
Chakwera azawina ndi 70 pelesenti – Chilenga
Phungu wa Chitipa South Werani Chilenga yemwe wajoyina chipani cha Malawi Congress (MCP) posachedwapa akuti m'tsogoleri wa dziko lino Lazarus Chakwera azawina ndi 70 pelesenti ndipo sakuwopa chipani cha DPP. "Zomwe anthu akumakamba kuti palibe… ...