Malawi Police in Nkhatabay district have arrested a 21 year old man for swindling villagers of K8, 000 by impersonating an aide to the district commissioner for Nkhatabay.
According to Nkhatabay Police publicist Ignatius Esau, the suspect Maxwell Manda went to Chavuka village in the district and told members of Mtukula Mudzi Association that the district commissioner will give them MK30, 000 but asked each member to first give him MK2, 000 as processing fees.
“The message convinced four members who paid the amount instantly while one member suspected foul play and went to ask the district commissioner who denied knowing Manda.
“The matter was reported to police who quickly arrested the suspect and recovered the money,” said Esau.
Manda has since been charged with obtaining money by false pretense contrary to section 318 of the penal code; an offence that attracts a minimum of five years in prison with hard labor.
Town sisunga kape ndi ndolo ameneyu
Koma ku Malawi ena kuba ndalama zankhaninkhani koma kuli ziii uyu waba 30,000 kukakamira kwakeko
8grand yachepa amasuludwe
A Goodwinnie Paligolo, mwalembatu zopepelanapa, kani mlomwenso ndi munthu? Kkkkkkkkk I don’t think so! Better u compare mtonga to fellow munthu not to chinthu chosaziwika ngati ngati mlomwe wamva iwe?
Ngati akuyamba peter iye atani tamusiyani ntchito kulibe ku khata bae akudyela zelu ameneu kkkkkk
Zofuna zamtima wake kkkk
Let him face the charge &be sent to prison
PALI MBAVA ZAKUBA NDI MATUPI AWO,NOW UYU WAKUBA NDI PAKAMWA PAKE LUSO LIMENELO.GWILANIPO JOB APOLICE AZOLOWELA AMENEWA.
mtonga kuberedwa zoti ndiwolalata ndikubwebwetuka zosaziwika…!! Mlomwe sangampange zimenezoooo….
kkkk ndalama yavuta abale inu bwanji osapeza njila yina yopezera ndalama
ndalama yavuta pa nyasaland
Kuzolowela za ulere akuti sabuside akalamucheje?
Musiyeni dziko laolakale ili,ndalama akugawana akumipando iye ndie atani?zikutiwawatu.
Kwacha yashupa pa nyasalande man
Good move rather than armed robbery….amasulidwe
Kkkkk #bay
kkkkkkk
Kkkkkk maluzi avuta pa nyasaland
Amalawi tisagone! ziwan kt anthu akuba achuluka
KUPUSA ATONGA….#CHELSEA FC ON DA MOVE
Kikikikiki