Activists to Mutharika: ‘Stop being reckless!’

Advertisement
demos
Billy Mayaya
Mayaya: We need change..

Besides being told to reduce his spending on travels, Malawi President Peter Mutharika has been asked to wake up from his slumber to end corruption as well see to it that donors get back to Malawi.

A petition that was presented by Human Rights defender and social commentator, Billy Mayaya to officials at the Lilongwe City Council officials in a vigil on Tuesday has drilled the Malawi leader on several issues that have been hitting the nation lately.

The peaceful demo according to reports saw law enforcers outnumber the demonstrators and also had low turn up because there was another ongoing vigil in the same city.

Among other things, the petition breathe anger over dwindling of health service delivery in Malawi hospitals.

demos
Demos on SDGs had parallel aims with the other vigil.

Speaking after presenting the petition, Maya said that the patronage was not a set back and the fact that the petition was delivered, it was enough.

“Day in day out we continue to witness the continued decline in quality of services in provision of service delivery in key sectors such as health, education and energy. We demand the President to address these concerns,” said Mayaya.

There were no cases of violence reported by police.

The other demonstration was aimed at raising awareness for locals to support and own the Sustainable Development Goals (SDGs).

The petition titled “SDGs are the hope for millions of Malawians let us unite to implement them,”

Activist Luther Mambala led the demos.

Advertisement

56 Comments

 1. 2018 muzamvotere KENDO.CHAGONA.kuti malawi azasangalale chifukwa aliyese azapasidwa mwayi opeza china chilichose chomwe akufufuna

 2. Vutor royamba ndirimenelo munya muuna mumapanga matama kuuna ngati mwapambana pano ndi zimenezo chimwemwe chasanduka chisoni mumkadzicha wozindikira munya ndameneyo wangoyamba sanati

 3. Kukula mutu konseko ndimayesa multi nzelu
  Kkkkkkkk mwango nzazanamo atonkhwtkhwe

 4. Amene analemba constution yathu sanali opusa kuti m’Malawi tizikhala ndi ufulu wa zionetsero iyayi,amabungwewo, azipani zotsutsa amathandiza kwambiri mdziko liri lonse limene muli ufulu wa zipani zambiri.koma bvuto la inu ame mukutsutsa nkhani ya zionetsere ndi kusaenda komanso kusapita ku sukulu(umbuli).

 5. It’s very difficult for uneducated people like southerners (akumwera) to understand the meaning of “peacefull demonstrations” choyamba fufunzani kaye tanthauzo la zionetsero ndi pamene muzipereka ma coment anuwo.keep up Billy Mayaya we are very proud of You.

 6. Ma donors anathawa tym ya JB due to her cashgate, so they pulled there K40 in every K100 that supports the budget. And i dont see any sense when sumbody says, president atule pansi udindo akukanika kulamula. Ngati ma activists ali a nzeru kwambiri, bwanji abwenzeretsepo K40 yo but zamathanyula ayi. Ngati sangathe kubwezeletsa K40 yo pa K100 iliyonse ya budget, they better shut up their stinking mouth……

 7. Kodi mavutowa akabwera momafulumira kuchula olamulira bwanji anthu ife tilinawonso udindo othesa katangaleyo mudziwe kuti poponda anthu sipangakhale president komanso kupanda otsogolera ndiye kuti tikhala out of line ndiye tsiku lina tidzakuyesani tione ngati mudzakhale abwino kwa onse

 8. Mayaya alibe nzeru uyu ,ati akufuna donnor aid mmalo mopeleka nzeru yoti dziko la malawi liziyimire payokha koma ali kakaka pa donnor aid ,zongodziwikilatu kuti zochita kutumidwa izi

 9. all activists have corrupted minds. sons of demons practising immorality, evil doers, lovers of themselves, lovers of money rather than God, power hungrey. they proclaim piece yet destruction hinds under their tongue. Unless they repent hell is waiting for them all.

 10. The same fools pushed donors out after publishing negativity of this country….and u think we are fools to listen to ur stupid calls ……kkkkkk amisala mwachuluka kumeneko ofunika mupite ku mental……

 11. Kod ndrama za kaelekela nd gold wa malawi zimalowa pati?cz malawi daily ali mmavuto nanga ndrama zmene mmabazi mmazitenga kuti?ndrama zothandizila anthu ku boma kulije kwa zau NKHWIBI ni bweka waka akazachoka pa mpando tizanva ali ndi ma acc azithumba kunja nanji anabadwira kale ku hamereka eishhh komatu kaya bolanso kamuzu ndithu cz mbala zinaz nde zkuonjeza anatiwelenga kale kut amalawi ndife opusa nde eee mavuto kwabasi kenaka azatiba ndife tomwe koma cancer izakulangani

 12. kukula mopempha/modalira basiii. mayiko ndi mabungwe othandizawo sizikuwayendera nde pano nkumati aPulezidenti itanani madonor abwere. Aaaa we are not serious. Basi kulilira kupempha mmalo moti tipeze njira zodzithandizira komkuno kapena tidzilimbikitsana kuti tidzitukule kwathu kunoo tokha. Enawa ndi masewera ambassador wakuGermany adanenetsa kuti tidzilimbikire tokha kudalira kuchepe ndelero ife timvekere obwana kadzipitani kukapempha. Kungozolowera mmene kumbuyoku mapemphedwe nde basi tidzingopempha nayetu ogawayo zamuvutatu. Tisinthe maganizo apa Paradigm shift of begging to self sponsorship living.

 13. Titha kuguliratu Chimanga before kukwera mtengo mkumazadya nthawi yoti chakwera mtengo plan yothandiza imeneyo guys. Koma mowa tichepese mkazi osangomukhazika pakhomo kumpasa zochita azitakataka

 14. Mr Mayaya and your friends we don’t need donor support we need strategies to make us completely independent for how long will we continue begging for donor aid??

 15. mukuchedwa nzimenezo mmalo moti muitanile pamulungu kuti athandize malawi? some situations are byond man’s ability…nzofunika ambuye izi, mo time to waste, meet Christ ndipo kulira konse kudzatha

 16. Thinking of donors aid is total waste of our precious time. Lets accept our situation and start doing things in a more positive way to come out of this awkward situation we are currently in.

 17. Kulasa mtengo ndi chamuna chomwe ,wandisokosela nkulinga utamva.mr mayaya mwayesesa mapelekapo maganizo anu,Pali anthu ena a mitu ya nantogwe ,azilemba zokunyozani ,ndi amantha ndiwopepera sangawiligule ,moti amawona ngati ndalama zomwe boma limagwiritsa ntchito zimachokela nthumba mwa a pulezidenti sadziwa kuti ndi zawo zomwe ndipo ali ndi ufulu ofunsa ngati asakukhutitsidwa ndi momwe ndalama zawo zikugwiliysilidwa ntchito

  1. alibe kanthu ndi kabawi mphawi ngati Ine ndemwe. nde kuti dzikoli ndi lanu nokha olemweranu? osawukafe tisamafunse tizingosekerera Kaya ziribwino Kaya ziribwino chifukwa choti ndife asendesende ongonela chiguduli kufunda chomwecho .

 18. I think this dull headed Mayaya is missing dreams. Agree with you who drawed an example from Zambia, the people found it worthy holding National Prayers instead of eyeing for demonstrations. This crisis you see Mayaya are not for malawians alone, all over the world people are crying for some thing worthy their living.

 19. koma mphevu imeneyi ndye itivuta ngat udindo wamukulira ujeni uyuyu amene mmati kaya ati amamuti Pitala ausiye azipita kwao kuja kuli ndalama zake kuja ~azikazitafunira pafupi

 20. big up Mayaya we r on the same lane….I hope I’ll catch up with u soon…Malawi need to wake up n fight against poor leadership….

 21. Anzako Ku Zambia anaitanitsa mapemphero to solve their country problems. nw iwe mavutowo utawawona instead of coming out with de solutions to solve dis basi chopusa chomwe waganiza ndima demo mxiiii stupit minded…

  1. zimene anayambana ndi boma lo ife zisatikhuxe bt what w’ve learnt from our neighbour “ZAMBIA” i thnk dats de solution coz mulungu ananena kale” pemphani kwa ine ndipo muzapatsidwa”

 22. Iwo ndalama zawo zili pathumba iwe jean yako ya mwendo umozi wautali wina waufupi veyaveya mumsewu ati mademo mfundo zomwe zili mu chikalatacho bwanji kungokambirana. Nanga zikapanda kutheka mademonso iyaaa ndalema nanu tsopano. Mayaya Mayaya wachani amandigulira mgaiwa ine, mxieeeeew!

 23. Actions speak louder than words. Industrial actions can best awaken this govt from its slumber but not just walking.

Comments are closed.