Tipita kukhothi ngati sitiyankhidwa – atelo amayi
Amayi omwe amachita zionetsero lachisanu zosakondwa ndi kusaikidwa kwa azimayi ambiri m’maudindo aboma, ati ngati mtsogoleri wa dziko lino a Lazarus Chakwera sawayankha madandaulo awo, atengera nkhaniyi ku bwalo lamilandu. Wanena izi ndi Maggie Kathewera… ...