Anjatidwa pochita malonda ogulitsa munthu
Zina ukamva kamba anga mwala! A Polisi ku Dwangwa m'boma la Nkhotakota amanga abambo awiri powaganizira kuti amafuna kuchita malonda ogulitsa mwana wam'muna wa zaka ziwiri. Abambowa ndi a Pilirani Thumba a zaka 38 omwenso… ...