Azipembedzo alimbikitsidwa kuchilimika pa ntchito yogonjetsa TB
Pomwe dziko lino likufunitsitsa kuthetsa matenda a chifuwa chachikulu cha TB pofika chaka cha 2030, langizo lapita kwa atsogoleri a zipembedzo komaso owatsatira awo kuti akhazikitse njira zosiyanasiyana zomwe zingathandizire kugonjetsa nthendayi. Izi zakambidwa pa… ...