
Waphwanyitsa sukulu kamba kofuna kukhala m’phuzitsi wamkulu
Mawu oti agalatiya mwataya chipangano apherezera pa sukulu ya sekondale yoyendera ya Emchakachakeni m'boma la Mzimba pomwe m'phunzitsi wina yemwe akuti anamema ana kuti achite ziwonetsero zokwiya ndi m'phunzitsi wa mkulu pasukuluyi amugwira pakhosi. Malipoti… ...