![](https://malawi24.com/wp-content/uploads/2022/10/Peter-Mutharika-Mulhakho-wa-Alhomwe-235x176.jpg)
Siyani kudya gondolosi musanakule – APM
Mtsogoleri wakale wa dziko lino a Peter Mutharika wauza achinyamata kuti asamadye nawo gondolosi pofuna kuonjezera mphamvu. Iye wanena izi pa mwambo wa Mulhakho wa Alhomwe kwa Chonde mu boma la Mulanje. Polangiza achinyamata kuti… ...