Vuto lakusowa kwa madzi lakula m’boma la Ntchisi
Anthu okhala m'mudzi wa Chikho, Mfumu yayikulu Kasakula m'boma la Ntchisi adanduala za vuto la madzi lomwe lakula m'mudziwu. Mudzi wa Chikho mulibe dilawo komanso mpope, ndipo anthu okhala mudziwu amakatunga madzi ochoka mu phiri… ...