Musawakwezere malipiro – yakuwa mokweza banki yaikulu
Banki yaikulu mdziko muno ya Reserve yalangiza boma la Malawi komanso ma kampani omwe siaboma kuti asakweze malipiro a ogwira ntchito awo nsanga ponena kuti zitha kusokoneza chuma cha dziko lino. Izi zayankhulidwa lero mu… ...