Namwino opuma agulilidwa nyumba ndi Triephonia Mpinganjira
Mayi Triephonia Mpinganjira, omwe amadziwika bwino ndi kuthandiza ochepekedwa m'dziko muno, agulira namwino opuma nyumba ya ndalama zokwana 30 miliyoni Kwacha. Mayi Ireen Tembo, a zaka 66, anali namwino ndipo agwira ntchito zipatala zochuluka kuphatikizapo… ...