
Chomwe mukufuna kuchita chitani mwansanga -Usi
Atalankhula modzifutukula ku nyumba yawo ya boma ku Mudi mu mzinda wa Blantyre nkumati chomwe akufuna a UTM achite mwansanga chifukwa atopa ndi kumangowazungulira m'mbali, a Michael Usi tsopano mawu awo aphera mphongo pamene awachotsa… ...