Silver wa ku CAF, Mponda atiwuze player amene akufuna tigula
Gavanala wa Reserve Bank ya Malawi, a Wilson Banda abetchela Peter Mponda ndi osewera ake kuti apanga chilichonse chofunika kuti timuyi isewere mu CAF Champions 2025. Poyankhula atatha masewelo ndi Premier Bet Dedza Dynamos pa… ...