The Bingu National Stadium construction in Malawi capital Lilongwe continues to be a target for thieves due to lack of security around the project’s parameters.
The Chinese funded stadium was due to be opened last August but theft of some relevant materials has delayed its completion.
Reports indicate that pipes which were supplying water to the pitch have been stolen, leaving the pitch dry.
In an interview with Zodiak Broadcasting Station, government architect McNight Munthali urged government to construct a police station at the stadium in order to tighten security.
Munthali said that security which is available is not enough hence the non-stop devilish acts.
According to Munthali provision of a police station around the stadium premises is the only sound solution that may ensure quick conclusion of the project.
As it stands, Malawians will have to wait longer than expected before the Flames kick a ball at the state of the art structure.
Malawi sazasintha malawi ndimalawi basi kkkkkk
Looks beautfl
Dick ulibho asati bingu stadium yankhulani ngati anthu onzindikila. Malawi national stadium!
Nyumba ikamachedwa kutha anthu amakabibamo kapena kuba ma flame chifukwa palibe mlonda
vuto lakuba anayambitsa ndi ameneyu
Ndine mtumbuka koma zikundimvetsa chisoni kuti wina akunyoza achewa, wina akunyoza atumbuka chonsecho nonse ndi A Malawi.enanu mukunyoza chonchi likafika tsiku la sabata ku church nkumalarikira kuti”abale tizikondana wina ndi nzake” enanu ndi atsogoleri m’mipingo yanu kapena mu ma mosque.
Koma kwenikweni chikuchitika ndichani,kuphsya kwamisika,umbanda ku stadium ya malemu bigman,kusiyasiya kwa madzi ndikuthimathima kwa magesi.koma Malawi yasanduka warm heart of chipululu.
Akulimbana ndi anthu osauka omwe amapeza thandiz ku business ya makala wht more anthu amene akuononga katundu wa ma millions!kathanenaoni2!!!!
tumbikalisim iz an ugly word
Apa nde ndi chimodzimodzi kudzibera zipangizo zomangira chimbudzi chako chomwe nkumangodalira cha neighbour , kuzolowera kuvutika basi .
Limeneli ndi gulu lokuba sugar kumakamwera tea kubafa Pajatu ili …
Mtandire pa spear head katundu umene ukupezeka iiiihh
Akagwira mbava aziipheratu this malpractice will eradicate
Can U c now am also a Tumbuka Hence no comment!!!!!!
Can U c now am also a Tumbuka no comment!!!!!!
dzina la stadium imupanga betray project
aba bwanji police ili pompo ?pamenepa ofunika intensive investigations.
Koma kunena kuti president akuba inu kumeneku kutani osamafulumira kuchosa chanzako chisoso
That is why it is better for them to use their own labourers and then hand over the finished project so we can destroy it.
Koma Ku Malawi Sikuzatheka
Jamanja akanyosyana chanti yele ana n weetu wampepe..jele xonophobia jele
Very bad
Amalawi eish
Shame!!!
muuzen uyoyo akhwimitse chtetezo..if nt nde atumbukawa ayawo nd alomwe akanaba.ayiniyakefe tkufuna tzchtleko gule wankulu pa stadium yabwnoy
kkkkkk
Yalowa kulodzana zala kodi, nkhani wina amvekere ndi atumbuka, ayao, alomwe eeee kkkkkkkkkk
Mtandire guys are sophisticated
the problem with our country everyone working in government or government funded projects is a thief and this has made our men in uniform also tobecome thieves akuona kuchedwa nde pano akutsogolera kuba ndi apolisi omweo
Musatinamize apa atumbuka mukati mwachita bwino ndiye mwakakhala ku lilongwe kapena bt.simwangodzadza kuno inu kumangoyankhula language yanu yausiru Mukuba ndinu nomwe
Machende Anu Amwene! Nyini Yamako.
Leave tumbuka’s alone.nyani iwe
Kodi ngati munthu achoka kumzuzu kuti kulilongwe NDE kuti ndimulendo kumeko
mbuz iwe eti…ngat kwan ndinu mbava zithele kwan konko
kkkkk koma kumeneko nyau izo
Sitidzalemela amalawi kudzibweza tokha mbuyo
Ngati Oyendetsa Boma Akuba(cashgate) Kulibwanji…
Ku Blantyre kuja mumaba za pa gate kuja?
Ozindikira etu
Comment Reserved.
I beg to differ.
Mw ndi otembeleledwa amadana ndichitukuko
Zovuta ndinthu
Stealing is Malawi culture
Nyerere za Noma zikuba…mxiiiiew
Akumaba police ilikuti?
Joyce banda soccer arena
Mabvuto azachuma anthu atani
Even if we, the malawian, go overseas particularly USA, we will make the USA country poor bcoz of stealing. U can just c on this…
Uwu Nde Uchitsilu Kodi Paja Achewa Mpila Ayi Eti Mnaiwala Kt Koma Nyawu Zitsilu Zakumwa Madzi Ometela Ndevu.Mukuba Chin2 Chomwe Cikupindulileni.Makape
y malawias whn r we going to change this is our on project
Atumbukawa sali sharp mmmmm……
why u cal it Bingu stadium?call it CHINA STADIUM
Last tym I checked we are gud at corruption, now we are adapting to be gud stealers, to make matters waste zochitatso kuthandidzida,,,,could we ever change?
Kukhala ngat #Gwamba nd #Crazy-G nd omwe akumasogolera kokuba
Koma ku malawi sikuzatukuka mpaka kalekale.mpaka kuonanga chituko? Mayiko ene atiseka choti muziwe.
Mwachoka Liti Kung’ombe Atumbuka Wochela Mutakalamba Sambirani Mukawone Ku Blantyre
Watch ur mouth….and de way u speak
Blantyre yake yiti? Kang’ombe bulding yokha basi
Machende Anu Amwene, Nyini Yamako.
Iwe blantyre ndiya mbwiyakoo?
Kutukwana Sikusova Vuto Muganize Zimene Mwanena Ngati Mayi Anu Alibe Ndathokoza Ambuye Akudalitseni
titus ngat kwanu mumagwa mulungu akukhululkile,koma ngat uli bwinobwino go to hell&rest in peace.mulungu akutenge lelo ufe basi
Iwenso Ufe Mukuwoneka Kuti Vuto Ndikochokera Kuzolowela Kutamba Ufi Wagwanayo Satana Walephera
LiLongwe ikozeke nose mukusamusidwa abwere atumbuka kumeneko mwitivich inu waku mozambic mukabe kumeneko akakupeni unsilu kuba malata achewa ndanyani bas …ukagwidwa iwe tidula manjao …..
.bwaphini
Atenge asilikali kuma barracks uko azikalondera dats der Job akungotha migaiwa ya boma basi…..
tsono chikuvuta ndichani boma ili ndi ndalama zambiri nkulemba wa guard koma cashgate mmmm mulibe anzanu.
Tikudzibela tokha amalawi, tasithani chonde.
Nchocho mukagwidwa akamati mukapedwe ndiye mudziti boma lankhaza anyani.inu mukagwidwa .kokhafela ndikundende nonse amene mumakhala ku LL panyo panu mapwaranu mbolizanu
ali bwino ndi abwanawo bank lawo liri ku america soka amalawi timamberana aphawi tokhatokha.
Mesa kuli ma CHINESE? Karate! Kung fuh! Ndi zina zoterozo zigwire ntchito basi! KUTETEZAAA
Ntandile eeeish akangoti atsegula within a months mipando yonse ya mma stand izazulidwa, even wire chidenga chija anthu asasula akakhomela zidebe shaaaa!!
paja achewa mpira ayi koma gule wamkulu bas?? mtisiyire ife akumpoto,anthu ozindikira ife…… anthu otani odziwa kuvina basi?
Ine si Mchewa koma #munthali apa sunayankhule bwino. Ground lija lili mtauni mmene mumakhala anthu osiyanasiyana. So why are you attacking chewa pple only?
kumpoto akaonera ndanii mpira
Kodi ngati akunena za kuzindikira. They are talking about theft iwe umawuswa mpirawo olo atakumangira stadium mkhonde? Wat is mpoto to be a leading province?
koma ma savage awa timatimu take tiwiri tija bac kkkkkk kodi kumpotoso ndkumalawi eti?
Iwe peleka maganizo oti umbava utha bwanji osat kumanyoza a cewa,achewa simbuli mbuli ndiwe sukumva zomwe akunena apa,ukalowenso mkasi
Kkk waupala wekha…tiye nazo kk
Wonthuni tamuwuzani aziyankha asamkhala phwii… ngati wolumpala ndebvu. Wapala moto kudambwe sugona. Kkkkk…
Paja Kumpoto ndikuti guyz?
chaku Afghanistan mu Islamabad… nde kumpoto!!
athu okuba pa MW pano ndi atumbuka ndawonera cash-gate dzonse
Sibwino…muzinena amene wayambitsa osati anthu a ku north we r all malawians no matter wat
Sinanga iye wanyoza achewa nanga
chokani achewa wosasamba wonunkha litsilo
poor achewa.go to hell.
atumbuka an2u opusa mumathawa kwanu nkumabwela mu lilongwe nd ku btz kut muzzaba bax……bwelelan kwanu mwatikwana….kupussa kwanu
Malawi
zakanika zakanika bax alonda aboma onsewa akumadzatigwira makomo atasowa zochitawa
zakanika zakanika bax
amenewo ndiwo achewa anazolowera nyau
Those stealing are actually workers at sight of project. People stealing in offices are same officers working in that office. No one will come from Mzuzu to steal at the project site. People stealing cement at project site are those people working at same project. People stealing maize are actually people who know us. Any thief knows very well where to steal, what to steal and how to steal. Let supervisors at project office mount campaign. You will find them already sold to someone. That someone will tell you sh/he bought from your worker.
Kmalawi asilikali amagwira tchito yanji cause iborn now am 25sindinave zakhondo then y osapitisa ma tata atatu they can gard there untill the project is done cme on
Vuto ndi bakha uja joice kutembrnuza kuti akhale wabwino malemu Bingu anaika kuti likhale ku blantyre amaziwa kuti anthu apakati koma kupalasira mmbali
pambuyo pake tidandaule kuti boma lopanda chitukuko; zathu zathu tikubanso
imatafna pomwe ayimangilila. papya tonola suzwa ntima wa moto
Anthu aku ellaz amadzola manyi mkumaenda maliseche at nyau nde alephere kukaba? Ai ndakaika manje
Ok tapulika so waba vichi?
Munthu alibe pabwino kutnso tionenetsetse nd anthu omwe amagwira nthito pompo amene amapereka ma mita
ife tinanena kale kut stadium imangidwe ku blantyre chfukwa timaziwa kut ku LL kwachuluka okuba kenaka timva kut akubako malata
kkkkkkk… kungomanga police station konko basi,mh mbava? hw?
aaaaa a police???
kkkkkk!!!
Mbuzi imadya pomwe ayimangilila kwainu ndizachilendo ngati
nde akubawo akufuna akaike pakhomo pawo stadiumyo? azikasewera usiku mpira wake mitu ya wanthu?, amalawi ndi agalu opanda pabwino sure!!!!
paja lilongwe ndimzinda wa cashigate afta kuseka zibowo zimatulukira dollar mwasowa zokuba tsopano mbuzi inu stadium yaku blantyre tu imenei mwava paja achewa mpira ayi koma kuvina nyau fotsek
usova inabwerabe pa central,aise.
Taitenge2 upite nayo kwanu
Aku BT musadandaule tangoinyamulani basi mupite bayo ku Chichiri
pasadi katole itole monga dzinalako kkkkkk solve better u shud nt get zero(0)
pasadi katole itole monga dzinalako kkkkkk solve better u shud nt get zero(0)
munthu wovesa chisoni, mzeru mulibe, kuganiza ngati Galu
Achewa mmalo moti muzilima mukulimbana ndikuba chitukuko cha mzika za kublantye shame on u chewas
akanamanga ku bt zonsezi sizikanachitika koma joyce anapangila dala kufuna kuwapasanso akuba anzache chotita iye kwinaku akulimbana ndi cashgate
malawi national stadium, to correct u…
ummm shame.malawi sazatukuka ndithu,no wonder ine kubwela kumalawi kuona akuti zomba highway ummm,misewu ya nkati ku mayadi kwa zungu kumaonekanso bwino kuno ku joni than umenewo
Basi nditumiza anyamata anga a #G4S apolice mwalepera ntchito.
malawi national stadium, to correct u…
Ma frnd its Bingu stadium not malawi national stadium as you are saying. May be you have grudges with late Bingu.
Its even written at the stadium “BINGU NATIONAL STADIUM.” amene akufuna Malawi National stadium adikire kaye.
I have never ever hrard this since born. Search around the world supeza even south Africa National stadium ukapeza achina Nelson Mandela bay Stadium.
Hahahaha Malawi National Stadium? Mwina neba wanganso ali ndi Mozambique National Stadium. Koma Zinazi hahahahaha
malawi national stadium, to correct u…
very sad
agalu amenewa ndi akum`mwera olo mube flames yabwera ku LL basi ng`oo akukutumaniyo wagwila palumbe
muavesese akubawo umphawi wakula pa malawi
abodza awa akasowa chochita amangopeka zolemba…
ndizoona even nkhan zapa Mbc Tv anena
other people they don’t appreciate the development mxim
Osangoyikakako millitary izingokwapula aliyEnse ongoti chimphonongolo biiiii kumeneko
Ndkanakhara Bingu ndkanangozuka ndku gafura chstadium chonse bas kunyanyara anthu osafuna malawi kutukuka
Anthu agule wamkulu ndi choncho ,muona akamanga yathu pa kanjeza smart ,Kkkk koma nyau basi
Ndapolice Omweo at Madeal amadyera M’momo
pa central region chitukuko chidzikuvutani,chifukwa cha uchitsilu ngati umenewu.
Nochibwe Mmewo dala.
#SomeMalawians stealing there Own Properties
ku lilongwe ndikwa mbava et?
It is sol woryd that some of the thives are project leaders they do comincat with joniors of the compus throw gards this leaders are the most development distroyers
pani ku lilongwe kuli mbava zoopsa kuposa ku ndirande…..kukubwerako azangonyamula ndi stadium yomweyo
how are there goin to steal while police iz there?then ndiomwewo apolice akuziwana choncho sitingatukuke
vuto la amalawi ndi limenero
how are there goin to steal while police iz there?then ndiomwewo apolice akuziwana choncho sitingatukuke
Nde OCHEWA omeneo.
Bodza ili
aaa chinthu chot chingapindulire dziko inu kuba bas asaaa
Y ma fellow countrymen amalawi sitizatukuka baxi.
Umenewo nde umoyo wapa malawi kukhalira kuba bax koma boma likalakwisa kulalata ngati ndife anzeru
but i always see a police land cruiser pick up full of PMS officers going to and from the stadium so how come theft cases are stil taking place. Opening a police station is not the only best solution since the p olice s always available , just talk to the police on this they might b in a better position to kno more on this
Is it not likely the police are helping to rob the site?
yes thats it they r part of it……they cnt b proffessional
Kodi amalawi munatani simuwona zabwino muwononge basi nonse aku lilongwe ndinu zitsiru mwamva.
mbava
Mboli yamako mbava iwe agalu inu simuwona zabwino ana masikini opephesa inu zitsiru zachabechabe #Gerard.
a#gerie chisiyen chi bakha chimenech ndichakum`mwera zakuwawan flames yafka sopano mu captal city ~ mwina matimu osauka opanda ma stadium aja apeze mpata
Ndiye ngati mukusangalala kuti muzionera nation team nanga mukubera chani makhebe akapolo inu munya agalu inu akakugwirani malala pipe inu akukwizinganu.
kkkkkkk ndikumva kukoma mukamatukwanana mitundu amalawi nokhanokha, tiyen naxo
Not all from LL are stealing &I believe its a small # of pple .
Zitsiru Zakum`mwera Zikufuna Kutisokoneza olo mube koma say gudbye 2 flames muzionongako trasprt ng`ooooo!!!!mboliro