Malo olembetsera kalembera wachisankho mulibe zipangizo za NRB m’boma la Zomba
Pamene ndime yachiwiri yakelembera wachisankho yatsala masiku khumi kuti ithe m'boma la Zomba, zadziwika kuti malo omwe kalembelayu akuchitikira mulibe zipangizo za Bungwe lomwe limalemba ziphatso za unzika la National Registration Bureau (NRB). Nzika zokhudzidwa… ...