![Namadingo said this in Times Exclusive interview with Brian Banda aired on Times Television on Saturday.](https://malawi24.com/wp-content/uploads/2024/01/Patience-Namadingo-t-276x176.png)
“Ndani amapeza vuto ine ndikamwa mowa?” – wadabwa Namadingo
…wati u Doc wake pano ndiwa #DocAnavaya osati wa UNISA Ngati munalibe bandulo ya intaneti kumathero a sabata yatha, zambiri zakuphonyani, komabe tikutsinani khutu pang'ono: Oyimba Patience Namadingo watsindika kuti iye siwoyimba nyimbo zauzimu, mukamuona… ...