Sitikufuna kubweleranso kwathu-atero mayi Hanoki
Mai Bertha Hanoki, ochokera m'boma la Nkhotakota amene akukhala pa msasa wa Ngala ngati malo omwe akukhala anthu omwe anakhudzidwa ndi kusefukira kwa madzi, ati iwo sakufunanso kubwerera ku mudzi kwawo ku Kanthum'dende komwe anaona… ...