
Namadingo sanapochere nawo K200,000 ku nyumba yachifumu ya Sanjika
Zadziwika kuti woyimba Patience Namadingo yemwe pakatipa watchuka ndi nkhani yoti amatchaja K10 million kukaimba malo amodzi, Lachinayi sanatenge nawo K200,000 yomwe nyumba ya chifumu idapeleka kwa achinyamata omwe anakacheza ndi m'tsogoleri wa dziko lino… ...