
Mnyamata wa zaka 16 wagwililira gogo wa Zaka 74
Apolisi m'boma la Ntchisi akusunga mchitokosi mnyamata wa zaka 16 atagwililira gogo wa zaka 74. Malingana ndi Mneneli wa apolisi ku chigawo cha pakati kum'mawa a Esther Mkwanda, nthawi ya kumasana pa tsikuli mnyamata anatsatila … ...