Ophunzira wafa atagundidwa ndi njinga yamoto
Ophunzira wina wa zaka khumi (10) m'boma la Phalombe, wafa atagundidwa ndi njinga yamoto dzulo Lamulungu pomwe oyendetsa njingayi anakanika kuyiwongolera kamba kothamanga kwambiri. M'neneri wa polisi ya Phalombe, a Jimmy Kapanja, watsimikiza za nkhaniyi… ...