Mutharika wati MCP ikukoza zodzabera chisankho
Mtsogoleri wakale wa dziko lino a Peter Mutharika ati chipani cha Malawi Congress Party (MCP) chikukonza zoti chidzabele chisankho chosakha mtsogoleri wa dziko cha chaka cha mawa. A Mutharika amayankhula izi Lamulungu pa Njamba munzinda… ...