“Ndale zaku Malawi ndizaufiti”: Mtambo wati sanagwilitse munthu ntchito
…ati zionetsero zija ankafuna kusintha zinthu …ati boma lapitalo linkafuna kuwapha A Timothy Mtambo omwe posachedwapa anali nduna ya mgwirizano, atsutsa mwantu wa galu kuti anangowagwiritsa anthu ntchito pochita ziwonetsero kuti iwo apeze zomwe ankakhumbira.… ...