
Maumboni ambiri akupelekedwa: Maranatha ikuyambiraso ma adiveti
Patadutsa miyezi iwiri anthu atawasowa ma adiveti okhudza mankhwala azitsamba osiyanasiyana omwe samasempha nyumba yofalitsira mawu, kampani ya Maranatha yati yayambilaso kusatsa malonda ake munjira zonse. Bungwe loyang'anira za mankhwala la PMRA komaso loyang'anira ntchito… ...