National
0

A Katsonga akwiya ndi a Chilumpha

Wachiwiri kwa Mtsogoleri wa mgwirizano wa Tikonze People’s Movement a Mark Katsonga Phiri ati zomwe apanga Dr. Cassim Chilumpha popereka zikalata ku MEC ngati mtsogoleri…