![](https://malawi24.com/wp-content/uploads/2023/07/DSTV-Malawi-235x176.jpg)
Kupsa pansi ndi pamwamba ngati chigumu; Multichoice yakweza mitengo ya DStv
…premium yafika pa K79,000 pa mwezi Pomwe mavuto a za chuma afika posauzana, a Malawi omwe amakonda zowonerawonera, alimbe mthumba kaamba koti kampani ya Multichoice Malawi yalengezaso za kukwera mitengo ya ma pakeji a DStv.… ...