadzi?
lamulo limati ngati ukumuona patient wamkazi usakhale wekha you need to have a fellow health worker of the opposite sex
Azimayi this too much..kutsimikiza ngati uli ndi pakati nde mpaka wina akaone maliseche anu, why? Kuli ma rapid pregnant test kunja kuno..wekha kunyumba ukhoza kuzieza ndikuona zosatira..so simple. Sizotiso ndi zodula.. no.. Mma pharmarcy ati mbwee ntauniwa zimapeka. Ngati simutha kuwerenga kumufusa akugulisa mmenemoyo akuuzani..zinazi timaziputa dala kufuna kuyesa anthu ogwira ntchito ku chipatala…mwina zovulavulazo zimakusangalasani..iyaa
koma chipatala chimenenechi eeee
Is Malawi 24 a registered news paper? I think most of the news they airing are forces and make some people scares. komaso why are you not giving us the names of the journalists who are reporting those stories ?
Ndiye Umboni Wake Ukhala Woti Bwanji Pamenepa?
Paja Mulhakho Ndilero2 Osaiwala.
Akanamusiya agwire ntchito yake bwanji phuma iyeyo amaziwa chomwe amapanga – zantchito
Aliyense azikhla dokotala kodi? Medical officer and radiographer are two different people ka.
Its not a medical doctor… koma RADIOGRAPHER
Exh….. Kuchinda basi ngati alinyatwa..kusekula njira mmakwana doctor…CIVO-1 MIGHTY-0
nde ubwino wa ntchito ya u dotolo
Usamunamiziremzako
azimai ena amaonjeza kavaridwe akamqpita ku hos
what do you mean? You mean women should dress the way you want? and not the way they want? think before you utter!!!!!!!!!!!!!!!
It seems it’s his character. Should the law take its course.
Mwati radio grapher???
Fodya eti mxiiiiiiiiiiiiii!
Tinve ziti zoopsatu izi
Basi azimayi oyembekela adzipita kwa azaba
I don’t think this woman has any backing that the said doctor, whether radiographer, wanted to rape her. He was doing his job using the methods he knows. If she knows how to examine pregnancy, why did she go to the hospital? Only to term the method used was an intention to rape her? Thus nosense. She is insane I hope.
Mai openga ameneyu wapanga bwanji?anasowa zochita eti kufuna kutiipisira mbirii basi
Mai openga ameneyu wapanga bwanji?anasowa zochita eti kufuna kutiipisira mbirii basi
Ngakhale Ineyo Kunalibe Ndizoona Madokotala Pofuna Kuona Njira Mpakana Kumugoneka Pabeni Undress Her Ndeno Nulupisa Chala Chake Kumenekoko
he waz examining,ngati amayiwo adali ndi dzilakolako asamunamizire munthu coz doctor amayeneka kupisako ndithu ndi ntchito yake.
oh what a shameful act and what example to the youth from the so called leaders
kuyesa mimba mpaka kulowetsa chala kumaliseche? No no no no no thats shit, kodi zipatala zinazi samalora mamuna kulowanao muroom yoyezerayo? Ndinapitapo ndimkazi wanga kuchipatala for scan, koma olo chovala chimodzi sanavule. Anangoti takwezani malaya pang’ono ndufuna pambali pamchombo basi. Ineso ndimaona kalikose, amatiuza tose kuti kamwana ndi aka kali ndi miyezi iwiri ndi masiku awiri. Galu uyu amangidwe uyu asamusiye ayi sizoona amapangazo.
This Is Untrue Story
Koma Nde Zafikapo
Madalazi
Inenso za u lawyer ndikutali koma nkhani iyi, wachipatala akuiwina. Analiko anthu angati kumene amayezanako. Boma lidza mulipila dzindalama zankhani nkhani…..
U r threatenng medical wth ur unnecesary reportng dats y malawians r dyn innocently coz they dnt want 2 b examined,anywy hop consent waz gvn dats ok.
Medical officer si radiographer inu a Malawi24.
Masiku osiliza sikulina timva augona mtembo.
A radiographer is not a medical officer!! Please edit your article
Sorry
Thats not rape. Chimizi. Its an examination. Amangoyesa ngati. And it “her husband” not “his.husband”
shaa!!! its District News!!!?.
siine lawyer koma khani iyi ayiwina
Doreen Mphesa
Is that attempting rape or sexual harrasment? I just need to know.
Lets borrow his radiographic machine & scan this case….any anormaly seen?…i guess not…bax free d man,the woman only need clarification..
Anangotota Dokotalayo Nanga Kwathu Awiriwiri Amakulitsa Njila Ya Mayiyo
Awoman can not be raped because she is an adult.
Re-defining the meaning of “rape”. Bro what is “rape”. The end of the world indeed.
Says whom? where did u get that information that an adult can’t be raped?
makani basi ngati mumaona ,mmesa mayiyo anachita kuvula yekha.
imeneyo timayisha vaginal examination u can use two fingers or specularm maiwa angofuna kutiipisila mbili galu ameneyi
Ts ws a pelvic scaning amayiwo kumaona ngati walowetsa chala,mayiyo I ges anachita kutumidwa
Paja scene ikaphulika mkazi amapeza njira yozitetezera nkumati amafuna kundigwililira..kkkk,komanso madotolo mumaonjeza pomuyeza munthu wamayi woyembekezera,mpakana kumaona njira munthu ali ndipakati pa miyezi iwiri? sikungomuseweletsa munthu wamayi chonchi? kkkk
ahahaha. I am sure you dont knw what realy yu are talking. That is vaginal examination.iii pitani ku chpatala mukafunxe bwino.ZA HEAD TO TOE PHYSICAL EXAMINATION.
Ndikuziwa zomwe ndikunena,koma ndati madotolowo amaonjeza,upeza mzimayi amuyeza bwinobwino,watha zomwe amafuna kuchita monga ntchito yake koma upeza akungobweleza bweleza procedure yomweija,especially vaginal examination yo…
Tumbocid agwile ntchito
She must give us evidence coz i dont see any mistake with adoctor he’s doing his job thuswhy finger was in to check ngati akutundira ndi mphavu mwamuna wakoyo. Dont blame doctor
Osamayesa ogwila tchito zipatala ndimtenda oti mumupangitse doctor akupangeni zina ndi zina.sizisowa kuti muli ndi mimba.kumadikila thawi yokhazikika. Doctor in Action.
mukhapen nd 5 yrs
Wankulu sagwiliridwa ndibodza limenelo anapangana
Tikhulupilira apolice akayankhulapo pa nkhaniyi.Osati inu ayi.
why raping fully packed woman .koma zinazi !!!!!
….fully packed…..packed to the brim kkkkkkk.
kkkkkkk kwaaaaa really #peter to the brim indeed.
adokotala uku kachala kali kusite uku dzanja liri mmabele…kuu3la kumenekooo kikikiki
Koma tsiku lidzadutsa osavako nkhani zogwililira? The end of the world
Anapangana mwasoka anapezelera