
Mphunzitsi wanjatidwa kamba kobela anthu ponena kuti ndi wapolisi
A polisi mu mzinda wa Lilongwe ku Area 3, anjata a Jonathan Nkhosa yemwe ndi mphunzitsi wa kupulayimale wa zaka 51 zakubadwa, kamba kobera anthu powanamiza kuti ndi wapolisi. A Nkhosa akhala akuchita bodza kwa… ...