Nyerere zakwelanso pamwamba
Mapeto a sabata awa anali okoma kwambiri kwa nyerere. Atagonjetsa timu ya Moyale pachiwelu, dzulo anaswanso khofi kwa ana asukulu a Mzuni pakwawo pomwe. Pa masewero amene anachitika pa Mzuzu stadium a mpikisano wa ligi,… ...