Zipolowe za ku Limbe ndinanenera kalekale – watelo mneneri Mtupa
Mtsogoleri wa mpingo wa Holy Palace Cathedral International, mneneri Rodrick Mtupa, wati kumayambiliro a chaka chino iye ananenera za ziwawa zomwe zachitika ku Limbe mu mzinda wa Blantyre ndipo wapempha anthu kuti apemphererebe dziko lino… ...