Titseke maso tipemphele – Chakwera alengeza za kusala kudya kwa masiku atatu
Pamene mliri wa korona wayamba kufala mopanda mantha m'dziko muno, mtsogoleri wa dziko lino amenenso ndi m'busa Lazarus Chakwera wapempha kuti a Malawi asale kudya. Mu chikalata chomwe chatulutsidwa ndi nduna yofalitsa nkhani komanso mneneri… ...