Letsani mitala ndipo pasapezeke obeleka ana oposa awiri – Phungu auza boma
Phungu wa dera la kumadzulo mu boma la Nsanje, a Chidanti Malunga auza Boma kuti likhazikitse lamulo loletsa a Malawi kubeleka ana oposa awiri. A Malunga anauza wailesi youlutsa mawu ya boma ya MBC kuti… ...