
Anandithamangitsa mu chipani cha UTM – Usi
Wachiwiri kwa mtsogoleri wa dziko lino a Michael Usi ati iwo sanachoke mu chipani cha UTM koma anangothamangitsidwa. “Ndati ndikonze malo amodzi. Ku UTM sinachokeko koma anangondithamangitsako ndipo anthu ache ali pompano. Sikuti ndikudana nawo… ...