Bushiri, Mboro khethekhethe tsopano
Ati asiya zokokanakokana. Tsopano ndi amodzi ndipo agwilila ntchito limodzi. Ndipo apo mwaona Bushiri, yembekezani kuona Mboro. Mneneri Shepherd Bushiri amene ali ku South Africa ati wagwilizana ndi M’busa wa ku South Africa komweko wa… ...