
Masankho akubwera pa 16 September sakufunika ndale koma kusintha umoyo – Kabambe
Mtsogoleri wa chipani cha United Transformation Movement (UTM) a Dalitso Kabambe ati nthawi yakwana tsopano kuti masankho omwe akubwera pa 16 September 2025 aMalawi asayang'ane kwambiri ndale koma kusintha umoyo wa anthu kuti ukhale bwino… ...