Sindingapangire kampeni UTM itandipatsa mavoti 21 okha – delegate wa chipongwe wabangulitsa Kaliati
Yemwe anali mlembi wa chipani cha UTM komaso ponda apa nane mpondepo wa malemu Saulos Chilima, Patricia Kaliati, watemetsa nkhwangwa pamwala kuti sangapangile kampeni chipanichi pomwe adapeza mavoti 21 okha ku konveshoni yapitayi. Iye waloza… ...