
Amangidwa kamba ka kupha mzake mchaka cha 2015
Mawu oti mulandu si uwola aphelezera pomwe Apolisi ku Bolero m'boma la Rumphi amanga Giuele Mfune pomuganizira kuti adapha Magowa Mtambo mchaka cha 2015. A Mfune akhala akuthawa kuyambira 2015 ndipo amangidwa anthu akufuna kwabwino… ...