Aphunzitsi alangiza boma kuti lichite zomwe lidalonjeza
Aphunzitsi omwe adamaliza maphunziro awo kuchokera m'sukulu zosula aphunzitsi akupulayimale zosiyanasiyanasiyana m'dziko muno m’gawo la IPTE 14, 15 ndi 17, koma sadalembedwebe ntchito ndi boma, apempha boma kuti lisamatsogoze ndale koma kukwanilitsa zomwe lidalonjeza. Izi… ...