
CRFA yamaliza kampeni ku Ntcheu
Akuluakulu kuchokera mu komiti yoyendetsa masewero a Mpira wamiyendo mchigawo chapakati ya Central Region Football Association (CRFA), amaliza kuchita kampeni ku mazoni a m'boma la Ntcheu, yomwe cholinga chake ndikugwetsa utsogoleri omwe ulipo pano m'bomali.… ...